By January 13, 2017

A Lazarus Chakwera ndi kutheka anagonja pa zisankho mu 2014, koma a chipani cholamula cha DPP sakugona nawo tulo.

Malinga ndi chikalata chimene chipani cholamula cha DPP chatulutsa, mtsogoleri wotsutsa bomayu ati ali pa kalikiliki ofuna kuchita chipongwe Boma la DPP.

Lazarus Chakwera

Chakwera akuti akufuna kulanda boma malingana ndi chipani cha DPP.

Mlembi wamkulu wa chipani cha DPP, a Francis Mphepo, ati a Chakwera agwilizana ndi nyumba zina zoulutsa mawu mu dziko muno kuti azifalitsa nkhani zabodza ati cholinga anthu aukile Boma.

“Akufuna amemeze a Malawi kuti apite kumseu akayambe zipolowe,” alemba choncho a Mphepo.

A Mphepo ati a Chakwera ali pa kalikiliki olengeza nkhani yoti Boma la a Mutharika linachita katangale Pogula chimanga ku dziko la Zambia.

Ngakhale a chipani cha DPP akukana kuti sipanachitike katangale, ma report anasonyeza kuti kugula chimanga ku Zambia panayenda njomba.

Zinamveka kuti Boma linagula chimanga pa mtengo okwela kamba koti ndalama ina amafuna achite chosolola.

Pakadali pano, chimanga chikugulitsidwa pa mtengo wa K12,500 ku misika ya Admarc. Koma akuti chimanga bwenzi chikugulitsidwa pa mtengo wa K5000 kukanapanda kusololedwa.
195 Comments

 1. I have never seen boma la mantha like this one.Chakwera asatsokomole AAA iai afuna alande boma,asapite Ku maliro ayi wayamba kampeni iiiiii kma

 2. Propaganda at its best

 3. Kulanda kapena kutenga?

 4. …feudalism is the only answer….POP-CORNiyo aziwabera akumwela omwewo, ife AYI!!!!

 5. Kkkk, kodi anthu mukuchedwabe ndi andale heee mufuse nkasa, adanena kale kuti ndale mkanyama koipa

 6. Osat Kulanda Ayi,, Koma He Is Taking What Is His,,,,, MCP Woyeeeee!!!!!!!

 7. Osat Kulanda Ayi,, Koma He Is Taking What Is His,,,,, MCP Woyeeeee!!!!!!!

 8. Chakwera ngati chipani chake chidamkana,….mukuganiza angalamule ndani?

 9. we dot want x 2 b presdnt but we nid changes so that we live haply.we dot hate apm nor dpp bt the way economy is.unless u tel us that things are ok,u cant tolerate it.may b problems rocking the country do not affect ppo who r strong dpp sapotaz.

 10. A MCP , mulipo ? Kkkkkkkkk

 11. Guys chiyambireni cholemba nkhani zonyoza atsogoleri azipani mchiyani chinasinthako panganizanu ndimabanja anu or mutakhala inuyo

 12. Boma Lake liti? A Chakwera ali anthu oti nkulanda Boma?

 13. Nthawi zambiri anthu amasokonezeka pankhani zandale chifukwa cha News paper ngati panopa malawi24 ikuonjeza bodza musinthe

 14. Bola Alande Dziko; Osati Bomalo

 15. what I observed is that politicians are lyk football clubs officials,they only being angels on opposing once gven a chance of ruling nzeru zonsezija ng’ooo.

 16. mwayamba kunjenjemela? 2019 paulendo

 17. Chakwera ndiye mbava yeniyeni.lnu anaona kuti chopereka Chimachepa ali koma ndikawone kundale.guy osachita mistake .Osaiwala anagwa MMANJA mwamulungu ndi jabulosi uyu mph wake wauja anaismpusisa Hava uja.

 18. Koma a DPP akudziwona uchisiru wawo, ayamba mantha tsopano akudziwa kuti Chakwera atenga boma pavute pasavute. Musanati DPP ndiya zisiru zokha zokha.

 19. Munasiya Ma Bible Ukooooo!!! Nde Lero Mwat Mupange Ndale!? Komwe Uliko Chakwera Umve Kut Mulungu Wakwiya Nawe Ndpo Boma Lino Sudzalamulira,pomaliza Mutu Wako

 20. If you didn’t vote for dpp you must just kip quite mkut dpp inabela mavotes pomwe ineyo ndnavotela dpp ife ambritu tinaivotela but the problem comes when you see that agalantia sanawine aliyese anavotela chakwera analuza sungamat ndewu ija sinaluze komano ndmangofuna mtendere that’s why ndavomeleza kuluza don’t lie to ppl when you luz u luz don’t expect to win when you gatta pikinin supporters DPP ND BOMA

 21. Mukumuopa Chakwera,Abusa sangalande boma,koma inu a Dpp zangokuvutani basi.osati mumupedzere zifukwa zoti mudzimumanga munthu wa a Mbuyeyi ayi.Musamusokonedze musiyeni munthuyi..

 22. Awa achakwera sangakhare papando komanso ndikaona mavuto akulu ndiakuti unsongoleli wakakamira kumwera dzikumanyasa chifukwa pa dzatenga nthawi kt udzafike Ku chingawo chapakati.kuti udzafike chingawo chapakaki ayembekedzere dzaka 27.kunsongoroku osati pano mukalambira popo achakwera pa otsawoo ndiye pando wanu.achakwera osati oramura dziko never.

 23. We r the MCP’s pambuyo pa Achakwera nganganga mulira Xeni-zen

 24. chakwela wafika ponyada! ganizo lake ndilofunadi kulamulira boma! koma ndikanakhala peter sindikadalora wotsutsa azinditcha “patient/,olephera/mbuli yophuzira’ ndithudi akadandiva!! kwa ine chakwela mchitsiru,galu wa munthu,bwanji safuna kuthandizapo ndi zelu zofuna kuthana ndi mavuto we’re facing,bwanji sathandizapo odwala azipatala,koma kunyoza basi! zauchitsiru basi!! nanuso amalawi24 simulemba nkhani yoyamikira munthu,koma zomwe wina wanyoza boma basi! why? even mundi blocky vuto mayazi koma nanuso mumachita zauchitsiru! ndikadakonda nanuso mutakhala gulu lotsekedwalo.ndamaliza!!

 25. Kapeni inantha kale inu achakwera cholinga chanu mukufuna mutinthamangisire anthu amene akutinthandidza osati kuwaunikira amalawi.mukudziwa kale tengo umene boma limangulira chimanga.ubuli achakwera nanu munali mutaba kale dzapingo.2019. Munsowa dzopangira kapeni ndalama.

 26. Binnwell Kachikopa says:

  Cardiac arrest redeemed us from dictatorial evil Bingu, another cardiac arrest is very soon going to redeem us from these evil walking dpp leaders, God is not Peter Mutharika or Chaponda. Just wait, cardiac arrest is looming

 27. chakwera ndi ntondo angozo enieni

 28. Ine ndikuonanso KT chakwela ndiye mbava yeniyeni inu taganizani mozama komanso yamban kupenya patali munthu kusiya kutumikila mulungu,kusiya nkhosa zamulungu ndikujoyina ndale ndiye mukuona kt ndichanzelu? Amalawi azanga mwatan?bola mbava zomwezi

 29. Ameneyo ,chisiru mbuli yachabechabe, kulanda boma aona ngati kulanda munda eti ,CHAKWELA chisiru kwa baasi.

 30. Ameneyo ,chisiru mbuli yachabechabe, kulanda boma aona ngati kulanda munda eti ,CHAKWELA chisiru kwa baasi.

 31. ayamba kale kunjenjemera…sakufuna kulanda boma timvetsetsane koma Ibu akufuna kulanditsa yekha boma..kwacha

 32. Mwayamba Kale kunjenjemera? Kkkkkkkkkkk

 33. Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?

 34. Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?

 35. Matenda avutawa adafalisidwa ndi #MCP amene amaumiliza kugonana ndi aliyense pogwirisa mphamvu za chipani komanso #Chakwera analephela kusogolera mpingo ndi azasogolera dziko lake liti?

 36. Peter mutharika ndi proffesor wa mkalasi osati ku ndale,utsogoleri ndi mphatso yochoka kwa ambuye osati kungogwera ayi,munalowera pawindo lero mutulukiranso pa windo

 37. hahahahaha mwaba nokha chimangacho. Zangokubvutani. Musiyeni Chakwera. Sanakutumeni kukaba chimanga cha amalawi.

 38. muziti chifukwa chosaziwa ntchito a DPP akufuna ku zisiya okha!!

 39. guys do your politics am never voting again,, to hell with malawian politics you make the country look stupid but God is watching you.

 40. Its better the devil we had(MCP)than these so called saints we don’t know!

 41. Chakwera is a failure.who can put him on presidency. He failed to lead 200 people in his Church. No wonder he is failing to lead MCP .Lo a country; Malawi; with central region only. Forget .stop dreaming in vacuum.DPP woyee 2019 motomoto.

 42. Nyote wajinga2 hamjuwi mnachokifanya pumbav zenu

 43. we are behind opposition, mbavazi tikumana nazo 2019 ndipamene azaone kufunika kwathu

 44. Fwetseke…vitsiru va diphi phi…vidempete vachabechabe…anthu oduka mitu

 45. Some tyms a malawi 24 amalemba zinthu zopanda meaning,what they tryng to tell the ppl of malawi????

 46. Dr. Chakwera Bomaaaaaaaaaa!!

 47. Osanama Boma Ili Latikwana Heve Angakhale Boma Ili Likudziwa Kuti 2019 Lili M’madzi Amalawi Onse Amadziwa Kuti Boma La Malawi Lidagula Chimanga Ku zambia Mwakuba Kusonyeza Kuti Chimanga Chomwe Chidabwela Kuchokela Ku Zambia Ndindalama Zomwe Boma Lamalawi Limanena Kuti Lidagwilitsa Tchito Sizimayenelana Ndalamazo Zimachuluka Pomwe Chimanga Ndi Chochepa A Cham’kwelawo Sakunama Boma Ili Linabadi Ndalama Za Mondokwa.

 48. Chakwera is the most stupid person in Malawi coz he failed to take the government through ballot paper. i Dont think he can take the government through any means. He must be kissing his anus……

 49. Ndimamva chisoni kuona anthu mukukangana nkhani zokhuza agalu andalewa taganiza ndi mtsogoleli uti yemwe analowa m’boma ali osauka ndikutulukamonso osauka? Ndiye muzifunse why, kapena chikuna ninji aphungu athu sanayambepo akana kuti musationjezere malipiro nthawi iwo tiyambe takonza za mavuto ali mdzikowa?

 50. Kho Mwamzy says:

  Munthu wamkulu,ena angotekeseka naye kkkkkkk

 51. Its a time for DPP to rule this country ngat muli ndi milandu khani ndi pa 2019 election bas ngat azalowe enawo tizaone ngat azathetse mavuto M’Malawi.

 52. Its a time for DPP to rule this country ngat muli ndi milandu khani ndi pa 2019 election bas ngat azalowe enawo tizaone ngat azathetse mavuto M’Malawi.

 53. Nkhani ya chakwera wanuo imandinyasa kwambiri anakanika kutumikira nkhosa zamulungu kuli bwanji kutumira dziko? Chimu2 chadyera ngati chimenechi ndipo akungovutika ndikubwebweta sangawine ataa!!

 54. O Ooooo Zamwe Mungandiuze Nthuni Inu Tsanotu M’mepa Nzongoonetselatu Kuti Ochakwela Oludzatenga Boma 2019 Komasotu Odara Ochakwela Sodaname Boma Iri Its Verry Hurd Kuba Odala Olutibela Olukapondeleza Kadziko Koomalawi Tsanotu M’mepa Okadapanda Kukhalako Mavenda M’mewa Dalatu Oma Admarc Om’mewa Okadati Gwirililatu Tikadasowa Kothawila Koma Oma Admarc Om’mewa Okhaula Ochimina Odziwaso Anya Awona.

 55. Chakwelayo kulanda boma, alimkanthu monga

 56. Bodza ili, Chakwara can not descend so low kufika polanda boma mwangosowa chonena inu.

 57. Malawi poorest country in the world

 58. kawirikawiri munthu amadana ndi chilungamo. Aboma mulikuba koma musatiopseze ai. makamaka chaponda mbava aDPP nose shem. chakwela sakulakwa vuto ndinu. Zodiac sidalakwe akukamba zoona, boma lakuba shem!!

 59. Face him, why fearing him?

 60. Tangowapasani achakwerawo ayendese dzikoli palibe zikulongosoka pa mw pano bola nthawi ya masten ija zikaonesa

 61. Adam Aluba says:

  Palibe kanthu ndipo zikhala bwino kwambiri

 62. Dziwani izi amalawi anzanga mungovutika ndikubwebweta za Galatiya uyu mukuti chakwerayu ameneyu oro zitavuta mpaka sangatenge boma la Malawi ndipo sadzalamulako mpaka kalekale ufuse John tembo bwino bwino .Amene adzalamule dziko Lima Ali pheeee inu simukudziwa munya muona tamangosililani ulamulilo wamzanuo ng,ooo

 63. Ibra Rajab says:

  bola Atalanda chakwerayo basi nanga pali chime chikuchitika apa?

 64. Wabwino ndani kudziko kuno?

 65. JUST CHANGE UR STYLE OF LEADERSHIP,STOP OPPRESING THE POOR, DO WHAT IS RIGHT PALIBE AKUFUNA KULANDA BOMA APA PPLE WANTs JUSTICE TO PREVAIL WHY R YOU STIL KEEPING THAT TWO FINGER CHAPONDA?

 66. a Malawi panopa azindikira sazaperekanso zaka 10 kwa President kuti alamulire dzikoli,,,,ndi Bakiri yekha yemwe anakwanitsa zaka ten,,,Bingu zaka 8,,,anamuchotsa ndi Mulungu pa mpando a Malawi atakwiya ndi ulamuliro wake mu term yachiwiri,,,Joyce Banda zaka ziwiri nayenso atangotsegura loko anthu kunali kuba ndarama ku likulu la boma,,,anthu anakwiya naye ndipo sanamuvotere amene anajijilika kumuvotera ndi omutsatira akewo,,,ndye awanso a Petulowa mukumva kuti zachitika,,,,koma 2019 sadutsa

 67. Kodi munthu kuzuzula ndikulanda boma..

 68. i hate politics . had to say it

 69. Zoopsezana zidatha nthawi ya chipani chimodzi. What is wrong with the leader of opposition when he opposes? If ordinary citizens are opposing, what do you expect the “leader” of opposition to do? Do not think you will be there forever. TIME WILL TELL. Dphwiphwiii chipani cha mbava, zigawenga, the failures.

 70. Haha #Chakwela amphawi wamukwana bola dpp kaya mukut ndiakuba bola tizitukuko tao taziona olo atati achoke lero titha kuzilodza nanga Chakwela olo atati wafa lero muzaloza kut wakupangilani chan agalu inu? Mcp ndmaipasa ulemu ndkamamva za #Kamuzu osat ana onyela nyelawa aka #Chakwela zazi dikilan muonenso dpp ikuwinanso kachikena cz #pp inatha #udf inatha #Mcp akungokanganamo okha okha mpaka kuotchelana ma galimoto bcz of Chakwela ndye mukuona ngat Mcp ingalamulire dziko lino Kkkkk mudakalirabe pepan

  • Kho Mwamzy says:

   u should be talking of DPP vs MCP not Chakwera vs DPP rather pitala vs Chakwera, pitala wapanga chani choti tizamukumbukire?

  • Dpp ili under ndani? Dpp ikamalakwitsa anthu amalodza chala ndani?

  • Pitala Wapanga Chitukuko Chokweza Chimanga Ndi Kuba Chimanga Cha Zambia Ndikubisa Chaponda Nanga Magetsi

  • Tatchula zomwe wapanga mdala wako wopanda manoyu ali mboma tiloza bwanji za chakwera ngt analamulilapo, umbuli osamachita kudzitsatsa osamangokhala osapanga cmnt bwa,kkkkkk km enanu kuvetsa chson

  • Pitala pazaka zitutu wapangapo chana kumangobela anthu ovutika basi

  • galu wamkulu ndiiweyo..Chakwera analamulira dziko lino liti kuti tikaloze chitukuko chake..Ibu wakoyo nde palibe 0 weniweni akungotisaukitsa ali pheee galu nzakoyo nonse ofunika chain

  • Chakwera citsilu camunthu azawina kwawo komko but never in the south !! Mcp inatizunza kwambili kumwera

  • takulani a malawi,mcp ya kale ija inatha,alipowa ndi anthu anzeru zawo ndipo sangabwerezenso zakale zija.

  • Komaso bola nthawi ya MCP yo timazuzika mukutero koma cilicose pamoyo Wa munthu cinali bwino talk of cakudya ,maphuziro, umoyo, magetsi in short zonse zinkayenda nanga pano

  • Haha ndzakupasan ulemu nonse amene mukunyoza dpp mukazafa ndiamene ndtazaziwe kut mdziko munodi mulinjara nanga munayambila kudandaula muja simukufa bwanj mpaka pano mulindizizukulu zanu enanu mpaka mwakula opanda chilema ndye mavuto ake ati mukuwanenawo zaulesi basi muzipanga maganju ngat ntchto zikusowa or mumuuze #Chakwela wanuyo akulemben ntchto yosesa zitosi za #tambala wakuda mumvekere kwacha ! Kwacha ! Ndye mukudandaulanji mesa kumalawi kwacha kod Kkk bravo mr #Peter #Muthalika ziko lilibwino kale ili but akufuna kusokoneza ndi awa a #Chakwela anathawa ku lalikila mu church pano akutukwana presidnt aneneri onyenga mumakwana mr ka Chakwela go to hello wif yo fuckn cheap pussy party well knwn as #mcp

 71. Kkkkkkkkkkk koma mantha ake

 72. Zanu izo ine ndiri bzy kugwira ganyo

 73. Mmmmmmmmmmm pezani zina zokamba kkkkkk

 74. Kape,mchewa ngati ameneyo tinamukana kalekale mu 2014 muja alibe ntchito akulira ndi mtima,Boma ndi lathu ili tizingosinthana ku south konkuno.

 75. Chokanipo makape inu a DPP zisiru za anthu tatopa nanu bwanji mngosazika ngati zakulepherani ndi Nyapapi wanuyo

 76. Dzna lot ibu or bwampn, limandmvetsa kukoma. Kutengela nd mmene mwn dznalo akuonekela.

 77. DPP SIKULABADA ZA ANTHU

 78. Driver akamyendesa basis mwausilu atha kuphetsa anthu,alandidwe stealing ena ayendetse anthu akhale moyo. Ah sinaone bama lonseli kukaopa munthu mmodzi. Nanga akazayamba ntchito limodzi ndi manganya si ma bp,ena kubibidwa ngati nthawi ya treason case ija.aaaa. mwinadi mavoti zisakho zapita zija kalipokalipo kanachitika kwa chakwera.nanga mantha amenewa bwanji anthu asyankhule basi mayooo mayooo.

 79. A malawi24 ndinu abodza munatinamiza kuti the president is going to conduct a rally in nsanje on wednesday apa mwanamanso i can see politicians driving u. Paja munthu akakutsutsani u brock him ngati afriem brock me.

 80. as we draw closer to 2019!

 81. mantha boma, kkkkkk. maulemu kwa Chakwera, man akuchokitsani, keep on fighting for us

 82. Cameron says:

  Ayerekeze Awone.

 83. U are failing to get inner peace because of the maize u steal. For show you will lose come 2019.this is multiparty democratic nation. Why u always want to silence a potential party. We are sick of your games. Kachipani kaanthu akuba

 84. Nawo adpp ndi manyaka bwanji !! Wy kumalimbana ndimunthu oti he wont b president az long az our voting system will still b based on majority rule ? Kodi mesa dpp comes from komwe kuli ambiliko ?? Mlekeni azawine kumpoto ndi central kwakeko !! Kwawo kwa mcp dpp izizapeza mavoti koma iwowo kuno ndi zero chitsanzo ndizisankho zinacitika zama by election Ku mcinji zomba kasungu pomwe dpp yapeza kukasungu pomwe kuzomba mcp zero . The same with mayor elections !!

 85. Kelly Kamb says:

  DDP is full of bunch of fools

  dpp Boma

  dpp chilungamo

  dpp chitetexo

 86. galu mukamamuyamba alipachean musamaone ngati saluma,muchenjere kuti akangodura pacheani muchotsedwa akatumba samalani a APM mwakhala pang’ono ndondocha zanuzo ziuzeni tatopa ndikutibera misonkho yathu agalu inu

 87. Sanagonje Ibu wanuyo anaba ma vote open your eyes my fellow Malawians some people are not born leaders but you force them to be a leader Ibu has failed malawi is seing a danger warning signs

 88. Welcome to africa the darkest continent of earth shaped like a question mark

 89. Welcome to africa the darkest continent of earth shaped like a question mark

 90. Odyazake Alibe Mlandu, Mchifukwa Chan A #dpp Mukunjenjema?

 91. Peter apite basi 2019,iwe ukoona ngati ndi kutali. Uwona!

 92. Mulira DPP tizawinaso 2019

 93. Koma mbava za DPP osanama zafika pakuba mwa uchisiru ndikwabwino kusiya kut ena atenge ayendese dzikoli. Ndikunena pano Britain yapereka 193 million pounds yot achepesere umphawi muziko muno koma ayi ndithu akuluakulu athoyolera ndalamazi mmatumba awo kutisiya anthufe tikuvutika.

  Nsanene nkhan ya ndalama zomwe chaponda akubazi linaperereka ndi dziko America kut agule chakudya ku Dziko lino koma Zachisoni ndithu waba ndalamazi . Anthu kut alembe a nkhaniyi mukusekanso pakamwa choona chisaziwike shame Peter Ndi Anzakowo bg up Times news

 94. Ndikwambwino chakwera atenge upulezideti chifukwa ntchito za mtsongoleri wa a peter sidzioneka katangale basi

 95. Azafa osadwala asamale

 96. Akufuna athawise nkhani ya chimanga anthu azikamba imenei nde munyeratu!!!!!

 97. I think this handsome man gives sleepless night to Dpp

 98. akapusa alandidwa adpp chifukwa adpp achulusa zibwana zakuba

 99. Anthu ochita zamdziko ndichoncho basi kukanganilana zapadziko cholinga choti alemere nd misonkho yamphawi kma anzelu akulimbirana ufumu wakumwamba ndipo ochita chamuna akuwupeza ufumuwo

 100. Boma2 simasewera! tangoyimanipoyera muwuzemtunduwa a Malawi kutimwalephera,anzanu akuthandizeni,basi!

 101. That’s a welcome news to us chakwera better do it fast

 102. DPP ikuthawa chithunzithunzi chake chomwe , 2016 inayenda moyera , yapondereza a Malawi , yapha a Malawi ndi njala , yapha mabizinesi a Malawi. 2017 ino iyembekezere zokhoma bwana weniweni aoneka kuti kuti , kodi ndi iwowo kapena ife timkapita kukawasankha pa mavoti . Chakwera asadane naye chifukwa akulankhula zofuna a Malawi .

 103. Kulanda boma losauka ngati ili ndimavuto ndithu

 104. Dpp Ali nje nje nje cz of chakwera especially cz they known kuti Ali pampando wokuba from chakwera yemweyo so sangagone naye tulo.dpp mwayaluka

 105. Dpp Ali nje nje nje cz of chakwera especially cz they known kuti Ali pampando wokuba from chakwera yemweyo so sangagone naye tulo.dpp mwayaluka

  • Anamubela cakwera ? North vote for amayi central vote for mcp & south vote for dpp . Therefore the region with high population z south so hw cakwera who come from minor region b the winner ? If dpp comes from north ur comment would hv make sense

  • Anabera y mbendera amalira?y amakana kuwerenganso votes and all computer systems hacked thru chilima.u u dont know??? Why akumusemera stoty yoopsa they want ti do treason like they did with casm chilumpha???? Evil pitala and all dpp followers,cashgaters.admarc maize gaters.shame

  • All those illegularities anganene ndani kuti dpp inawina? Whre in the world munthu amawina ndi 36percent meaning 64persent sinamuvotere.ask pitala will tell you kuti anabera

 106. Eeeeeeh kkkk a boma akudera nkhawa ndi munthu wa opposition kkkk

  nde sanatitu

 107. Kulanda boma lake liti?

 108. Mwina kapena ku Malawi mkukhala nawo mbili zolandana boma.But i wil wonder if that happens,MCP has a lust for power since it has been in opposition for 20 yrs now

 109. ASANGOFUNA KOMA ALANDILETU ZIKHALABWINO.

 110. Bvuto ndilakuti olamula amene alopowa akumuopa chakwela, sizoti azinena zomuyipisa apa n for the way i c its btr one party system timadula makadi ndipo ndalamayo imagwila ntchito zotukula boma than this pipo who are full of corrupted. Pa umoyo nthawi yomwe ndimakula ndinalibe maganizo ozagwila ntchito mayiko akunja koma the way things are it made me left my blvd country. Koma ndimene kwacha ilili panopa olo Mwana wokwawa akuuza zopinda kunja shame on u bingu leave chakwela alone

 111. Love Khamu says:

  dzikoli ACHAKWELA akuitenga ngt ndikumozambiq et??? zakunyelo basi Ndale zkusokoneza kwambili ndichfkwa chake mwatulusa k2.000 ya solid kupusa basi…

 112. Kulamulilidwa ndi agwape ndi vuto, kodi amakagula chimanga ku zambia ndi chakwera……
  Zinthu zakusokonekelani mukufuna muone ponamila.

 113. Boma lake liti? Palinso zoti pali boma apa.

 114. Zayenera kutero ndipo tikuthandiza chakwera kulanda boma

 115. Koma apa dpp mantha basi alibe zida uyu koma Chauta akunva kulira kwa malawi

 116. Can someone shut up here

 117. Mmmmmmm thats nonses

 118. Atalanda bolani, boma ili liri mmanja mwa chitsiru

 119. DPP has always had insecurity issues.

 120. Fuck Malawi24 ur backing up this Gvnment so much I’ve never seen u publishing good stories concerning Opositions

 121. Kkkk koma Ndale yavuta apa 2019 kuchedwa ine

 122. Boma lake liti? Boma lomweri la Chiradzulu lomvetsa chisoniri

 123. Yes if u continue to stl our money u wll s in 2019.Chaponda stl alot of money 4us and people nw dying bcz of him.Wat kind of leaders is this?.

 124. CHAKWERA NDI MKANGO WA MALAWI ALANDE BASI

Leave a Comment