Saulos Chilima
Days after he asked Malawians to stop handclapping for politicians, Vice President Saulos Chilima is reportedly not in good books with some Democratic Progressive Party (DPP) leaders. https://malawi24.com/2017/01/02/stop-applauding-stupid-things-chilima-tells-malawians/ Sources have told Malawi24 that Chilima’s remarks… ...
Nyasa Big Bullets
Mwina bola akanabela osewela a nyerere zikanamveka. Koma ayi ndithu chipongwe achita osewela awo omwe. Ife a Malawi24 tapeza umboni oti anthu ena ochemelela timu yampira ya Nyasa Big Bullets adasolola ndalama zimene zimayenela kupita… ...
Lazarus Chakwera.
A Boma komanso a chipani cholamula atopa naye mtsogoleri wa Kongeresi Lazarus Chakwera moti ayamba kumuvula pagulu. Akulualuku a chipani cholamula cha DPP anamemeza atolankhani mu mzinda wa Lilongwe pamene anayamba kumumasula mtsogoleri wa zipani… ...