Five buses carrying 285 Malawian nationals coming from South Africa have arrived in the country through the Mwanza formation. This is a Malawi government program to repatriate citizens who were stranded in South Africa due… ...
Articles By Archangel Nzangaya
Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika adzudzula mchitidwe wa zipolowe pandale omwe wakula m’dziko muno koma ati gwero lazonsezi ndi ndikuyankhula udyo kwa atsogoleri azipani zotsutsa. A Mutharika amayankhula izi lachisanu kudzera kwa owayankhulira… ...
Bungwe la eni maminibasi m'dziko muno la Minibus Owners Association of Malawi (MOAM) lati oyendetsa ma minibasi onse omwe sanatsitsebe mitengo yawo akuyenera kumangidwa. Wayankhula izi mlembi wamkulu wa bungweli a Felix Mbonekera omwe anati… ...
An association for independent school owners, the Independent Schools Association of Malawi (ISAMA), has threatened that it will call for demonstrations if government fails to open schools by 1st June this year. This is according… ...
Anthu asanu ndi atatu (8) omwe anapezeka ndikachilombo ka corona komwe kakumayambitsa matenda a COVID-19, athawa pamalo omwe amawasungira kwa Kameza mu nzinda wa Blantyre. Watsimikiza zankhaniyi ndi nkulu wa zaumoyo mu mzindawu Dr Gift… ...
Ku Malawi, chiwelengero cha anthu omwe apezeka ndi kachilombo ka Corona komwe kakumayambitsa matenda a Covid-19 chafika pa anthu 101 tsopano. Watsimikiza za nkhaniyi ndi nduna ya zaumoyo m'dziko muno a Jappie Mhango omwe amayankhula… ...
As part of efforts to support the fight against the COVID-19 pandemic in Africa, MultiChoice has partnered with the One Africa Global Foundation for a continent-wide broadcast of the COVID-19 Hope for Africa Concert. Confirming… ...