Kutsatira mpungwepungwe omwe wadza kamba koti a Lazarus Chakwera asintha dzina la chipatala cha Phalombe kukhala John Chilembwe Hospital, m'modzi mwa anthu omwe amayankhulapo pa zochitika m'dziko muno a Wonderful Mkhutche ayankhula moyikira kumbuyo a… ...
Articles By Ben Bongololo
Boma lati ligawa masikito otetezera ku udzudzu mzigawo zonse m'dziko muno pofuna kuthana ndi nthenda ya malungo yomwe ikadaperekabe chiwopsezo chachikulu pa umoyo ndipo ntchitoyi igwilika ndi thandizo la ndalama pafupifupi 84 biliyoni kwacha lomwe… ...
Kutsatira kusefukira kwa madzi komwe kwakhudza anthu m'boma la Dowa ku Mponela, bungwe loona za ngozi zogwa mwadzidzidzi la DODMA dzulo lapereka thandizo losiyasiyana kuphatikizapo ufa, mabulangete, mabigiri, matenti, komanso nyemba. Bungweli lapereka mabulangete okwana… ...
Tsopano mayendedwe akhala wovutirapo pa msewu wa M5 pamene madzi ochuluka adula msewuwu, omwe umatchedwanso kuti Lakeshore, kamba ka mvula yamphamvu yomwe yakhala ikugwa. Msewu umenewu waduka pa malo otchedwa Mwalawoyera kuchokera pa Salima Turn… ...
Tsopano Mavuto Phiri ndi mfulu popeza bwalo la milandu ku Karonga lathetsa mlandu womwe wakhala akuganizilidwa kuti adapha mchimwene wake mchaka cha 2018 pa mkangano omwe udabuka pakati pa abambo ake ndi mchimwene wake amene… ...
Apolisi kwa Jenda akusunga mchitokosi njonda ina yazaka 33 zakubadwa yomwe inapezeka itabisala kudenga la sitolo ndipo anachita kuthira utsi wokhetsa misonzi kuti itsakamukeko. Malingana ndi mneneri wa apolisi m'bomali a Macfarlen Mseteka, njondayi yomwe… ...
Kampani ya MultiChoice yatsimikizira anthu okonda masewero a mpira mdziko muno kuti mpira wa chaka chino wa Africa Cup of Nations (AFCON) ukhala ukuonetsedwa pa kanema wa Super Sport Chikalatachi chadza pamene masiku apitawo panali… ...