Mkulu wa banki yaiyikulu m'dziko muno ya Reserve, a Wilson Banda, akana zoti bankiyi ikufuna kutulutsa K10,000 yogwirana. Polakhula ndi atolankhani a Wilson Banda anena kuti Bankiyi ilibeso maganizo otulutsa ndalamayi pakali pano ndipo zomwe… ...