Nyumba yosindikiza nkhani ya m’dziko la United Kingdom ya British Broadcasting Company (BBC), yawonjezera mkwiyo komaso chisoni cha a Malawi pomwe yanena kuti malemu Saulos Chilima anazengedwapo milandu ya katangale m'boma. Lachiwiri, BBC Africa yatulutsa… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Bungwe lowunika mauthenga la Malawi Communications Regulatory Authority (MACRA) ladzudzura mchitidwe otumizirana zithunzi zowopsa za ngozi ya ndege yomwe yachitika Lolemba m’dziko. Malingana ndi kalata yomwe wasayinira ndi mkulu wa bungwe la MACRA a Daud… ...
The 2024 Malawi Investment and Trade Forum which aimed at exploring ways Malawi may progress in various sectors, has been cancelled in Dar es Salaam, Tanzania. Malawi High Commissioner in Tanzania, Andrew Kumwenda, told delegates… ...
In a solemn address to the nation, Malawi's President, Dr. Lazarus Chakwera, expressed deep sorrow over the tragic loss of Vice President Dr. Saulos Chilima and eight others in a plane crash. Confirming the discovery… ...
Mtsogoleri wa dziko lino walephera kunyamuka ulendo wake opita m’dziko la Bahamas komaso Switzerland kamba kakusowa kwa ndege yomwe anakwera wachiwiri wake Saulos Chilima. Kalata yomwe boma latulutsa yomwe wa sainira ndi mlembi wa mkulu… ...
In its recent Sustainability Report released on June 7th, 2024, Airtel Africa, a leading telecommunications and mobile money services provider, announced a surge in its customer base across the 14 countries it operates in, attributing… ...
Pomwe anthu ena amafalitsa mphekesera kuti woyimba Lucius Banda wamwalira, mkhalakale pa mayimbidweyu wayankhula kwa omutsatira pa tsamba lake la fesibuku. Banda yemwe amadziwika ndi dzina loti Soja ali m’dziko la South Africa komwe akulandira… ...