Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera ati mitengo ya zinthu mdziko muno imapitilira kukwera kwambiri chifukwa boma linagulitsa makampani a boma omwe amatha kuchititsa kuti dziko lidzipeza ndalama zambiri kuti katundu adzikhala ndi mitengo… ...
Articles By Mphatso Khutcha Richard
Phungu wa nyumba ya malamulo wa dela la Lilongwe Mapuyu South Esther Cecilia Kathumba ati akapita kunyumba ya malamulo akawupanga mpando wa mtsogoleri wa dziko kuti ukakhale wa muyaya ndipo kuti a Lazarus Chakwera adzapitilize… ...
Bungwe lowona masewelo a mpira wa miyendo pa dziko lonse la FIFA lasankha a Godfrey Nkhakananga kuti akayimbile masewelo a ndime ya chipulula a mu mpikisano wa World Cup a mchaka cha 2026. Malingana ndi… ...
The Mzuzu University is still holding in limbo thousands of its alumni who had to formally leave the university with the coveted paper that opens doors to some. Pending graduates of the university have raised… ...
Kafukufuku ataulula kuti khonsolo ya boma la Dowa ndi yokhayo yomwe yachita bwino pa kugwiritsa ntchito bwino ndalama za khonsolo zaonetselatu kuti ma khonsolo ena akukanika. Malinga ndi kafukuku wa 2024 owona za momwe mankhonsolo… ...
Malawi Congress Party (MCP) National Director of Youths and Minister of Local Government, Richard Chimwendo Banda, has strongly denounced political violence within the party. Addressing a political gathering in Dowa on Sunday, Banda emphasized the… ...
Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Mukuru wanderers Nsazurwimo Ramadhani wazisiya, watula pansi undindo wake patangotha myezi yosaposa inayi chibweleleni ku timuyi. Mphunzitsiyu yemwe watsogolera masewelo asanu ndi atatu okha (8) watula pansi udindo wake… ...