Awagamula zaka zisanu ndi chimodzi za kalavula gaga chifukwa chokodzela mzawo

Advertisement
Area 25 Women Jailed

Lawaluma lamulo ndipo lawasiyila chilema chachikulu chokuti ngakhale a chipatala sangathe kukonza. Ndipo inu nonse okonda kuchitila nkhanza ena, bisalani patali chifukwa mawa mutha kukhala inu.

Amayi atatu a ku Lilongwe amene anagwila mmayi mzawo ndi kumusunga momukakamiza ndi cholinga chofuna kumuchita nkhanza, agamulidwa kuti akasewenze ku jele kwa zaka zisanu ndi chimodzi.

Area 25 Women Jailed

Amayiwa amene amachokela ku dera la Area 25 ku Lilongwe, ati anagwila mmayi mzawoyi chifukwa amafalitsa nkhani yoti mmodzi mwa atatuwa ali ndi kachilombo ka HIV.

Iwo ati pokwiya anamutenga ndi kumutsekela m’nyumba ndi kumuchita nkhanza kuphatikizapo kumumenya, kumukodzela ndi kumuvula. Pochita izi iwo adali akujambula.

Atafika pa bwalo, mkulu oweruza wawagamula kuti apite ku ndende akasewenze kwa zaka zisanu ndi chimodzi.

Amayi atatuwa ndi a Thokozani Msiska a mmudzi mwa Enukweni, Mfumu yaikulu Mtwalo mu boma la Mzimba. Palinso a Zelifa Phiri ochokela mmudzi mwa Setha, Mfumu yaikulu Zulu ku Mchinji. Omaliza ndi a Rodness Chose ochokela mmudzi mwa Gonthi, Mfumu yaikulu Kamenyagwaza mu boma la Dedza.

Advertisement

135 Comments

 1. zithu ngat izi ndizovesa cisoni ndipo mwin azimayi ena atenger phuzi koma izi zikacitikaso osawanyengelera kuwapasa cilango athu atengere phuzi

 2. Mmmmmm acita bho athu mwin tisiye zover azathu azimayi ena ndiopusa satha kufusa mwina muthuyo mwina muthuyo amabwala oh awapase cilango cacikulu mwina asazapangeso azmayi

 3. Tizingowaloza,poti umfiti kulibe Ku police,nanga tikawamenya atimanga,NDE azimayi tipeze mankwala owapotoza mapazi bola osajambula powalozapo

 4. Zaka zachuluka guys, Nkhani yake yochepayi… Mukulephera kumanga nduma zaboma zikungoba ndalama zamisonkho ya aphawi…. Agalu inu mukapsa moto kumwamba nonse ama Court…

 5. Chigamulo chimenechi chilimbikitsa atsikana kuti asamakane amuna oti ali ndi banja lawo kale, chonsecho akudziwa kuti munthu akundifunsirayu ali ndi nkazi wake. Acourt unikani bwino pamenepo

  1. aweluzidwa pazomwe adamuchitira mzawo pomuvula ndikumukodzera wosati kuti amayenda/kunyengana ndi mwamuna wandani? zakukhuzani poti ndi azimai anzanu koma akadakhala kuti achita izi ndi amuna mukadalalata. Mutengerepo phunziro

  1. akulekeranji kukhululukidwa anthu wosalakwa akungidwa mundende zadziko lino? pali akazi anu/bwenzi lako? wosadanda uzimuyendera kundende konko

 6. Mmene timarakwitsira anthu ife bwanji mulungu satirangiratu pompo koma azimai awa sanamve kupepesa kwamzawo kuranga okha mosamva chisoni eish satero

 7. Awatu akhale ma germs azimai kodi iwowa salakwa bwanji osamvako kupepesa kwamzawo uja ndiye chabwino banjalo likomanso pamenepa zaka zachepa mwina akarandile yesu konko komanso akathandizenso ntchito za boma antchito ngochepa

 8. Mmmm zakozo zachulukitsa,sanaphe munthu azimayiwa,ogamulayo aganizirenso bwino za chilangocho,3-6 months cud be better,apapa mulimbikitsa ziwerewere ndi kusakhulupirika kwa azibambo to their wives.

  1. Alimbikitsa ziwerewere nde kuti chani ukuganiza azimunawo sankanyenga or alipo amunawo ali ndi zibwenzi atenga zibwenzizo akaziwonso anali ma hule otha ntchito

 9. Zanziii ndiposo ndizofoila zokondera bwanji sanamugale George chaponda uja ndiye mukuwagamula azimawo chifukwa chot alibe ndalama shatapu

  1. iweyo ukuganiza kut chaponda uja ndi azimai amenewo anapweteka athu ambiri ndindani oky sopano issue ya chaponda ija bwanji sanamangidwe koma iweyo takayesa ukabe nandolo tione ngat sukalowa ku ndende

  2. komabe ndizosiyana man bola akanakamba issue yofanana ndiyachaponda think of your mother achitilidwa zinthu zochitisa manyaz ngat imeneyi mmmmmmm akagwilebe jele amenewo

  3. komabe ndizosiyana man bola akanakamba issue yofanana ndiyachaponda think of your mother achitilidwa zinthu zochitisa manyaz ngat imeneyi mmmmmmm akagwilebe jele amenewo

 10. yaaaaaa komaaa tinkhan tinat mumaxiwaa kuthana nato komaa kut pangan zitukuko kurephela magetsi dairy kuzmaa koma chosecho mumatirandaa misonkho

 11. shit happens in life ka 6 years nkambiri bora osazapeza azimunanu akwatira shame all the best to the other side ati its more like hell

 12. Do you believe there is an herbal doctor who cures HIV? I was HIV positive for 9 years and taking ARVS until I was cured completely by Dr Tiam. His herbal medicine is very powerful and reliable you can get him on call or WhatsApp: ‪+2348037284837‬

 13. ndangowamvera chison a rodnes chisale wo coz amandisanjitsa ndikapwa. koma apita ndi dollar zanga zomwe ndinawakonzera magetsi

 14. Aaaaaa! Chirango chaphweka ichi akanati 15yrs coz komwe anapanga apa ndikupha. kukozera munthu mkamwa mix mkozo wake ula ophatikizana ndi #PERIOD zauve apa chirango chafewa. #ZANDINYASA.

 15. In the US when a traffic officer stops you and you put your hands in your pocket he shoots you instantly..

  In my country when a traffic officer stops you and you put your hands in your pockets he starts to smile.

  Guess which country I come from….

  1. Pajatu akuti mmodzi wa azimayiwa naye ali hiv positive ndipo ndinkhani yomwe anamuzunzira mzawoyi chifukwa amawulura kwa anthu za status yake.ndiye pamenepa mkodzowo tinene kuti unalibe tizilombo ta hiv?

 16. Yes,yes yes,ena atengelepo phumzilo,aleke chibwana,koma ee zaka 6osawonana ndi amuna awo,amve m,bebe mbuzi zaanthu,sindikuziwa kwathuku KT zozathaso bwanji.ku24.

 17. hello wonderful friends and my country people my name is Thandi Daniel and this is a testimony of how i got cure from HIV/AIDS, my joy has no limit as it has been long i have being suffering from HIV/aids for the past 7 years without the expectation of being cure, Happiness is all am experiencing now as am posting this about Dr Abuu the man that God has been using to heal people, and I was one of them because I was cured from HIV/aids by his medicine, if not for God and Dr Abuu my children would have been orphans today but i thank God and Dr Abuu for saving my life, for those who are passing through the same should call or whatsapp Dr Abuu on whatsapp with his number +2348066454364 OR EMAIL [email protected]

  1. If u gat nothing better to do, jst go n rot wit ur friends in jail. Since mulibe chochita and yet u want everything to b @ th tip of ur fingers, ndi izo mukungodzera anzanu instead of making money. If u will live ravishly, will die of AIDS, like/hate t. To H.E.L.L wit ur so-called testimony.

Comments are closed.