Wachiwiri kwa mkulu woona chitetedzo cha m'madera akumidzi kunthambi ya a Police m'dziko muno Senior Supritendent Albert Nyongani wapempha a Police kuti adziyendera kawirikawiri malo (misasa) omwe anthu okhudzidwa ndi ngozi zokugwa mwadzidzidzi amakhala pofuna… ...
Articles By Raphael Likaka
Southern Region Water Board (SRWB) has announced emergency shutdown of main treatment plant for three to four days following theft of anchor straps on water pipes between Mulunguzi Dam and main water treatment plant. SRWB… ...
Mwana wakhanda wamiyezi yosachepera itatu yemwe mai ake sakudziwika wapezeka atafa mumtsinje wa Likangala mu Mzinda wa Zomba. A Auzious Chimalala omwe amakhala m'mudzi mwa Chilupsa mu Mzinda wa Zomba awuza Malawi24 kuti ana ena… ...
Six children aged 4 to 13 are struggling to make ends meet in Thyolo after their parents abandoned them. The plight of the child headed household was noted after Everlasting Life Ministries Church visited Khonjeni,… ...
Pomwe mabanja ena akusowa ana palinso mabanja ena akuthawa udindo wao wopereka chisamaliro kwa ana awo obereka okha mdziko muno. Ana awiri, Loveness ndi Liviness Weremu omwe ndi amapasa azaka 13, m'mudzi mwa Jolichi mfumu… ...
Mwambo wodzodza ma Deacon 20 ampingo wa Katolika udachitika Loweruka ku St Peters Major Seminary mu Diocese ya Zomba ndipo adatsogolera mwambowo ndi Bishop wothandidzira mu Diocese ya Chipata Mdziko la Zambia Ambuye Gabriel Msipu… ...
Everlasting Life Ministry Church has set up a new congregation at Chinamwali Township in Zomba to reach out to its members in the township. Speaking during the opening of the new congregation at Chinamwali Private… ...
Advancing Girls Education in Africa (Age Africa) has supported 30 girls with secondary education in Zomba District on top of supporting three other girls with tertiary education at University of Malawi from January to March… ...
The World Union of Catholic Women Organisations (WUCWO) General Assembly, which is meeting in Assisi, Italy has elected Mrs Lucy Vokhiwa from Malawi as WUCWO Board Member 2023 to 2027. Mrs Lucy Vokhiwa is a… ...
Minister of Local Government, Richard Chimwendo Banda, has disclosed that Zomba Stadium will be ready for use in December as government has allocated finances in the current fiscal year to complete the second phase of… ...
Malawi Network of Older Persons Organisations (MANEPO) and University of Malawi (UNIMA) students that are studying gerontology visited and assisted older persons that were affected by Tropical Cyclone Freddy at Chemusa in Blantyre. The group… ...
Makhansala ena amu Mzinda wa Zomba komanso Phungu wamu mzindawu Bester Awali adakonza upo wofuna kuchotsa Khansala Rams Kajosolo pa udindo wa wapampando wa Komiti ya ntchito zachitukuko. Kudzela muchikalata chawo chomwe adalemba ndipo chidasayinidiwa… ...
Development Communications Trust (DCT) has urged the media to write more on the negative impact of child marriages on top of writing court convictions and sentences about those that are found guilty of either marrying… ...
The Monkey Bay First Grade Magistrate's Court yesterday sentenced a 43-year-old man, George Lucian Phiri, to 14 years imprisonment with hard labour for raping his 15-year-old biological daughter and impregnating her twice within a period… ...
Bungwe lomwe limawona zamadzi mchigawo chakum'mwera la Southern Region Water Board layamba ntchito yomanga fakitale yopanga madzi a mumabotolo ndipo ntchitoyi idya ndalama zoposa K2.1 billion. Poyankhula kwa atolankhani pa Old Naisi Turn Off mu… ...