The District Commissioner for Zomba, Reignhard Chavula, says the Zomba District Council is well prepared to work with the Malawi Electoral Commission (MEC) in the 2025 tripartite elections. The DC made the remarks at Sunbird… ...
Articles By Raphael Likaka
Nduna yakale ya za masewero mu ulamuliro wachipani cha United Democratic Front (UDF) a Moses Dossi yamwalira. Mwana wamalemuwa Susan wati a Dossi amwalira kuchipatala cha Blantyre Adventist kucha kwa Lachinayi ali ndi zaka 70… ...
A polisi m’boma la Machinga alimbikitsa chitetezo pakati pamalire a dziko la Malawi ndi Mozambique pomwe akhazikitsa makomiti owona zachitetezo chakumadera akumidzi. A Polisiwa alangizanso mzika za dziko lino kuti zidzikhala tcheru pankhani za umbanda… ...
Minister of Information and Digitalisation, Moses Kunkuyu, says the government will not spare any defaulter who accessed a loan through the National Economic Empowerment Fund (NEEF). Kunkuyu made the remarks at Riverside Lodge in Zomba where… ...
Minister of Homeland Security, Dr. Ken Zikhale Ng'oma, has urged the University of Malawi MCP Students wing to participate in politics because they are the future leaders of Malawi. Zikhale Ng'oma made the remarks during an… ...
Anthu ochita malonda mumsika waukulu wa Zomba ati sakukondwera ndizomwe achita akulu akulu akhonsolo ya mzindawu pokweza mtengo wachiphaso kuchoka pa K200 kufika pa K300 patsiku. Wapampando wa anthu ochita malondawa a Ayatu Chidothe ati… ...
Star Nursery School in Zomba has appealed to parents to support their children in nursery school so that they realize their ambitions of achieving their aspired professions. The school's Coordinator, Sellina Bomani made the appeal… ...
Mayi wina yemwe dzina lake silikudziwika Boma la Zomba wathawa atapha mamuna wake pomukoka malo obisika. Wofalitsa nkhani za apolisi Boma la Zomba, Sub Inspector Patricia Sipiliano watsimikidza zankhaniyi poyankhula ndi Malawi24. Sub Inspector Sipiliano… ...
Commissioner of Police in the Eastern Region, Violet Magwaya, has called on Civil Society Organisations (CSOs) to renew their commitment in advocating for the protection of women against gender based violence (GBV). Commissioner, Magwaya, made… ...
Akhristu a Mpingo wa Katolika ku St Charles Lwanga Parish komanso akhristu a mpingo wa Anglican ku St George's Parish mu mzinda wa Zomba lero ayenda njira yamtanda mogwirizana pokumbukira imfa ya Yesu Khristu. Njira… ...
Girls Activist Youth Organisation (GAYO) has urged parents and other stakeholders to support girls and women so that they should be able to realize their dreams. Girls Activist Youth Organisation Programmes Manager, Gilbert M'bwana, said… ...
St. Luke's Hospital under the Anglican Diocese of the Upper Shire at Malosa in Zomba has commissioned a new digital X-ray machine worth K65 million. Speaking during the commissioning, Vicar General, Rev. Canon, Grant Timpudza… ...
Zakwathu Ku Namitambo (ZKN) Trust, a group of individuals from Namitambo in Chiradzulu distributed tree seedlings to three schools which took their turn to plant around their premises. The tree seedlings were distributed to Namitambo,… ...
Bwalo la Principal Resident Magistrate ku Zomba likuyembekezeka kudzapereka chigamulo chake pa 10 May kwa mkulu wa Bungwe la Malawi First a Bon Kalindo pamulandu womwe akumuyimba woyambitsa chisokonezo paziwonetsero zomwe adachititsa mu mzinda wa… ...
A teacher at Mulunguzi Primary School in Zomba, Mukire Rachel Mhango, has donated school uniforms to 20 needy students to encourage them to remain in school and concentrate on their education. Speaking when she donated… ...