Zina ukamva ndithudi kamba anga mwala; pamene inu mumasamba thukuta mukangophika chipagala kwa kanthawi kochepa, mayi wina ku Nigeria walowa mu tsiku lachitatu akuphika zakudya zosiyanasiyana osapuma. Hilda Effiong Bassey amene amadziwika kwambiri ndi dzina… ...