Zadziwika kuti mayunitsi a lamya okhala pa khadi lija limachita kukalidwa lija, akhala akuthetsedwa mdziko muno sabata ya mawa ino. Izi zikutsatira mikumano yomva maganizo a anthu yomwe bungwe lowona za nkhani zolumikizana la Malawi… ...
Articles By Archangel Nzangaya
In six years, malaria may become history to Malawi only if the government put more into the fight against the disease, the Health and Rights Education Programme (HREP) made the call through a press statement… ...
A 32-year-old woman identified as Rose Machokolo was found dead at a home in Bangwe on Wednesday morning, April 24, the Limbe Police has reported. It is reported that Machokolo was last seen on April… ...
Potsatira zionetsero zomwe aphunzitsi msukulu za pulayimale m’boma la Machinga anapanga Lachinayi, ofesi ya maphunziro m'bomali yabweza ganizo lake lokweza ndalama ya welofeya yomwe inachoka pa K1000 ndikufika pa K3000. M'mawa wa Lachinayi, aphunzitsi a… ...
Aphunzitsi m'boma la Machinga athamangira ku ofesi ya mkulu wa maphunziro m'bomalo komwe akuti akufuna kupeza mayankho pa ganizo la ofesiyo yokweza ndalama ya welofeya opanda chidziwitso. Malingana ndi m’modzi mwa aphunzitsi, yemwe tayankhula naye,… ...
The European Union has expressed worry over Malawi's futile efforts to combat corruption, arguing that the results have fallen short of expectations. Rune Skinnerbach, EU ambassador to Malawi, expressed the concern yesterday, April 23, when… ...
Forestry Assistants at the Department of Forestry under the Ministry of Natural Resources and Climate Change, have threatened to down tools over their unpaid salaries. The assistants, 76 in number, were recruited by the ministry… ...
Illovo Sugar Malawi plc has started distributing maize flour in Chikwawa with 16000 households expected to be the beneficiaries. Chikwawa district is currently hunger-stricken following constant cyclonic weather which has been adverse to peoples’ settlement… ...
Pomwe miyanda miyanda ya anthu omwe amakhala mphepete mwa nyanja ya dziko lino akhudzidwa ndi vuto lakusefukira kwa madzi, mtsogoleri wampingo wa Enlightened Christian Gathering, mneneri Shepherd Bushiri wagawa chimanga ku mawanja okhudzidwa oposa 200… ...
Ngati muli ndi zithuzi zomwe munajambula zakudya zomwe munaphika nokha ndipo zimaoneka mopatsa mudyo, pansi mtedza; kunjaku kuli Crossroads Hotel (Blantyre) yomwe yayaluka kamba kotenga zithuzi za zakudya zophikidwa kwina mkumati zaphikidwa kwawoko. Chatsitsa dzaye… ...
Interns, who conducted phase four of the national identity card registration outreach in Zomba district last year, are planning to storm National Registration Bureau (NRB) district offices over delayed payment of their allowances. Malawi24 understands… ...
It's a new start for four homeless elderly people at Chitakale in Mulanje as a lay movement of the Catholic Church, Community of Sant’Egidio has finally handed over two houses with piped water. 20th April 2024… ...
Gulu la anthu ogwira ntchito zaumoyo omwe sanalembedwebe ntchito, awopseza kuti apitilira ndi ganizo lawo lokasumira unduna wa zaumoyo pa zotsamwitsa zomwe zinachitika pa ndondomeko yolemba anthu ntchito ngati undunawu suwalemba ntchito nsanga. Nkhaniyi inayamba… ...
Tributes continue pouring in for the versatile former Mighty Mukuru Wanderers defender, Kondwani Lifeyo who has died at the age of 31. Lufeyo who was born on 12 November 1992, died on Friday morning, 19th… ...
Pomwe zotsatira za kafukufuku zasonyeza kuti anthu opitilira 15,000 ndi omwe anatenga kachirombo ka HIV chaka chatha chokha, akatswiri ati kugwiritsa ntchito njira zingapo zopewera kutenga kachiromboka, kungathandize kuchepetsa chiwerengerochi. Izi ndi malingana ndi a… ...