FCB Nyasa Big Bullets were made to sweat for points as they claimed a hard-fought 2-0 victory over Mzuzu City Hammers at Kamuzu Stadium on Saturday afternoon. It was a must-win match for the defending… ...
Articles By Malawi24 Reporter
Bungwe loyendetsa kalembera m’dziko muno la National Registration Bureau (NRB) lati ilo likupitilira kugwira ntchito yake mwaukadaulo ngakhale pali madandaulo kuchokera kwa mzika zina zokhudzidwa kuti kalemberayi sakuyenda bwino. Izi zadza pamene gulu la mzika… ...
Bwalo la milandu ku Lilongwe laimitsa mulandu wa a Shepherd Bushiri komanso mayi akunyumba kwawo a Mary Bushiri omwe akuyankha milandu yomwe adapalamula mdziko la South Africa. Banja la a Bushiri likuyankha milandu yokhudza kuzembetsa… ...
A tragedy mirroring Malawi's recent home-made beer fatalities has unfolded in Zambia, where 10 individuals have lost their lives after consuming the suspected brew. In the previous month, a locally brewed beer called 'Ambuye Ntengeni'… ...
Inu amene mukumapeza mwayi otsukuluza mkamwa pa nkhani zokhudza mtsogoleri wa dziko lino a Chakwera yambani kuyenda mosamala. Ayamba kunjata anthu kunja kuno ati chifukwa chonyoza a Chakwera. A Sainani Nkhoma a ku Dowa akuyembekezeka… ...
Iyi ithera ku waya ndithu. Mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera akuoneka kuti sanathane ndi moto omwe owatsutsa a Peter Mutharika adayatsa ku Blantyre lamulungu lapitali pa msonkhano wawo wandale. Adakapitiriza kuwayankha mokuluwika. Lero… ...
The 2023 Fam Goshen Women’s National Championship is complete after the conclusion of pulsating quarter-finals on Wednesday. However, the semi-finals list comprises Lilongwe-based teams namely last year’s runners-up Ascent Academy, Malawi Defence Force ( MDF)… ...