Ramadhani wazidomoka

Advertisement
Nsanzurwimo Ramadhan

Mphunzitsi wamkulu wa timu ya Mighty Mukuru wanderers Nsazurwimo  Ramadhani wazisiya, watula pansi undindo wake  patangotha myezi yosaposa inayi chibweleleni ku timuyi.

Mphunzitsiyu yemwe watsogolera masewelo asanu ndi atatu okha (8) watula pansi udindo wake ku timuyi itagonja kawiri motsagana.

Ramadhani watsimikira Nyumba ina yolemba nkhani kuti watula pansi udindo ndipo anati ngati zotsatila zolongosoka zukanika kubwela mkwabwino kuleka.

“If the table doesn’t serve you anymore what do you do? complete the sentence yes I won’t comment further” anatelo polankhula mchizungu.

Mphunzitsi wamkuluyu wapeleka kalata yake yotula pansi udindo kwa mtsogoleri wa Timu ya Wanderers  Dr Thom Mpinganjira.

Advertisement

Leave a Comment

This site uses Akismet to reduce spam. Learn how your comment data is processed.