Political nomads Uladi Mussa and Brown Mpinganjira have joined the ruling Democratic Progressive Party (DPP).
According to reports, the two will be welcomed into the party on Sunday by President Peter Mutharika at a political rally in Blantyre.
Mpinganjira who served in the Joyce Banda administration as minister took a break from politics a year after the 2014 elections but hinted that he would be available to work with government.
Salima South Parliamentarian Mussa will be rejoining the DPP since he helped found the party and also served as minister during the first term of late Bingu wa Mutharika.
Mussa was earlier this month fired from opposition People’s Party (PP) for claiming that the party was willing to enter into an alliance with the DPP.
Before that, he was PP acting president and vice president for the central region but was removed from the two positions last year after declaring that party founder Joyce Banda’s term as PP leader had expired.
Mbava za anthu kutha kwa nzeru uku mukathera komweko anthu anachangamuka masiku ano sangagomere Nsalu ndi T Shirt old Fashon.
Mmene anayambira ndale muja sakutopa azibambo amenewa, dyera ndi ndalama basi
Kukaonjera kuba ndalama tsopano. Shame on you
i hate politics yakumalawi anali enemy lero ndi friend same old fools and cashgaters they want again money they aint satisfied malawi mavuto ameneo sazatha mwina pabwere bill ija yoti mp akajoina chipani chomwe sanaimire pa ma election azipanga announce dera lake vacant kuti ma election achitikenso may be it can bring sense chifukwa pano akuyendera#follow the leader komwe kuli ndalama ndikumene tikupita …. mtima wa ndyera basi achina change golo ati anuwakeo
Apa zingotsonyezelatu kutu anthu amenewa ndi zitsilu zitselekwete mbuzi agologolo apumbwa
Including atsogoleri achipani alandira makamakape amenewa
Gyz tizachangamuka liti anthu amenewa ndamene akutionongera dzikolathu
Why
Why
Am surprise that you are surprised ‘ what would you expect from these cowards? We voters must just educate one another about politics, these guys are taking us for granted
The country where everyone wants to a politician. Hahaha
Mwanakazi pala nthengwa yamala akwamba uhule nakuyooya viheni vya mwanalume sono uladi tikumzizwa yayi ninkhalo yakhe. Wa dpp chenjelani gulu ili ndilo linoza la cesh gate mungakondwanga na wanthu awa yayi ndiwo wakawiska amamq jb namunyakhe uyu akabisa motorbike ngoniyu . Ine nganga pa dpp kwni uskanimo wankhubgu nga G.C. M.N. U.M. Zoona mkukhala pamoza nawankhungu namweso musambililenge kwiba
Change golo osadabwa tanthauzo mukulidziwa nokha
If you cant act as a child you are not a politician, follows/voters are like empty tins; amangoti auje omwewo kuti wa wa wa!
Awa sikuti alowa Dpp iyayi koma abwelela mu Dpp coz chipanichi anachiyamba okha
Mahule amenewo nainee sindikudabwa
Most welcome
Asauka awa akufuna la solo pano.Ndi omwewanso paja mu 2013 analowa PP nkumuluzitsa JB,nde pano akufuna kuluzitsanso enawa.
sanchez ndi mzake
Mmmmm Uladi? Hiaaaaa! xa!
crazy politicians
Ndakomoka
Old politics
MCP nsanje m’maona ngat wina aliyense adzingojoina razalo wanuyo asà.
Bravo Mr uladi mussa
Onrewa Ndi Makala Osayaka Alibe Chikoka M”madela Akwawo Wima Wasiya NDA
DPP is political of scrape all scrape must go to DDP yes am not bother blz of uladi and BJ it’s scrape people no where to go he has failed
That’s better choice gentlemen, let the foolish blame you but its your choice in Democratic country.
Akuba awa
kkkk kenako mumva mia wapita ku mcp wina mpaka ataziphatu chifukwa cha ndale pali wina wake pfb pa amakhala pa pa nomber 1 kuika comment a meneyo eeee sizimupita
That’s what we call political prostitution
Shitholes
Magamba; mulibemo iliyose
MCP siikuopa zimenezo atsata kolamula chifukwa ndiokhaokha mbava.Chaka cha mawa agwera limodzi.MCP siwanyengerera anthu amenewa,kugwetsakugwetsa. Kutereku a dpp asanyadire kuti apeza ziphona molaro idatha kalekale amenewo. Ochakwera mtima mmalo mavoti tidzaponya ndi ife.
kudya basi
The end
mbava imatsata kumene kuli ndalama
Ine #chingelezi chimandivuta kumvetsetsa, nkhaniyi ikuti Charger cha Phone chatani?
no wonder they are all wounded
Shud read poti alowa not slow
KKKKK I have gone through almost all the contents but mmmmm kkkkk! Shame! Had it been that these guys made a choice of joining MCP eee bwenzi kuli kuchemerera eeeee akatundu eeee what what! Koma poti slows DPP u ur calling them zitsiru asaaa! Recycled politicians hahaaa! What about MIA?
osati mwina akukonda MCP chifukwa chake
A simple conclusion; people are fade up with Selfish DPP Gvt
BJ is sale by past date. Stories are still remembered how BJ manipulated Mlongoti, an MCP candidate for Ndirande by election in 1996. Besides, BJ has a very bad political history. Together with late Dumbo Lemani eish these guys were dangerous. Even Bakili feared him. His time is over. As for Uladi my comments are exhaustive. He doesn’t impress me.
Palibe cha nzeru apa bola bola akadapita mcp
Change Golo sadzatheka
AKUTI IYEYOTU ULADI AKUPANGA NDALE ZA ATCHEYA ANAPHUNZIRA KWA ATCHEYA ZIMENEZO
ULADI HE TRYING TO ESCAPE ARREST
Umphawi watibula akusowa ya sopo
Sin and poverty are the most dangerous things on earth. Look at these poor ministers
Political prostitutes tionana 2019 ma floods aa MCP will wash these rubish! MCP woye!
Ha Ha Ha Ha Ha. Koma guyz u made me laughing
mahule amundale awa
Mr Uladi ndima veteran mu ndale, kulibe komwe angamukane taaaaa, amatiimilira ku Salima yonse bwana mkubwa ameneyi. Kkkkkkkk change golo nanga!!!!!!!
There rolling stones, have nothing to offer to people but looking for money, yes, doing business in politics
Walowanso wokuba makoponiujaineeee !!!!!!! Yaaaaaa
Ameneyo ndiwo madimba a wanthu andale kupita komwe kwanona thumba
A ndalenu musamayese mmalawi ngopusabe ngat mma 1990, tidakutulukirani kt mumangotsata kubisa milandu yanu yakuba kt mupitilize kubanso. Ndani samamudziwa mpinganjira kapena uladi? Anthu okuba, a dziphuphu oyenera Dpp. Ngakhare mubisale MULUNGU yekha sathawika mumfunse yona!
Politics needs people. No matter How nomadic these people are, they wil add value to DPP.
Mmmmmmm komwe alowako achita chisankho chabwino koma musinthe makhalidwe
Mahule amenewo!
Kwavuta welcome brothers
Nomadic kikikikiki these are the people who are failing the country they have nothing to offer to the nation.
just proves that there are no permanent enemies in the inner circle of politics even though fans remain permanent enemies
Nothing can change with those guys….expired people..koma nde kudzadza zitosi ku dpp bwanji.
Nothing can change with those guys….expired people
Chelsea 4 inayo zilooooo
We Wil Kick All Ov You There Manyaka Nokhanokha Inu Sitikuopa Ife, Mcp 2o19 Bomaaaaaa!
ULadi walowa DPP CHIFUKWA CHOZEMBA MURANDU WAPELEKA ZIPHASO MZIKA ZAMAYIKO ENA KUKANA KUMANGIdwa NDALE KU M L W ZOKHAZIKIKA
kkkkkkkk chenji golo waiyionera patali game kulowera kuuna limozi ndi bwampini nose out pompano…. usintha magolo mpka liti uladi
Welcome back Uladi and Mpinganjila
aaaaaaaaaaaaaaaaaa
expired goods
WELCOME BROTHERS
Gold-diggers
Madzi ayamba kutuluka kuno
ANA ACHULUKA UDINDOSO WAKULA NANGA APANGA BWANJI UDI
Birds Of The Same Feathers Flock Together , Mbava Zapitaso Kuchipani Cha Mbava Zokhazokha , If Malawians Will Mistaken By Putting Them In Power They Wil Sweep Al Money .
Mapwefu pwefu party
Yah follow the leader, komwe kuli ndalama ndikomwe tikupita……….
MMMMM koma anthu akenso? Oookey!!!recycled politicians achinyamata tidzukepotu apa otherwise tifikila kukalamba amthuwa akutilamulilabe.this is too much.we need new blood.
koma akanalowa mcp ndiye mukamawayamikira . they are just exercising their freedom of association
Kulowa mcp ndiye kuti amangidwetu’ ali ndimulandutu uladi, mbava yabwelera kuchisa,
Kaya bola alowa, mulanduwo ukuwudziwa ndi iweyo anakalowa mcp analibe mulandu.
Inde mulandu ndikuwudziwa kwambiri alo atati ndikakhale mboni, mulandu opeleka ziphaso za uzika kwa ma burundi,
That’s true nao achakwera anasiya mulungu ndikufuna satana izindiye zosamveka kukana yesu
James! did u say MCP?Aaah ayi MCP is great and only for smart pple
Mr williams jali mukati chakwera anasiya zaumulungu iwe ukamachita machimo umati akakupulumutsa ndi chakwera?motooouwooo
Ndiye ofuna satanawo ndi ambiritu achina pitala muntharika,
Uladi mcp sangailowe kulibe size yake mwina akanakhara zenas
Chipani chakhalamba
?
Mbuzi zimenezo mbava tisesela kumozi
Dpp woyeeeee 2019 bomaaaaa
Political Prostitutes with no values
Bola anonga chipani cha chamba
adya chan pa town…..mwaladilidwabe bc
Recycled politicianz cannot develop this country..unless we see new blood
That’s why nyasalande will NEVER DEVELOP
MCP inalandira Mia,Inu mwalandira Uladi ndi Mpinganjira,aaaa mukuona kwanga sizikusiyana.
MCP inalandira Mia,Inu mwalandira Uladi ndi Mpinganjira,aaaa mukuona kwanga sizikusiyana.
Prostute politicians and greedy nothing shaken my mind with these kind of people,2019 people will speak their mind not by the mind of politicians
Uladi musa real name ,,#change goal ,,,
Paja ndale zili ngati ufiti, zimakanika kungozisiyatu.
Ma prostitute amenewo
Zonvesa chisoni zikuchitkazi mulungu alowelele ndithu. Ndipo ife ovota amatitenga ngati ana oti sitiziwa chilichonse kapena ambuli
Inu ndimakuunzani kuti muhtu wandale ndi mbuzi kupatulako Lucius Banda ndi muthi oziwa ndale dzoko lonse lathuli onsati mbizi zinazi zimasitha ngati mbilimankhwe mutengo wa mango
Akayanjana alekeni
Kodi ndale zathu ndizotani Ku Malawi. Zikuchita kuonekeratu kuti cholinga chathu mkuzilemelesa osati kutukula Dziko. Ndiye tiyeni tidikile tione a MCP ndi nthawi yanu sopano
Wellcome B, Mr Uladi Mussa, Bj Mpinganjira To Chipan Chafuko Dpp Woyeeeeee
Kodi BJ mpinganjira wake ndi uja bakili amkamunena kuti analanda mkazi wamwini? Tandiuzeni amalawi ndi dziwe,
Yes . He is the same BJ who was once implicated in 186 million kwacha during the Muluzi era.
Eee ayi ndiwofunikadi apite ku dpp ndiye kuli azinzake koma zikuwoneka kuti ndiwachimwe-lomwe e,AMEN
Dpp kukhala chipani cha fuko? Aaaa,koma umadzinamiza eti
Aliposo wina!!! muzilowa kuti tikuchoseleni limodzi team,acoach,maprayer munthela limodzi tikazinga mbewu imeneyi isazameleso ndikangoti izabeleka zipaso zabwino koma bola tidula mtengo umenewo ndikuuwocha mphulusa lake tikukaponya nyanja zilowani
End of political career atabwali adzadabwa 2019 ma constituency itapita ku mcp , I ha feeling kuti dpp ukutuluka
Recycled politicians has nothing to offer ….
Anonga ndiamene alowe MCP zachamba anthu odziwa ndale amapita komwe kuli phavu inu mukukangana nokha ndikumati muwina muyiwale
Mkangano opsa uli ku dpp, Chilima camp Nankhumwa camp and Chaponda camp, akufuna mpando wankhalamba ya zaka 81 ija,
WAIWALA MWANA WA MULUZINSO KUTI WALOWA MCP
Political prostitutes you have nothing to offer.
Uladi mussa running away from passport gate.
The Arm of the law will still catch you.
You are just dirtying the image of the DPP as……….
Birds of the same feathers.
#zisiyeniZitsiruIziTizionera,
#zikuloweraKuchionongeko
change golo uyu
Anthuni azibambo amenewa tiwayankhule bwanji kuti apume pa ndale?
Ndidanenapo kale ine kuti tione ndi chipani chopusa chiti chiwalandire, so, it has been revealed, DPP, they will perish together in 2019. Kwacha…! Mmmmmmh.
Mumaonangati angalowe MCP pepani zisakuwaweni
Inu Mmensa Munagulisa Chipan Kwa #Mia, Kuchita Kulamula Kt Ndikufuna Vp, yayayaya Kma Zipan Za Masiyezi Kma Akt Kuli Madeya, Okha okha.
ngat mumadikila kt angalowe k mcp mwangwanayo khoswe ndi mpaka sizikhalila limozi DPP ndimoto
Regardles political prostitution. I don’t c a reason of giving support kwa nkhalamba za ndale izi. Pliz my fellow youth Malawians. Let’s stand up and give them a BIG NO!!!!!
a MCP adafika potikwana ndi ka fisher kachambaka keni kenika kkkk
mcp inatha kale 1994
Uladi mussa ndiye ndani? musatisazitse tangodya kumene nsima,
Mia kungolowa mcp dziko kugwedezekwa why a malawi
Amafunaso kuti alowe nyau party.akanasangalala viva dpp.
AGondwe yankhulani bwino tikakuyankhani muziti aTumbukanu timadana nanu, sindikuyankhani a Gondwe,
MCP SINGAWINE MALOTO ACHUMBA.DPP woyeeeeee!
#Benard, Usamat #Mia, Kulowa Ku Mcp Dziko Kugwedezeka Kma Udziti Mcp Kusokonekela.
Ndi MCP yanuyo bola tisadzawone a #Mia anuyo akudumphamo mu Chipani chanucho monga muja adapangira akubyonthoka ku PP Masankho atayandika.
munthu akalowa mcp a mcp kuomba mmanja kayaso akalowa dpp a dpp onse kusangalala. Zikuonesa kuti sitikuona khalidwe koma alowe chipani chathu paja mkaz amakhala hule ngati sichibwezi chako. Zaka 2000 zapitazo aristotle 384-322 political philosipher wa ku greece yesu asanabadwe anati ndale zinayanja anthu omwe amafuna kuti zonse zikhale zawo, amakwanilisa zofuna zawo ngakhale ena atavutika or kudandaula komatu panthawiyi greece idali mu democracy komaso republic yomwe idayamba ndi solon mu 594 B.C yesu asanabadwe.
NDANENA BOLA NDAKUZANI’ MIA NDIUFULUWAKE, KODI INU ADPP MESA KUNALOWA AMZOMERA NGWIRA? PANGANI ZA MZOMERA MIA MUSIYENI,
Koma nkhalamba party iyi kodi ku dpp kulibe candidate amene alindi zaka chama 50+? nanga mpaka 81 years,
Kutelekutu Uladi akuthawa mlandu wa ma passport. Don’t forget kuti DPP imapanga harbor ma criminals
Inuyu muzizatenga boma2019 popanda mavoti? a dpp sazavota nawo? tilipo tiyeni tiwonane pa 2019 po.
Mwamuyiwala kale #Mia zoti amayidumpha asanafike Masankho ? Musamudalire angadzakukhumudwitseni.
As MCP lovers we are not going to vote 4 human being,,,,but 4 the party because we love the party,,,, kaya tizaluza still more my vote belongz to kwacha!!!
Winawe umwa tameki chaka chake ndichino voterani Kokoliko leroso
Tameki ndi uladi ? azanu app ataya kuti chawola inu adpp mukuti mapeza mtaji, mudzadyanazo mphutsi zimenezi,
broke silly politicianz
broke silly politicianz
DPP IKUGULA MAPULEYA APABECHI ULADI MPINGANJILA ONSEWA ANAYAMBISAPO ZIPANIZAWO KOMA ZINAPITAKUTI ,AGALU AZISIKA KUDPP
Za Mmasiku Otsiriza Izi! Anthu Akukonda Ndalama Kwambiri Kusiyana Ndi Kukonda Anthu Anzawo. Shame On Peter, Chakwera ,uladi And Brown.
Where is Maravi party??? People from salima south watch out I personally like you!!! 🙁 🙁 🙁
Za Mmasiku Otsiriza Izi! Anthu Akukonda Ndalama Kwambiri Kusiyana Ndi Kukonda Anthu Anzawo. Shame On Peter, Chakwera ,uladi And Brown.
STUPID
Recycled politicians
waiwelenga uladi ndi milandu akumuzenga ija
Political nyerere kkkkkkkkkkkk
It’s because of these same stupid people that we are in this mess today.
These guys are foolish,they just need money
Everybody wants money
Akuluwa ndioyamba kukhala pa moyo wanga kuva kuti ndalamasamadzifuna
Kkkkk
These guys are not the real deal ndifans yongotengeka ndiomwe anasokonezanso masten komanso akajoina chipani then those are the signals of the end of days for that party.
Yoooh mpinganjira after being refused in Mozambique to join politics he’s back ,,
mbara za mifut zimenezi akufuna adye ndarama za mu dpp zo akatero athawe
Uladi Stability Nde Mulibe, He Makes Decisions Out Of Frustration. Kuteloko Ka 3 Year Anali Ku Opposition Samamva Bwino. Poor Timing Coz Just A Few Months From Now, Mcp Will Kick Your Butt, 2019 Ur Returning Whr U Belong, The Opposition
Hahaha MCP is dead even Tembo has said so..and MCP u make a good opposition,why change
man mukunamatu apa. let’s wait.
I think its time that young people should take over the political scene in all parties because these recycled politicians will not add any value to whichever party they can join. Mpinganjira comes from Mulanje Central and dont see him unseating the youthful incumbent. All Mpinganjira wants are favours from the DPP….in form of a job or business contracts. Coming to jobs please asiyileni ena nawo adyeko. Akulu akulu ambiriwa adyelela boma kokwanila.
kukwela ya kupwa kumeneku
achange goal tsopano kuli nzake ken nsonda konko
Kkkkkk athu akuyoza sopano .akanolowa kwa ng,ona mbwezi awkuwombera manja. Viva dpp.
Mbava yapita ku mathanyura party
The fail of uladi has come in time
Uladiyu waiwala kuti anathamangisidwa ku DPP konko
I don’t like them both.Why are they so unstable especially Uladi?It clear there is nothing these two can offer.They are not all about the ware fair of Malawians but to filll their pockets.What greedy and selfish politicians!
Hai, which other Facebook pages can I get to be reading current affairs of Malawi on Facebook?
Malawi voice,Nyasa times,Malawi independent, The Maravi post, MBC Malawi,Zodiac Online and Malawian Watchdog are some of them…
Mbava iyi inu
2019 tidzamva kuti alowa MCP
2019 tidzamva kuti alowa MCP
Mahule awa akagwere uko
Mia is loading….70%
Headless chickens
These political gurus are money hungry,they always sway where the honey comb is succulent,originally from MCP,UDF,DPP,PP and back to DPP why not Afford?kkkk unstable politicians ,finally you’ll end up being washed away by these so called floods.
Mmmmmmm ampinganjirawo ndiye ayi zawo zinada kale a Uladiwo ndiye sadalilika
kupepera iya
Change goal nthawi yomweyi 45 minutes zatha? Iwedi zuzatheka ayise eish!!!!
zaziiiii
koma mbala imeneyiso itivutatu.
I like the way you have put it “POLITICAL NOMA’S” I can’t say much it’s for the people who vote to judge the kind of behaviour of these unstable politician’s
Uladi Mussa amangondisangalatsa kut no matter kt ali chpan canj,kma samaluza u MP.Adaimra UDF,DPP,MPP,PP kumangowina.Sndkudziwa ngat pali MP wina amene anakwanitsapo zmenez.He deserves to b the campain director
Ee koma ndiye amakusangalatsanidi
Ine amandimvetsa chisoni anthu aku dera lomwe amawinalo
He is ruling dead people. …there is nothing to smile about
Chenji Golo
Recycled Pliticians, Resdues, A Brown Mpinganjira Anatha Kalekale! Sanza Zokhazokha
Welcome the duo, take a seat feel free. Okwiya akwiye
Ngati dpp ingawalandire anthu ndekuti kulibe anthu a nzeru.Nchiyani chomwe dpp ingapindule kuchoka kwa anthu osokonezawa ???Uladi anachita kuchotsedwa ku dpp komanso pp kusonyeza kuti ndiokanika.
Hahahaha simukunama ndima political nomads
So Mr mpinganjira is still around..?
Timadziwa kale
I didn’t read the story but I think Ronaldo is better than Messi
Nosense
Yea bro.. sanches amugulanso a man u
hazard wagolesa chachiwiriso
You are right and I am even told that heavy rains have washed away the yet to be constructed bridge
kkkk koma guys
BJ ndi ULADI ai koma mia kaya mumati mua sindikusamala ameneyo nde munthu? mia sangamake pa BJ ndi pa chenji golo
Ife sitikondwa naye ameneyi, chifukwa adakhala akunyoza mtsogoleli wa chipani cha DPP pamene amkachemelela mbava yayikazi ija ndi chipani chake cha pp. Ndikanakhala ndinali mwa m’modzi odziwika kuchipaniku ndidakamuwuza kuti chipani chadzaza malo mulibe.
Dpp is now filling its house with self serving politicians. On the other hand,other parties have some new blood though they have been hit by political earthquick…nkhani yake kulimbirana maudindo
Za zii kuteloko awalandila
zovala zada bwanj…
Winayu paja ndi 45 mins change goal ndie kuti yakwana
Tilibe nawonso chidwi palibenso chimene angatiuze ife kuwamvera .Mbava zokhazokha.
mbala zikuopakumangidwa ulad alindimilandu yachinyengo stupid person
Tikudziwa kuti Uladi Mussa akudzela ukazitape mu chipani cha DPP.
Kom chimunthu chimenechi !!!!! The party’s full of puppet indeed.
Kodi kuphika kwa bonya kuti akome mumatani?
Uladi and mpinganjira are politician bitches
ndale ndi za anthu omwe mitu yawo siiganiza za yesu, umunthu adabwerekesa, amafuna za pompo pompo komaso maso ali pa ndalama.Asiyen alowe dpp chifukwa ndi andale pajatu izi si zamulungu. onse omwe akulowa dpp kaya mcp ndiwoti ndi mbava zokhazokha palibe wolungama.
kuti
KKKKK Nzosadabwitsa ndipo nzomwe anthu amaembekezela kumva. Ndiufulu wawo kutero koma bola nawonso alemekeze komwe achokako, coz akhalako ndithu ndiye sindikuona chifukwa chomakwela pachulu nkumanena zawena. Coz amane atsala kuchipaniwo nawonso atha kupezanso zolankhula. Ndiye mwati ampinganjilanso? KKKKKKK okay koma yaah ndale pamalawi kodi zolosela losela zija sizikuenda? Kapena muziphatikiza? Nanga anthu atakufunani kuti mukawanenele inu muli kunsonkhano wandale mungasiye nkukanenela Kaye pamunthuyo? Kkkkkk okay ayi nanunso ndiwanu ufulu koma zakumwamba zimadana nkusakaniza pangani zimodzi akulu
Ukamuuze Kaye Chakwera
zikugwilizana bwanji ndichakwera?
tachiwuza chimbuzi akuti book
Brother mpakiza anthu enatu amangofuna kungofuna kidziwika kuti amaika ma comment pa fb koma kumene kukuliwela nkhani ndizomwe akunena iyeyo mmmm kusiyana bkwakeko, koma ndikudziwa amafuna poyambanilana ndianthu koma ine ayi zimenezo sindifuna. Tiyeni tikambe zomwe zikuchitika munthawi imeneyo
koma kukamba chilungamo chakwela ndindani mesa ndi busa ndiye mukumunena mpinganjila kt watani muyambe mwanena chakela kenaka muzimunena winayo
Mpinganjira wake uja bakili ankati analanda mkazi wamwini? koma kumeneko sitiva kuti nduna yalandidwa mkazi?
Nkhani iyapa ndiya uladi ndi mpinganjila ndiye dzina lachakwera likubwera kumakhala kuleredwera pachilolo .Tinene kuti mbuzi ndizambiri
Mpakiza phiri mbuzi ndiwe,kape mzakoyo akukamba za ubusa ndi ndale,Lazaro nayenso anathawa ubusa nde if you can’t see kuti the stories relate nde kasume kwa chakwerayo
Akulu palibe nkhani yokuti mungakwiye nayo yapa & chomwe mingadziwe ndichakuti apapa ndipochezelapo kapena kupelekapo maganizo, ndipo palibe chomwe mungawinepo ngakhale mutakwiya mwantundu wanji, komanso mosakitsekani xofuna zanu musankhe zomwe mungakwanitse bola kuzimaliza, Mpinganjilayo ndim,bale wako? Ndipo chomwe chakunyasa iweyo ndichani? Ngati kuti Dzina lakwanu yapa? Ngati wapsa mtima upse mtima zeni zeni wamva? Ngati umatha ungonena
No wonder that’s politics tilila nawo anthuwa mpaka kale mulunge yekha akudziwa zonse ife tawalephela
Palibe kusitha kulikonse komwe ndikuonapo apa
Anamasupuni
Anthu awa ngati komwe angayime ngati aphungu ndipo mkuwina zidzangosonyezelatu kuti ku malawi anthu opusa adakalipobe chifukwa si ndi ukuchiwona chowapatsilanso mpando akaligondo amenewa
I cant wait to see Alexis Sanches at Old Trafford wearing jessy number 7 for Manchester United..
ndimaona ngat mukunena anthu enieni ndi anthunso amenewa