Lawaluma lamulo ndipo lawasiyila chilema chachikulu chokuti ngakhale a chipatala sangathe kukonza. Ndipo inu nonse okonda kuchitila nkhanza ena, bisalani patali chifukwa mawa mutha kukhala inu.
Amayi atatu a ku Lilongwe amene anagwila mmayi mzawo ndi kumusunga momukakamiza ndi cholinga chofuna kumuchita nkhanza, agamulidwa kuti akasewenze ku jele kwa zaka zisanu ndi chimodzi.
Amayiwa amene amachokela ku dera la Area 25 ku Lilongwe, ati anagwila mmayi mzawoyi chifukwa amafalitsa nkhani yoti mmodzi mwa atatuwa ali ndi kachilombo ka HIV.
Iwo ati pokwiya anamutenga ndi kumutsekela m’nyumba ndi kumuchita nkhanza kuphatikizapo kumumenya, kumukodzela ndi kumuvula. Pochita izi iwo adali akujambula.
Atafika pa bwalo, mkulu oweruza wawagamula kuti apite ku ndende akasewenze kwa zaka zisanu ndi chimodzi.
Amayi atatuwa ndi a Thokozani Msiska a mmudzi mwa Enukweni, Mfumu yaikulu Mtwalo mu boma la Mzimba. Palinso a Zelifa Phiri ochokela mmudzi mwa Setha, Mfumu yaikulu Zulu ku Mchinji. Omaliza ndi a Rodness Chose ochokela mmudzi mwa Gonthi, Mfumu yaikulu Kamenyagwaza mu boma la Dedza.
zithu ngat izi ndizovesa cisoni ndipo mwin azimayi ena atenger phuzi koma izi zikacitikaso osawanyengelera kuwapasa cilango athu atengere phuzi
Mmmmmm acita bho athu mwin tisiye zover azathu azimayi ena ndiopusa satha kufusa mwina muthuyo mwina muthuyo amabwala oh awapase cilango cacikulu mwina asazapangeso azmayi
Nanga mamunayo amutani?
mmmm Mathew
Ndiposo zakazo zachepa
Apa nde azimuna ao anyenge momasuka iyaa ndili ine singakangamuone ataa!! ku prisonko.
Tizingowaloza,poti umfiti kulibe Ku police,nanga tikawamenya atimanga,NDE azimayi tipeze mankwala owapotoza mapazi bola osajambula powalozapo
Guys Mukufuna Azimay Gati Amenewa Anole Mano Ndiamuna Aeni Zaka Zachuluka
Gud judgement akonza sadyeka wadyeka apa amazitenga mashasha kuyalutsa mai mzawo,
come on please! Iam here enjoying reading your comments!You are entertaining me! I need more pliz!
Zaka zachuluka guys, Nkhani yake yochepayi… Mukulephera kumanga nduma zaboma zikungoba ndalama zamisonkho ya aphawi…. Agalu inu mukapsa moto kumwamba nonse ama Court…
Koma Ngati Zili Nsanje Nde Zawavulaza
A big lesson to all Malawians as citizens let’s improve our moral value’s who have completely dilapidated mawa ndine
chigamulo chachepa anakawa nyonga ndinakasangalala zozuzana kuno ayi siku sudan kuno shirt
Zachepe zakazo
Mkaziyotu koma afendithu kuti azimayi oyendayendawa atengelepo phumzilo
achita bwino
A court aiwalapo chipepeso cha mkazi ochitidwa nkhanzayu,akuyenera kukalowa chokolo basi
koma azimayi anayerekedwa awa. Amvekere ‘tamajambulani azikaoneka bwino’. Apeza atakwatira azimunawo.
Ndi zochititsa manyazi zimenezo.
Chilango chachepa mmmm 6 yrs yokha
NDIYE ABAMBOWO AKWATIRA HULELOTU
Zachepa zakazo chifukwa kunali kupha kumeneko
zaka zachepa……azimai oipa mitima
Zachepa zakazo. Osawapatsa 14 bwanji? Anamuzunza mzawo.moyipa kwambiri.
Alakwitsa vuto ndi mamuna chifukwa nkazi ndiofusilidwa
Zikanakhala 15
Zoona
kkkkkkkk angomusiya chimecho ndiye chikondi
Good for them.
Azikakodzera kumeneko
Zachepa zikhale 20 zachimanga zija ayi koma. kuziwa kugamula zausiruzi. Zamahure no 1
Zedi-zedi maba titha kukhala ife
Chigamulo chimenechi chilimbikitsa atsikana kuti asamakane amuna oti ali ndi banja lawo kale, chonsecho akudziwa kuti munthu akundifunsirayu ali ndi nkazi wake. Acourt unikani bwino pamenepo
Mmm Lamulo lili bwino ndipo atsikana siwolakha wolakwa ndiwofusila chosecho ali ndinkazi,nkazi ndiye wofusilidwa
Cecilia this case ndiyomunena Thoko kuti amamwa MA ARV komano that case you saying ndiya ku 24 sinagamulidwei
aweluzidwa pazomwe adamuchitira mzawo pomuvula ndikumukodzera wosati kuti amayenda/kunyengana ndi mwamuna wandani? zakukhuzani poti ndi azimai anzanu koma akadakhala kuti achita izi ndi amuna mukadalalata. Mutengerepo phunziro
Mlanduwu ndioti eti amafaritsa nkhani yoti aThoko ali ndi kachirombo osati amayenda ndi mwamuna wa mwini ayi.
Kkkkk amafuna tosabeleka ka
Zaka zonsezo????
Poti alibe Mau Osawuka
Chaponda alipheee atapha anthu ndinjala
Not good, forgive them, they don’t know what they ar doing.
akulekeranji kukhululukidwa anthu wosalakwa akungidwa mundende zadziko lino? pali akazi anu/bwenzi lako? wosadanda uzimuyendera kundende konko
Mmene timarakwitsira anthu ife bwanji mulungu satirangiratu pompo koma azimai awa sanamve kupepesa kwamzawo kuranga okha mosamva chisoni eish satero
anyway bola apezeka olakwa
Awatu akhale ma germs azimai kodi iwowa salakwa bwanji osamvako kupepesa kwamzawo uja ndiye chabwino banjalo likomanso pamenepa zaka zachepa mwina akarandile yesu konko komanso akathandizenso ntchito za boma antchito ngochepa
Mmmm zakozo zachulukitsa,sanaphe munthu azimayiwa,ogamulayo aganizirenso bwino za chilangocho,3-6 months cud be better,apapa mulimbikitsa ziwerewere ndi kusakhulupirika kwa azibambo to their wives.
Wa chibwezi ndi nkhani yaku 24 iyi ndi yaku 25 ati anawanena kut amamwa ma ARV
Kulimbikisa zibwenzi in what way?
Zoonadi
kodi ya ku 24 ili pati anawamanga kodi
Aaaa ndi abale ako eti ndi akhaulatu amachitira dala akhaula akaolera komweko
Alimbikitsa ziwerewere nde kuti chani ukuganiza azimunawo sankanyenga or alipo amunawo ali ndi zibwenzi atenga zibwenzizo akaziwonso anali ma hule otha ntchito
Zakazo Zachepa Zikadakhala 12 They are Floosh Wimen Aziona Makape!
Zanziii ndiposo ndizofoila zokondera bwanji sanamugale George chaponda uja ndiye mukuwagamula azimawo chifukwa chot alibe ndalama shatapu
Ohhh!!!george adakozeranso munthu kkkkkkkk
Kkkkkkkkkkk Ameneyu ndioyipa kwambiri anzake onse tikusangala ndi judgment iye nkumati za Ziii shaaa
iweyo ukuganiza kut chaponda uja ndi azimai amenewo anapweteka athu ambiri ndindani oky sopano issue ya chaponda ija bwanji sanamangidwe koma iweyo takayesa ukabe nandolo tione ngat sukalowa ku ndende
komabe ndizosiyana man bola akanakamba issue yofanana ndiyachaponda think of your mother achitilidwa zinthu zochitisa manyaz ngat imeneyi mmmmmmm akagwilebe jele amenewo
komabe ndizosiyana man bola akanakamba issue yofanana ndiyachaponda think of your mother achitilidwa zinthu zochitisa manyaz ngat imeneyi mmmmmmm akagwilebe jele amenewo
zacepa ofunika kuonjezer nzakaz
mmmm choka
Mayazi asamajaile
Awachita bwino, nanga nsanjeyo kuchita kukhala ngati kuti mamunayo anabereka okha?
Wa chibwezi ndi nkhani yaku 24 iyi ndi yaku 25 ati anawanena kut amamwa ma ARV
Good akaseve basi azikalowetsano dzala mix nyele
Good
yaaaaaa komaaa tinkhan tinat mumaxiwaa kuthana nato komaa kut pangan zitukuko kurephela magetsi dairy kuzmaa koma chosecho mumatirandaa misonkho
shit happens in life ka 6 years nkambiri bora osazapeza azimunanu akwatira shame all the best to the other side ati its more like hell
Awachita bwino ndipo mwamunayo akungoyenera kumutenga mkazi wozunzidwayo basi
kkkkkkkkkkkkkk. Komaditu can be a good decision
Wa chibwezi ndi nkhani yaku 24 iyi ndi yaku 25 ati anawanena kut amamwa ma ARV.
Wakodzela pamwendo, Mkati, Pantchafu kapena Mkamwa, Kkkkk. It’s not boh.
u dream and ua rich u wake up everything is gone…..u dream and urinate in the dream it comes to reality. people why is it so?
Remember w r living in the world filled wth negativities,negativity is easly achieved than positivity.kkk
Do you believe there is an herbal doctor who cures HIV? I was HIV positive for 9 years and taking ARVS until I was cured completely by Dr Tiam. His herbal medicine is very powerful and reliable you can get him on call or WhatsApp: +2348037284837
Apa ma MG 2 athu aziyenda momasuka!
Kodi ena aja nanga zikuti bwanji ???
Zikundimvekera bwino kwambiri
kkkkkkkk kma inu
Pakufunika Kukawaponya Mu Ndende Za Amuna Akaone Kiyama Akakumane Ndiwamibulu Kkkk!
Moyo woipa opanda chikondi. Akaphunzire moyo wa chikondi ndipo ena atengerepo phunziro ndathokoza zikomo akhothi.
ndangowamvera chison a rodnes chisale wo coz amandisanjitsa ndikapwa. koma apita ndi dollar zanga zomwe ndinawakonzera magetsi
Aaaaaa! Chirango chaphweka ichi akanati 15yrs coz komwe anapanga apa ndikupha. kukozera munthu mkamwa mix mkozo wake ula ophatikizana ndi #PERIOD zauve apa chirango chafewa. #ZANDINYASA.
Yeah aziwona kumenya mpaka kukozela nkamwa kuzula sisi lammutu iiiiii
Awachepesela zaka
Happy mwawachita bwino fiti
Mkodzowo amkaleka kukawapatsa amanoma wathelatu akanalandira kanganyasetu m’malo mokalowa cel kaya zofuna Amai
In the US when a traffic officer stops you and you put your hands in your pocket he shoots you instantly..
In my country when a traffic officer stops you and you put your hands in your pockets he starts to smile.
Guess which country I come from….
Kkkk too difficult
None of
Kikkkk, no other than NYASALAND
#Zambia
kkkk i gues ur 4m d nucler weapon state ie vetenam
kkkkk,u people u ar very funny
Iraq bua!?
Kkkkkkkkkkk u ve made my day
Ku usa kulibe dzina lakut Kalikokha. kkk
Malawi
Nigeria
nsanjle o united states of mulanje
United states of thyolo kkkk
Ndi Mft Zmenezo Zaka 6 Zachepa Akatuluka Azingopha Sopano
zaka 6, ?..which is equivalent to 3 years, ___ bola aka severtu boh boh, tisamve kut wina wamwalirapo apa….
Kodi aise Cosmas zaku 24 ngwenyazija zilipati padakalipono zangoti ziiitu kapena zalowa chinyengo etii
Ngwenya Zatan?
Zaka Zachepa,life Imprison Mpabwino.Kupepesa Munthu Ata Osamva Mfiti Za Azimai
Akuti Iwo anali ma MG1 olimbana ndi ma MG2 kkkkkkkkkkk apa zaonekeratu MG2 wawina basi
Mg2 Eti Koma Lovemo Iwe
Amukwatire Basi MG2
Achita bwino akagwire ndende
Azimayi kudziwa kukodza kwambiri eti mpaka mzawo chinkodzo pwa
kkkkkkkkkkk
Your Majesty, koma zakazo zizinacepe? Please revisit your Law books.am annoyed with them..
Nkhani ndiyayikulu iyi kunena zaka six tisaname zachepa kwambiri ndikanakondwa zikanakhara 8 kapena 10kumene
munthu amagwirilira mwana ndi kupasaso HIV.. akulandila chigamulo chazaka 10…… ndiye do u think chingamulo chamulandu umenewu chingaduse zaka six???
Pajatu akuti mmodzi wa azimayiwa naye ali hiv positive ndipo ndinkhani yomwe anamuzunzira mzawoyi chifukwa amawulura kwa anthu za status yake.ndiye pamenepa mkodzowo tinene kuti unalibe tizilombo ta hiv?
Kikkkkkkk Stella ur very funny
Phuma azimayi
Ni normal but osationelamo for commenting monga ndise osangalala vifundo tili navo
Awa wanthu wakamba manga asowa chopanga post kulibwino muyende kumanyandule mkapeze khani yotitumila bakolewa awa khaze
Kkkkkkkkkkkkk nishi palibe tandizo yopasa naise tizatambako chabe
aaaaah ayi… nkhani ndiyamikozo basi?
Ndende ndyatonxe palibe zot ndnkaz welcome to hell
Yes,yes yes,ena atengelepo phumzilo,aleke chibwana,koma ee zaka 6osawonana ndi amuna awo,amve m,bebe mbuzi zaanthu,sindikuziwa kwathuku KT zozathaso bwanji.ku24.
Akakumana ndi akaidi otopa ndipo adzabwerako ndi ana ndithu
Mikodzo chemwali kukalowa nayo kunja? Muzatipeza koma ndimmene likusinthila dzikoli mudzakumbuka mayendedwe amtaunimu?
Kkkkkk
Mmmmmmm!
kkkkkkkkk koma yah alibe mwati chani pano??
Aponye ku cel ya amuna buzi za anthu
hello wonderful friends and my country people my name is Thandi Daniel and this is a testimony of how i got cure from HIV/AIDS, my joy has no limit as it has been long i have being suffering from HIV/aids for the past 7 years without the expectation of being cure, Happiness is all am experiencing now as am posting this about Dr Abuu the man that God has been using to heal people, and I was one of them because I was cured from HIV/aids by his medicine, if not for God and Dr Abuu my children would have been orphans today but i thank God and Dr Abuu for saving my life, for those who are passing through the same should call or whatsapp Dr Abuu on whatsapp with his number +2348066454364 OR EMAIL [email protected]
Is Dr Abuu Malawian?
If u gat nothing better to do, jst go n rot wit ur friends in jail. Since mulibe chochita and yet u want everything to b @ th tip of ur fingers, ndi izo mukungodzera anzanu instead of making money. If u will live ravishly, will die of AIDS, like/hate t. To H.E.L.L wit ur so-called testimony.