HIV law has remained unknown to many since its introduction in 2018. The National AIDS Commission (NAC) is raising the alarm that a large part of the population is unaware of the HIV and AIDS… ...
Articles By Ben Bongololo
Kwachema kwa Manase ku Blantyre pamene apolisi ayamba kunjata anthu onse omwe akugulitsa mowa omwe ndi owopsa ndipo ukutchulidwa ndi mayina monga: Ambuye tengeni, magaga, komanso taya njinga omwe pakadali pano waphapo anthu asanu (5).… ...
Ofesi ya Zaumoyo m'boma la Blantyre yati ikufufuza za imfa ya anthu asanu omwe amwalira kutsatira atamwa mowa osadziwika bwino ndipo ofesiyi yati idzabweretsa poyera zotsatira zakafukufuku-yi akatha. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe khonsolo… ...
Ophunzira wamkazi wa sitandade 5 ku Mulanje wadzipha chifukwa chokwiya ndi malangizo amayi ake omuletsa khalidwe lake lopanga zibwenzi atadziwa kuti akuchita chibwezi ndi m’nyamata wina mdelaro. Nkhani yonse ikuti mtsikanayu, yemwe dzina lake ndi… ...
Kuchema kumabwalo amilandu pomwe bungwe lomwe limathana ndi katangale m'dziko muno la Anti-Corruption Bureau (ACB) lati likuyembekezeka kuzenga milandu khumi, isanu ndi iwiri (17) yokhudza katangale m'mwezi uno wa April ndipo pa milanduyi pali anthu… ...
Boma kudzera muunduna owona za Ulimi m'dziko muno watulutsa mitengo yoyambira kugula mbewu ya chaka chino ndipo mwazina Chimanga chizigulidwa pamtengo wa K650 pa kilogiramu. Izi ndi malingana ndi chikalata chomwe undunawu watulutsa lachinayi pa… ...
Inu anthu omwe mumatuluka kunja kwa dziko lino tamverani! Nthambi ya lmmigration ndi Citizenship Services m'dziko muno yatsutsa mphekesera yoti ziphanso za dziko lino sizikuvomerezedwa pamabwalo ena okwelera ndege. Nthambiyi yanena izi lero kudzera mchikalata… ...