Ulendo wa ku CAF watalika kwa nyerere: ayamba kupemphetsa

79

Onse okonda nyerere ndi akufuna kwabwino, sonkhani limodzi limodzi kuti ulendo wa akatswiri a ligi opita ku CAF asauyende wapansi. Wa ana a Israeli mu chipululu.

Ngakhale anakwela pachulu, kuziguguda pa chifuwa kuti iwo zivute zitani chuma ali nacho chochuluka chokawafikitsa ku mpikisano wa CAF, manoma tsopano abwela poyela ndikupempha oikonda timuyi achite limodzi limodzi kuti ulendo wawo wa ku CAF ukhale wa thyathyathya.

Nomads

Nyerere zikupemphetsa

Nyerere zatulutsa uthenga opempha ndalama za ulendo wawo wa CAF. Iwo mwa njira ina akumema a Malawi akufuna kwabwino kuti atumize kangachepe kudzela ku Airtel Money ndi ku Mpamba.

Manoma ayamba kale kupempha ngakhale kuti sanasewele ndi komwe masewelo awo oyamba amene akuyenela kuti asewele ndi AS Vita ya ku DR Congo.

Koma mlembi wamkulu wa nyerere a Mike Butao ati kupempha kwawo si ndiye kuti ali mmaluzi ayi.

“Tili ndi ndalama zokwanila ndithu koma sikuti kangachepe sikangatithandize penapake. Tifunika kusewela masewelo opimana mphamvu ndi matimu ena akunja. Zifuna ndalama zimenezo,” anatelo a Butao.

Share.

79 Comments

 1. JAMES CHUMA and his fellow bigots can sponsor Nyerere. We thought ma vendor ogulitsa magalimoto will “be forward” kuthandizapo apa!
  Ife ndalama tilibe. Ngati mukufuna ingopangitsani promotion.
  Nthawi yoti “Anyakhavi” ndi “Akharupa” omwe akhala akudya ma gate collections abweze ndi ino.
  Osamayamba kufuna kupita ku chimbudzi musanadye. Mwathamangira kukumba chimbudzi pano mukutivutitsa kuti tikudyetseni chifukwa mmimba mwanu mulibe tudzi toti mukanyere! Lol!

 2. Koma page ya Malawi 24, imalolelanji mabulutu kumalemba nkhani mopusa chomwechi,,,?
  Anthu azikutenga serious ndiuchitsiru wake umenewu

 3. Amalawi kuzolowera kupemphetsa!,kodi simesa muli ndi sponsor!,simunamuwuze!,anzanu aBullets nthawi yija ankapephetsa chifukwa analibe sponsor!,nanga inu!,osamatelo munaziyamba nokha!,osadalira kupemphetsa!

 4. This Zambian is not knowledgeable with what has happened to Zambian kwacha. The Zim kwacha has undergone a process called redenomination, where some zeros are removed from the currency or a decimal point moved some places to the left. This is done because monitory headaches and high inflation. Remember in Zambia, there were K20,000 and K50,000 notes. So to reduce the dead weight of carrying money to markets and shops, redenomination has been considered. However, the value and buying power remains the same because this is not revaluation. I think I have schooled this stupid Zambian who thinks the redenominated Zambian kwacha is any better than our Malawian kwacha

 5. MMMMMM Musadzivute Guyz ndipo ndikupempheni kuti mudziwe kutseka pakamwa panupo, zomwe mukunenazo ndithu ndimaganizo anu amenewo ndipo nyerere sixikusowekelanso kuti inuyo mupeleke Kali konse khalani ndichingambwe fc yanuyo koma nyererez zamyamuka waku Caf basi inu khalani nsanje yanuyo

 6. Nanga osapita ndiweyo bwanji useless mmalo momalemba zinthu zothandiza Malawi ulibuzy kulimbana ndi team ya noma imakumvetsa kuwawa eti kakolope India ocean

 7. amenewatu ayenera azione kaye, masapota 2much mwano, kuyankhula chipongwe as if they are on top of world. zampira koma matama okhawo…!

 8. Hahahaaaa Neba Neba Neba!!!!! Don’t force matters.Sitimapanga ma plan kudalira ndalama zopephetsa kodi mesa muli sponsorship??.
  Inu mukatitukwanitsako basi

 9. And someone somewhere is comparing Zambia and Malawi. when even your clubs are failing to participate in the CAF competitions due to lack of funds. For your own own information, our Zambian clubs, just a shirt sponsorship deal is worthy K1.7 million, which is billions if not trillions in Malawian Kwacha.

 10. Tikupaseni ndalama ngati mukachitako bwino zachamba mesa mumadalila kukoza pagolo zikozani mwina patuluka ndalama muwapephe ambuyanu

%d bloggers like this: