Uladi, Mpinganjira join DPP

Uladi Mussa

Political nomads Uladi Mussa and Brown Mpinganjira have joined the ruling Democratic Progressive Party (DPP).

According to reports, the two will be welcomed into the party on Sunday by President Peter Mutharika at a political rally in Blantyre.

Uladi has joined DPP.

Mpinganjira who served in the Joyce Banda administration as minister took a break from politics a year after the 2014 elections but hinted that he would be available to work with government.

Salima South Parliamentarian Mussa will be rejoining the DPP since he helped found the party and also served as minister during the first term of late Bingu wa Mutharika.

Mussa was earlier this month fired from opposition People’s Party (PP) for claiming that the party was willing to enter into an alliance with the DPP.

Before that, he was PP acting president and vice president for the central region but was removed from the two positions last year after declaring that party founder Joyce Banda’s term as PP leader had expired.

Advertisement

234 Comments

 1. Mbava za anthu kutha kwa nzeru uku mukathera komweko anthu anachangamuka masiku ano sangagomere Nsalu ndi T Shirt old Fashon.

 2. i hate politics yakumalawi anali enemy lero ndi friend same old fools and cashgaters they want again money they aint satisfied malawi mavuto ameneo sazatha mwina pabwere bill ija yoti mp akajoina chipani chomwe sanaimire pa ma election azipanga announce dera lake vacant kuti ma election achitikenso may be it can bring sense chifukwa pano akuyendera#follow the leader komwe kuli ndalama ndikumene tikupita …. mtima wa ndyera basi achina change golo ati anuwakeo

 3. Apa zingotsonyezelatu kutu anthu amenewa ndi zitsilu zitselekwete mbuzi agologolo apumbwa
  Including atsogoleri achipani alandira makamakape amenewa
  Gyz tizachangamuka liti anthu amenewa ndamene akutionongera dzikolathu
  Why
  Why

 4. Am surprise that you are surprised ‘ what would you expect from these cowards? We voters must just educate one another about politics, these guys are taking us for granted

 5. Mwanakazi pala nthengwa yamala akwamba uhule nakuyooya viheni vya mwanalume sono uladi tikumzizwa yayi ninkhalo yakhe. Wa dpp chenjelani gulu ili ndilo linoza la cesh gate mungakondwanga na wanthu awa yayi ndiwo wakawiska amamq jb namunyakhe uyu akabisa motorbike ngoniyu . Ine nganga pa dpp kwni uskanimo wankhubgu nga G.C. M.N. U.M. Zoona mkukhala pamoza nawankhungu namweso musambililenge kwiba

 6. If you cant act as a child you are not a politician, follows/voters are like empty tins; amangoti auje omwewo kuti wa wa wa!

 7. MCP nsanje m’maona ngat wina aliyense adzingojoina razalo wanuyo asà.

 8. kkkk kenako mumva mia wapita ku mcp wina mpaka ataziphatu chifukwa cha ndale pali wina wake pfb pa amakhala pa pa nomber 1 kuika comment a meneyo eeee sizimupita

 9. MCP siikuopa zimenezo atsata kolamula chifukwa ndiokhaokha mbava.Chaka cha mawa agwera limodzi.MCP siwanyengerera anthu amenewa,kugwetsakugwetsa. Kutereku a dpp asanyadire kuti apeza ziphona molaro idatha kalekale amenewo. Ochakwera mtima mmalo mavoti tidzaponya ndi ife.

 10. KKKKK I have gone through almost all the contents but mmmmm kkkkk! Shame! Had it been that these guys made a choice of joining MCP eee bwenzi kuli kuchemerera eeeee akatundu eeee what what! Koma poti slows DPP u ur calling them zitsiru asaaa! Recycled politicians hahaaa! What about MIA?

 11. BJ is sale by past date. Stories are still remembered how BJ manipulated Mlongoti, an MCP candidate for Ndirande by election in 1996. Besides, BJ has a very bad political history. Together with late Dumbo Lemani eish these guys were dangerous. Even Bakili feared him. His time is over. As for Uladi my comments are exhaustive. He doesn’t impress me.

 12. A ndalenu musamayese mmalawi ngopusabe ngat mma 1990, tidakutulukirani kt mumangotsata kubisa milandu yanu yakuba kt mupitilize kubanso. Ndani samamudziwa mpinganjira kapena uladi? Anthu okuba, a dziphuphu oyenera Dpp. Ngakhare mubisale MULUNGU yekha sathawika mumfunse yona!

 13. Birds Of The Same Feathers Flock Together , Mbava Zapitaso Kuchipani Cha Mbava Zokhazokha , If Malawians Will Mistaken By Putting Them In Power They Wil Sweep Al Money .

 14. MMMMM koma anthu akenso? Oookey!!!recycled politicians achinyamata tidzukepotu apa otherwise tifikila kukalamba amthuwa akutilamulilabe.this is too much.we need new blood.

 15. Zonvesa chisoni zikuchitkazi mulungu alowelele ndithu. Ndipo ife ovota amatitenga ngati ana oti sitiziwa chilichonse kapena ambuli

 16. Inu ndimakuunzani kuti muhtu wandale ndi mbuzi kupatulako Lucius Banda ndi muthi oziwa ndale dzoko lonse lathuli onsati mbizi zinazi zimasitha ngati mbilimankhwe mutengo wa mango

 17. Kodi ndale zathu ndizotani Ku Malawi. Zikuchita kuonekeratu kuti cholinga chathu mkuzilemelesa osati kutukula Dziko. Ndiye tiyeni tidikile tione a MCP ndi nthawi yanu sopano

 18. Aliposo wina!!! muzilowa kuti tikuchoseleni limodzi team,acoach,maprayer munthela limodzi tikazinga mbewu imeneyi isazameleso ndikangoti izabeleka zipaso zabwino koma bola tidula mtengo umenewo ndikuuwocha mphulusa lake tikukaponya nyanja zilowani

  1. End of political career atabwali adzadabwa 2019 ma constituency itapita ku mcp , I ha feeling kuti dpp ukutuluka

 19. Anonga ndiamene alowe MCP zachamba anthu odziwa ndale amapita komwe kuli phavu inu mukukangana nokha ndikumati muwina muyiwale

 20. Political prostitutes you have nothing to offer.
  Uladi mussa running away from passport gate.
  The Arm of the law will still catch you.
  You are just dirtying the image of the DPP as……….
  Birds of the same feathers.

 21. Ndidanenapo kale ine kuti tione ndi chipani chopusa chiti chiwalandire, so, it has been revealed, DPP, they will perish together in 2019. Kwacha…! Mmmmmmh.

  1. Regardles political prostitution. I don’t c a reason of giving support kwa nkhalamba za ndale izi. Pliz my fellow youth Malawians. Let’s stand up and give them a BIG NO!!!!!

  2. Ndi MCP yanuyo bola tisadzawone a #Mia anuyo akudumphamo mu Chipani chanucho monga muja adapangira akubyonthoka ku PP Masankho atayandika.

  3. munthu akalowa mcp a mcp kuomba mmanja kayaso akalowa dpp a dpp onse kusangalala. Zikuonesa kuti sitikuona khalidwe koma alowe chipani chathu paja mkaz amakhala hule ngati sichibwezi chako. Zaka 2000 zapitazo aristotle 384-322 political philosipher wa ku greece yesu asanabadwe anati ndale zinayanja anthu omwe amafuna kuti zonse zikhale zawo, amakwanilisa zofuna zawo ngakhale ena atavutika or kudandaula komatu panthawiyi greece idali mu democracy komaso republic yomwe idayamba ndi solon mu 594 B.C yesu asanabadwe.

  4. As MCP lovers we are not going to vote 4 human being,,,,but 4 the party because we love the party,,,, kaya tizaluza still more my vote belongz to kwacha!!!

 22. Za Mmasiku Otsiriza Izi! Anthu Akukonda Ndalama Kwambiri Kusiyana Ndi Kukonda Anthu Anzawo. Shame On Peter, Chakwera ,uladi And Brown.

 23. Za Mmasiku Otsiriza Izi! Anthu Akukonda Ndalama Kwambiri Kusiyana Ndi Kukonda Anthu Anzawo. Shame On Peter, Chakwera ,uladi And Brown.

 24. These guys are not the real deal ndifans yongotengeka ndiomwe anasokonezanso masten komanso akajoina chipani then those are the signals of the end of days for that party.

 25. Uladi Stability Nde Mulibe, He Makes Decisions Out Of Frustration. Kuteloko Ka 3 Year Anali Ku Opposition Samamva Bwino. Poor Timing Coz Just A Few Months From Now, Mcp Will Kick Your Butt, 2019 Ur Returning Whr U Belong, The Opposition

 26. I think its time that young people should take over the political scene in all parties because these recycled politicians will not add any value to whichever party they can join. Mpinganjira comes from Mulanje Central and dont see him unseating the youthful incumbent. All Mpinganjira wants are favours from the DPP….in form of a job or business contracts. Coming to jobs please asiyileni ena nawo adyeko. Akulu akulu ambiriwa adyelela boma kokwanila.

 27. I don’t like them both.Why are they so unstable especially Uladi?It clear there is nothing these two can offer.They are not all about the ware fair of Malawians but to filll their pockets.What greedy and selfish politicians!

 28. These political gurus are money hungry,they always sway where the honey comb is succulent,originally from MCP,UDF,DPP,PP and back to DPP why not Afford?kkkk unstable politicians ,finally you’ll end up being washed away by these so called floods.

 29. I like the way you have put it “POLITICAL NOMA’S” I can’t say much it’s for the people who vote to judge the kind of behaviour of these unstable politician’s

 30. Uladi Mussa amangondisangalatsa kut no matter kt ali chpan canj,kma samaluza u MP.Adaimra UDF,DPP,MPP,PP kumangowina.Sndkudziwa ngat pali MP wina amene anakwanitsapo zmenez.He deserves to b the campain director

 31. Ngati dpp ingawalandire anthu ndekuti kulibe anthu a nzeru.Nchiyani chomwe dpp ingapindule kuchoka kwa anthu osokonezawa ???Uladi anachita kuchotsedwa ku dpp komanso pp kusonyeza kuti ndiokanika.

 32. Ife sitikondwa naye ameneyi, chifukwa adakhala akunyoza mtsogoleli wa chipani cha DPP pamene amkachemelela mbava yayikazi ija ndi chipani chake cha pp. Ndikanakhala ndinali mwa m’modzi odziwika kuchipaniku ndidakamuwuza kuti chipani chadzaza malo mulibe.

 33. Dpp is now filling its house with self serving politicians. On the other hand,other parties have some new blood though they have been hit by political earthquick…nkhani yake kulimbirana maudindo

 34. ndale ndi za anthu omwe mitu yawo siiganiza za yesu, umunthu adabwerekesa, amafuna za pompo pompo komaso maso ali pa ndalama.Asiyen alowe dpp chifukwa ndi andale pajatu izi si zamulungu. onse omwe akulowa dpp kaya mcp ndiwoti ndi mbava zokhazokha palibe wolungama.

 35. KKKKK Nzosadabwitsa ndipo nzomwe anthu amaembekezela kumva. Ndiufulu wawo kutero koma bola nawonso alemekeze komwe achokako, coz akhalako ndithu ndiye sindikuona chifukwa chomakwela pachulu nkumanena zawena. Coz amane atsala kuchipaniwo nawonso atha kupezanso zolankhula. Ndiye mwati ampinganjilanso? KKKKKKK okay koma yaah ndale pamalawi kodi zolosela losela zija sizikuenda? Kapena muziphatikiza? Nanga anthu atakufunani kuti mukawanenele inu muli kunsonkhano wandale mungasiye nkukanenela Kaye pamunthuyo? Kkkkkk okay ayi nanunso ndiwanu ufulu koma zakumwamba zimadana nkusakaniza pangani zimodzi akulu

  1. Brother mpakiza anthu enatu amangofuna kungofuna kidziwika kuti amaika ma comment pa fb koma kumene kukuliwela nkhani ndizomwe akunena iyeyo mmmm kusiyana bkwakeko, koma ndikudziwa amafuna poyambanilana ndianthu koma ine ayi zimenezo sindifuna. Tiyeni tikambe zomwe zikuchitika munthawi imeneyo

  2. koma kukamba chilungamo chakwela ndindani mesa ndi busa ndiye mukumunena mpinganjila kt watani muyambe mwanena chakela kenaka muzimunena winayo

  3. Nkhani iyapa ndiya uladi ndi mpinganjila ndiye dzina lachakwera likubwera kumakhala kuleredwera pachilolo .Tinene kuti mbuzi ndizambiri

  4. Mpakiza phiri mbuzi ndiwe,kape mzakoyo akukamba za ubusa ndi ndale,Lazaro nayenso anathawa ubusa nde if you can’t see kuti the stories relate nde kasume kwa chakwerayo

  5. Akulu palibe nkhani yokuti mungakwiye nayo yapa & chomwe mingadziwe ndichakuti apapa ndipochezelapo kapena kupelekapo maganizo, ndipo palibe chomwe mungawinepo ngakhale mutakwiya mwantundu wanji, komanso mosakitsekani xofuna zanu musankhe zomwe mungakwanitse bola kuzimaliza, Mpinganjilayo ndim,bale wako? Ndipo chomwe chakunyasa iweyo ndichani? Ngati kuti Dzina lakwanu yapa? Ngati wapsa mtima upse mtima zeni zeni wamva? Ngati umatha ungonena

 36. Anthu awa ngati komwe angayime ngati aphungu ndipo mkuwina zidzangosonyezelatu kuti ku malawi anthu opusa adakalipobe chifukwa si ndi ukuchiwona chowapatsilanso mpando akaligondo amenewa

Comments are closed.