Renowned Malawian musician Lucius Banda says he will contest against Atupele Muluzi at the convention of the United Democratic Front (UDF). Lucius Banda, who is also member of Parliament for Balaka North, said he is… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
United Democratic Front (UDF) has turned the heat on Democratic Progressive Party (DPP) and President Peter Mutharika over plans to have Atupele Muluzi replace Saulos Chilima as DPP's running mate for the 2019 Malawi presidential… ...
Onse okonda nyerere ndi akufuna kwabwino, sonkhani limodzi limodzi kuti ulendo wa akatswiri a ligi opita ku CAF asauyende wapansi. Wa ana a Israeli mu chipululu. Ngakhale anakwela pachulu, kuziguguda pa chifuwa kuti iwo zivute… ...
Sanachiteko olo msonkhano umodzi oitanila anthu ku chipani. Olo kuvala makaka a chipani sanachiteko. Osewela mu timu ya Bullets amene tsopano walengeza kuti mtima wake uli pa ndale, Anong'a Fischer Kondowe wanena kuti iye ndi… ...
Bambo Francis Itende amene anatsomphola phasulo la a Mutharika agamulidwa kuti ndi olakwa. A Itende amene anachita chipongwe chawo chaka chatha pa 23 December anatsomphola phasulo m'manja mwa a Mutharika ati chifukwa amayesa muli ndalama.… ...
Eni ake akolawo ali ndi chimwemwe kuti akhwasula, kuti mavoti onse a Kum'mwera kwa mzinda wa Blantyre tsopano akhala awo. Koma kwa aneba awo ndiye kuli phwete. Pamene ndale zafika pa chi inde inde, chipani… ...
Democratic Progress Party (DPP) has warned Malawi Congress Party (MCP) to be wary of Reverend Maurice Munthali who joined MCP, saying the Reverend is unpredictable and behaves in the manner of a 'political prostitute'. DPP’s… ...