Just in: Musician Mwiza Chavura arrested

260

Police in Blantyre have arrested controversial musician Mwiza Chavura.

The musician has been arrested for his song titled ‘Ndidzakupanga rape’ which sparked controversy as rights groups said it promotes sexual abuse of women and children.

Chavula

Arrested

National Police Publicist James Kadadzera has told the local media that Chavura is currently being held at Blantyre Police Station.

Police had been looking for Chavura for over a week following controversy that followed the release of the rape song.

In the controversial song, the musician warns a girl that he will rape her.

Following the release of the song, Family Rights, Elderly and Child Protection (FRECHIP) called on the police to arrest the musician.

FRECHIP said one form of sexual harassment is through rude jokes and suggestive stories hence the call for Chavura’s arrest.

Share.

260 Comments

 1. Zopusa mmalo motimuganizezanjala chilala mukulimbana ndi zopusa amalawi kupepelatuuku kodi oseaimaimbanyimbo zotukwanazi mumalekakuwamanga huuuu kma mm zochitikakumalawi

 2. Where is the freedom of speech now?You failing to arrest the criminals but you are good on arresting the simple innocent man.You are not showing your proffessionalism.My simple advise to you Malawian policemen/women is,let not the politicians control your job.

 3. mmmmm koma guys mpaka amumanga nkhani yake iti? to me the song is just OK only that he has done it in a wrong country which doesn’t appreciate good music

 4. Ndiye amene mumazitsatanu mukuti pamalamulo mulandu umene amumangira mchimwene wathuyu ndichani? Ndipo lamulo limenelo linapangidwa introduced litilo?

 5. Andale Akaba Ndalama Amakhala Akupanga Zitukuko Zawo Komaso Kuti Awamange Ndalamazo Sizingwila Tchito Koma Awa Oyimba Umakhala Mwano Chipomgwe Chomwe Sichingapindulile Wina Ali Yense Olo Dziko Olo Kholo Silivana Ndi Mwana Wa Mwano Athunu Mumadziwa Kanyoza Mpulumuseni Muthuyo Mukanika

 6. Well done apolisi pomutenga n’kuluyu anatimenyera martse mfana wozika kuimba # 1:osati zake ku chikwati !!!! Mkalimbana ndi ine mafana muzatenga tsoka freshmen!!!

 7. Koma apolice aku Malawi mmalo momanga bwava za Zikungoba misonkho yathu kukamanga munthu woti wangoyimba zolakwika ndalamanso wayimbilazinso nzake mmesa nyimboyo it was burned sipanakwane

 8. It took a half a year for the police to arrest chap0nda Chimanga who robbed those women and their broke men even though there was full evidence,And one week to arrest a ghetto youth who was just singing.kabungwe kameneka kangofuna kutchuka

 9. Ndikunena pano nyimbo yanga atamalidza kundiopyeza anaibana ku radio one ndi ma radio ena zopusa basi .ineyo ndakodzeka andiphe sindiopaso ai nditulusaso ina popano khawa njeeeeee

 10. Ineso ndine oimba anandiopyezaso nditatulusa nyimbo yanga ya yoswa .ndizisiru zawathu samafuna chilungamo ai paribepo khani apa amusiye osafuna kuimvera nyimboyo idzo ndizake zopusa basi

 11. I hate to b a Malawia, komwe amabungwe ake ndi an2 opusa amasiya Kambuku akuyendayenda kusakaza the wellbeing of innocents Malawians kumalimbana ndi nyerere chifukwa yakwera. pa bread. shame on u!!

 12. Why are law enforcers,always keen with petty issues,the muzik is circulating in corners of Malawi,in desk tops,lap tops and even phones,there are other cases which died natural death,like Issah Njauju,Robert Chasowa just to mention a few,nothing has proved futile,nkhani zikakhala zawamba ndiye kumango thokota pamedia,kkkk.

 13. Koma akanaimba zothamanda aPeter akulu apolisi mphuno ngati mwalowa nyelele ,mukufuna Joseph Mkasa akati Yoswa ndiye president anuwo kusangalala ,monkeys police anyani apolisi makamaka Table Spoon

 14. i think the best way is just to ban the song and not necessarily arresting the guy

  plz… plz…. our police, you have alot to do magalimoto akupatsani ma china-wa agwiritseni ntchito moyenera for the betterment of ours

 15. Malawi police arrest these people and put them under house arrest for their cases to be hurried up tione pomwe zathera akagwire ya kalavula gaga.1 Bakili Muluzi,2 George Chaponda

 16. Onse opanda umunthu kumawamanga. Enawa alibe azimai kwao,koma akazayamba kubeleka ana akazi ndiku citilidwa nkhanza azayamba kuzindikila

 17. Ngati anapepesa palibe nkhani yommangira akanangonena tamugwira and tampanga desclipline sadzapanganso kwaonse amalawi omwe nyimboyi inakhudzani pepani basi nkhani yatha tiyeni apolisi kupatula kufuna kusangalatsa munthu kapena malamulo umunthu ndi chikondi zikhale patsogolo pathu nthawi zomwe tidzakhala ndi malawi wabwino kwambiri

 18. Izi zandinyasa zedi bwanji si munamumange chaponda umenewo ndi ugalu anyapapi inu mutuluseni walakwa chani mwinza uchitsilu basi asa panupo mwapanga izi

 19. Kkkk muziko mukabwera chitukuko timatama presdnt apaso chavura wamangidwa tizit wamumanga ndi pitala but y nt chadyaka malawiiiii y mabungweso uhv nonses yes nonses there is alot of burning isue across the country but y cling to this small isue

 20. apolis asowa ntchito zogwira kumalawi,tawapezelan chochita ngt mmene mukuwachitira asilikali ku drc,chommangila chavula ndichan?kalipo sinyimboi ai,mabungweso akumalawi,mot mwapeza chogwira,panyimbo yachavula,mukulephera kutumphula zambava kt zimangidwe,mulimbana ndphawi,nanga mahule akunyengedwa mwachisawawa,kumaenda atavula kale musawamanga bwa?musiyen mwanayo

 21. Koma a polisi kkkk mh kungofuna potchukira eti?? Kuli nyimbo zambiri zopusa koma aaaa can’t believe it… Arresting??? I don’t like any of chavula songs but mmmm kumaona zinazi

 22. The best way was kumdzudzula publicly osati kumumanga that is useless General Kanene anamangidwapo ndi nyimbo zake zotukwana zija? Or he was just supposed to be banned? Condem his song publicly not arresting him coz we r not in Colonial rule treat him in good way

 23. as a member from comment readers association wordwide am humbly give thanks to you all for short comments i’ve manage to read all one after another

 24. I think Malawi police are always stupid in tackling matters , the guy has a rights and freedom as the country claims. It is only if one has violeted the law and abusing someone then you can arrest him/ her. Now on what offence does this guy committed? And against who? Does his song mentioned someone’s name? I blame Malawi police are very naive and stupid in handling matters and leaving big issues. STUPID MALAWI POLISI SERVISES.

 25. That’s what I like with Malawi police. If you say go they go in full force but ignoring big crime committed by big fish. If the song is bad why not ban it. But choose to show security whereby some are running free with big crime like Chaponda. Ndende ndiya amphawi

 26. Palibe nkhani apa. Why arresting him. The boy has not done anything wrong to warrant an arrest.
  Why are you not arresting anthu akuba ambirimbiriwa.

 27. Ndine munthu m’modzi wokhumudwa chifukwa cha m’khalidwe wotengera munthu wamkazi kumtengo ngati njoka yakufa .Moti ndipemphe ku anthu odziwa malamulo kuti uyuyu chigawenga uyu mutamupatsa chilango chokwanira kuti ngati alipo ena amzeru ngati zakazi alekeletu

  • Munthu opusa opanda mzeru chitselekwete Mbatama mburi yomwa madzi ometera ndi yomwe imamuwona munthu wa mkazi ngati opanda pake monga uliri iweyo okubalani akanangotsamira muli akhanda olo akangochotsa mimba yako amai ako sipakanalakwika adabeleka chidzete

 28. Why wasting time with small things? There is so many big fish in the lake so why catching this small fish? Ngaunju , chasowa and etc anaphedwa but no arrest, chimanga chinabedwa . Pliz do the right thing at the right time.

 29. Police authorities have done well for arresting Chavura as well a long his song is full of nonsense that hurt the whole Malawian citizens especially those are borne with humanity and discipline in mind…..Nobody will appreciate this stupid massage of satan@ GUIZ Chavura he doesn’t know how to compose and sing the songs so i think this is a right time he must leave it to those with merit to dedeserve it or other wise he has to join politics because in politics now a days every bad act that one does is legal

  • you see how stupid you are!! M’mwe unetu jwangatenda gele manyigo get lost you creep!! and never mind how you related to that Guy Chavura so don’t become hostile to me so if you are amongst those his coworkers please I warn you stop urging others kupanga zinthu zoputsa like of that your friend has done…… kkk don’t put blame on me because I am here just contributing my views so if you got a point clearly never hold grudges against me wamva ukapange claim ku court

 30. We Have No Police In Malawi But Political Police That Arrested Poor People That Stole Chickens And Ducks And Leave Free People Who Have Stolen Our Billions Malawi Poor Taxes.Oh Shame On U Our Dogs.

 31. Kumanga oyankhura kusiya Ochita, iye ndi mau okha okha ndipo sanapange kanthu mwamumanga pomwe wina wabela ndikudzunza mizimu ya asauka koma ali mwa ufuna, mulandu waung’ono nde kuonesa chamuna mbudzi za anthu……

 32. komaa a police ndi mabungwe moti mugwire anthu omwe anasowetsa mzimu wa ROBATI CHASOWA ndiku manga athu oba chimanga koma thukuta komukamu kumanga anthu oyimba ndi mavenda ogulitsa nsima ku city center choncho Mulungu angadalitse dziko lino

 33. Zodandaulitsa kwambiri, komabe Mwiza angolumikizana ndi lawyer uja adadzipereka zomuimirira kuti achite manyazi madyabulosi amenewa… Mmmmmmh.

  • There us real criminal out side there walking freely but kumanga Chavura kunali kungomuyakhura not mpaka arrest him mangani akuzunza anthuwo kuononga chuma cha Boma zindalama za khanikhani kupezeka nyumba pomwe ma civil servants not get paid in time, mankhwala kusowa nzipatala but he is walking freely in this planet shame.

 34. komaa a police ndi mabungwe moti mugwire anthu omwe anasowetsa mzimu wa ROBATI CHASOWA ndiku manga athu oba chimanga koma thukuta komukamu kumanga anthu oyimba ndi mavenda ogulitsa nsima ku city center choncho Mulungu angadalitse dziko lino

 35. I see some stupid comments from people here trying to defend him, what kind of people are u? The message in his song is very upsetting.One day your sister or child might be raped, tell me if also u can praise the rapist?

 36. Malawians we just know how to comment pa fb basis. if we ain’t happy about show physical action kuonetsa kuti zatinyasa eg kupanga mademo basi. wakupolice komko to free chavula and present our grievances pamilandu yaserious yonwe ikuwolayo rather than kumangotokota APA basi

 37. mkona a malawi stdzalemera kukanika kumanga anthu anapha isa njauju,joyce banda,bakiri muluzi,chapondah etc anthu ot anaba ndalama zankhaninkhani nkukamanga munthu ot wangoimba nyimbo?grow up malawi!where are u headng to?

 38. Ugalu uchitsilu he did mistake en he admit for that and apologized for the mistake he made.He is a human
  While mukulimbana ndivuto laling’ono kusiya lalikulu uja Kape anaba za chimanga uja Chaponda.Kukalimbana mzauchitsilu za kape wachabechabe.
  Mbuzi za atsogoleri kmamso Mbuzi za a Police forsake

 39. Amayi mukuwalephelatu koma zukomele anthu osauka anthu aba ma thiliyoni for nothing koma uyo mwat mumukamate which means osaukafe tilibe gawo basi

 40. Akukanika kumanga akuba ndalama za boma uyu NDE amuonera chani asowe ngati chasowa ife achinyamata mukutionerera mdziko lino why Malawi Nyimbo ikhale omangira munthu shame on you