Inkosi ya Makosi Mmbelwa, imene ndi Mfumu yaikulu ya Angoni, yadzudzula a Livingstonia Synod ndi kuwachenjeza kuti akapanda kusamala athamangitsidwa mu dera lake. Pa mwambo oveka ufumu a T/A Mzukuzuku ku Mzimba, mlembi wamkulu wa… ...
Articles By Kondwani Mkhalipi-Manyungwa
Mpingo wa Katolika mu Diocese ya Zomba watulutsa chikalata choonetsa kukhumudwa ndi wansembe wawo a Thomas Muhosha amene anamangidwa poganizilidwa kuti anatengapo mbali pa imfa ya a Macdonald Masambuka. Malinga ndi chikalatachi, a Muhosha aimitsidwa… ...
Ati za Chilima muiwale. Ngati aimile ndiye mwina chipani china basi koma kuja ku DPP, palibe amene akufuna a Mutharika achoke. Anthu ali nganganga pambuyo pa a Mutharika. Komiti yaikulu ya chipani cholamula cha DPP… ...
Top brass of Democratic Progressive Party (DPP) has endorsed President Peter Mutharika as torch bearer for the party in the 2019 polls, effectively breaking rank from Director of Youth Lewis Ngalande and former first lady… ...
Pamene moto umene anayatsa alamu a mtsogoleri wa dziko lino Mayi Callista Mutharika ukukhala ngati ukuvuta kuthimitsa, amene ali ndi udindo wa zothamangathamanga mu chipani cholamula a Ben Phiri ati kunena kuti Chilima atenge utsogoleri… ...
Ati iwo adanena kale kuti dziko liri mmanja mwa agalu koma ena adali kukayika, tsopano pano ndi uthenga umene afuula Mayi Callista Mutharika mu chipululu kuti a Peter azitaye ndiye kuti zaphelezera basi. Amene akutchulidwa… ...
After a week of breaking ranks with his brother-in-law who is also the President of the country and ruling DPP, former first lady Callista Mutharika was absent at a private memorial mass the Mutharika family… ...