Zisankho za mu dziko la Amereka zasokoneza utumiki wa mkulu wa ku Nigeria otchuka ndi nkhani za ulosi, a TB Joshua.
Lachiwili pa 8 November anthu anavotela Bambo Donald Trump kuti ndiye akhale mtsogoleri wa dziko la Amereka akachoka a Barack Obama chaka chamawa.
Kupambana kwa Bambo Trump kwasokoneza mitu anthu ambiri amene amayesa kuti a Mayi Hillary Clinton apambana. Mayi Clinton amene anakhalapo ndi udindo mu ulamulilo wa a Obama amaoneka a chikoka ndi okondedwa.
Chikoka chawo chinasokoneza mutu mtumiki wa Mulungu TB Joshua mpaka anapanga ulosi oti Mayi Clinton apambana.
“Ambuye wandionetsela za zisankho za mu dziko la Amereka,” anatelo Bambo Joshua amene ananenelapo za imfa ya mtsogoleri wa kale wa dziko lino a Bingu wa Mutharika.
“Ine ndikuuzeni kuti Ambuye akuti apambane ndi mzimayi,” Bambo Joshua ananetelo uku owatsatila akutchaya ma Ameni.
Koma zotsatila za zisankho zitatuluka, a Joshua anapezeka kuti ananama.
“Wawina zisankho ndi munthu wammuna, iwo aja bwanji amati azakhala wamkazi?” anafunsa choncho anthu odabwa.
Kkkkkkk munthu wa mulungu anabalalika day imeneyo
Zazii zopanda mutu
Galamukani ndipo dzuwa lapendeka
Moses ndi Mirriam akanakuletsani izi. Bola mirriam anapanga khate koma mwina chilango cha onyoza chikhala temberero which lasts for 4 generations.
nonse amene mumakhulupilila. maprophets mumakhala ngati mulibe nzimu mumayendela ziwanda osati mulungu kapena satana onyenga ngati maprophets
Is only God who choose a leader not dis fake prophets
Inu musamalimbane ndi alaliki wonyenga ufuna kutchuka ndi ndi chuma olosela imfa kulephere kulosera zawo
Nkhn nd a escom mages azivutabe mpka lit ? hq..
Nkhn nd a escom mages azivutabe mpka lit ? hq..
Jeremiah 14vs14..When a prophet speaketh in the name of the LORD, if the thing follow not, nor come to pass, that is the thing which the LORD hath not spoken, but the prophet hath spoken it presumptuously: thou shalt not be afraid of him
Ok basi atilamura yemweyo tamunyadita trump woweeeeeeeereeeh
Sananame ulosi wake ndiolondola kungot crinton waberedwa mavote kkkkkkkk lol
Kaya ine zaulosi ndili nazo kutali coz kwathuku kuchislam kulibe nyasi zaulosi timamvera kwainu amzathu ndiye mulungu wafuna kudzachitisa manyaxi ma so called prophets
kma ajoshua amenewa nchanichimenechi
Inu nthawi zina zake muzitha kupanga post zinthu zothandiza..ife zimenezo zitipindulira chain #zausilu_basi
Man of satan
why prophet is taking part in election,? is God allow this?or its a fank prorpht ?
Zovu zeeedi mezi. Chofunika ndikukhulupirila Mulungu yekha basi. Munthu utamuyika 99.3% udzakhumudwa naye.
Awa amalosela zaimfa basi
busy with american politics but yu wil never heard americans busy wt yos..
Clinton has won the popular vote…and her supporters are angry how the presidency is lost…
eeeeh kaya ine zsandkhuze!!
Masiku osiriza buku loyera linalosera kale kuti masiku osiriza kuzakhala aneneri onyenga ndiye apa mwakhulupila nokha
mulungu simunthu. ndipo ngakhale atafuna kuti inu Lero mutchulidwe dzina loti maliro zimatheka. nde uyo mukumunenayo mmmmmmmm ayi amangolosera koma wokwanilitsa ndi yehova basi.
Zkusonyeza Kut Onse Amene Akhumudwa Nd Zotsatlaz Stl Otsata Mulungu .Kowa Kuyambla Lero Dzwan Kut Tl Osiyana Nd Mulungu
Satana Teptope Joshua
Ndakukuvani nonse mumatha kuyakhula, Koma dziwani kuti Mulungu simunthu chiweluzo chukubwela
wabodza uyu palibe chimene amadziwa lero waziona kulosera zabodza kkkkkkkkkkkkkkklllll nigerian prophet
Zovuta izii pray hard, read the bible bola asakhale mzake wa bushiri chifukwa bushri ndiye ndiwasatanic kma mkulu uyuyu mwna zangovuta ine itrust hm 90% bushiri 0%….zofunikira osalimbana ndi anthu prophets, pastors etc its waste of tm rather focus on ur relationshp wt God!!! Is it gd or nt,, the holy sprlt wl direct u n everythng!!
Hahahahaha
Without a spirit of God u can’t understand what man of God is saying
Deu 18 v 22 , 2 PETER 2 V 1 -3 Isaiah 28 v 7-13 Lamentation 2 v 14 MUKAWERENGA MULIUZA DZIKO ZOMWE MULUNGU AKUYANKHULA KWA ALOSIWA
if GOD wrote he wrote stop bleme one anether bcz only God knows the trueth, jesus says if some preaching the word of GOD in the name father, son & holy sprit, he is son of GOD leave TB JOSHUA to preach the word of GOD, just repeat ur sins and follow jesus ways to have life, GOD say s , otembereledwa ose onyoza mtumiki awamulungu.
Aaaa kk achepa mwana
Tb Joshua it’s not God to believe on him who is him .zausilu bas tiyen tikhulupiriren mulungu bas.
Inu a news a ku Malawi please please muzimva chinzungu amanenera kuti please tell if you was there last Sunday mene amanena bwinotu
PVT: God and his Prophect they are never wrong on American election ,actually the popular vote . Hillary Clinton she win Trump as 47.7% to 47.5%. She got 59,755,284 votes , Trump got 59,535,522 votes ,actually Hillary Colinton she narrow win 0.2% as Prophet T B Joshua told us at the Sunday Service . in God’s opinion She is the winner of this election ,but we human being’s system maybe against God’s will …
Glory be to God ,thank you Lord, thank you Prophect T B Joshua …
Mutale Nsomeka, if you really understood the electoral process of the USA (especially that of the president), you couldn’t have been scribbling this gibberish. However, I take it that u are a “Prophet” fan, and I understand that. But if I were you, I couldn’t have been wasting my time defending the indefensible. TB Joshua goofed (and for your own enlightenment, he has erased the tweet that proclaimed what you are unconsciously denying). That is it. And please stop this nonsense of “God’s opinions”; you make God look stupid (a thing that He is not and cannot be). God never has opinions; Hillary lost. And if you are really a Christian you would want to read Romans 13:1.
U R A FOOL MR NSOMEKA. ask me why.
Malawian pp,pliz dont comment much on this .Let God Himself judge.
Ulosi wanji olosela zakuthupi.mulungu.wayambapo.kuonetsa.kukwiya.tsopano.chenjelani
He he he he ndiye zakhalilamu Mr joshua akut chanino,tiuzeni anthunu amene mumansatilanu.apa drivelayu wakulowesani tchile ndiye mutani muzinkhulupilirabe kaya
God never lie but He can change accordingly
Tiziwapemphelela anse amene alindi maso ndi makutu koma samapenya kapena kumva
Taonani Ndidza Nsanga Ndipo Mphoto Yanga Ndiri Nayo Yakupatsa Yense Monga Mwa Ntchito Yake (Chibvumbulutso 22) Watch Out For The False Prophets And Their Prophecies.
Usaweluze pakuti naweso uzaweluzidwa
Mmmm man of God mwatani? kkkk koma kulosera imfa za ma president
Is he chosen by people or God??
Mau a mulungu amati neneri akanena mau kusachitika simulungu amene wanena
Bushiri sana losele nawo? Kkkkkk
I wonder what God was thinking telling his messenger a lie.
sizirizonse tikuyenera ku losera!!!!!!!!!!!
TB joshual wanama kokwana phanvu zake nzochokera kumidima mumadziwana kunyanja komko koma choti mudziwe akuluakulu mulungu akamuongola muthu palibe omusocheresa chimodzimodziso amene walandila mkwiyo wamulungu palibe omuongola nde ine sindimadabwa muthu akamakakamila tchimo olo ataona kuti chilungamo ndi ichi satembenuka muzichedwa mkumakonda athu oti ndasasatana onamizila yesu chisomo sichinakugwereni utumiki wamulungu sumangobwera ngat phepo ayi atumiki enienu amulungu adapita kale panopa anatsala mautumiki onyenga mmalo mowauza athu azilapa mukukangalika kuwapatsa athu zamdziko zomwe zisakhalitsa zoti kulichilango chamulungu mudayiwala TB Josual ndi ena omwe amazitcha ndatumiki amulungu asaliodzidzedwa ndimulungu mudziwe mulindimilandu tsiku kachiweruzo mukusocheretsa mitundu ya athu ndipo nmukayakha komaso chilango chowawitsa chikukudikililani moto waukali ulipansana panu musiye kumawanamiza athu athu ambili piano akungofuna zadziko lapasi ambili mudzawaone amapita chifukwa chamatenda kusowa kwabanja ndi mavuto ambili sapitika chipumutso chamukungu dziwani kuti ndithu kusauka sitchimo kupanda mwana sitchimo ayi lelo osauka amaoneka kuti adamulakwila mulungu ameneo amakhala mayesero amulungu musiye kuzitayitsa thawi ndikuyang’ana chipulumutso kwamuthu nzanu olengedwa TB Joshual is a DEVIL LIAR STOP MISREAD PEOPL MOTO UKUKUDIKILILANI
TB Joshua watinamiza kokwana
I don’t trust a man,God will remain himself and he cannot be corrupted by the evil people’s mindsets .Prophets are just competing for their own popularity.
Step down babilon . a song by late matafale
Anawona amene alindimulalo ndikumalozera bwino
muli buzy kukangana za zii…..
MMm koma pipo ‘;dot judge z leave t for GOd,
Nawenso chisilu chamuthu ana kuuza zoti mulungu ali ndimwana ndani zachamba basi mulungu alibe mwana tazingokambani zina apa osati zoti mukalowe kumotozi pepherani kasanu pasiku mulungu akakuloweseni kumwamba
Tiyeni tikuluphilile Mulungu yekha basi
Kkkkk! za ulendo uno, zilibe meaning.
Let God b God
Chitsanzo chabwino chimenechi musamakhulupilire anthu aziwanda. Anthu onama mdzina la Yesu. Akupanga zimene Yesu sanapangeko
Hoseya 4 ndime ya 6 anthu anga akuwonongeka chifukwa chakusadziwa Mulungu akutero (wake up malawi be wise)
Atumiki onyenga awa
Apa Zavuta kuchimuna Mlosi Wanji Wongodziwa Kulosela Zakumwalira Kwawina.
palibe chanel chimene tb Joshuah analakhulapo ndi fb idiots people anamuika mawu kamwaaa
Hahahaha,,, ife kuma followers ake onse tingoti pepani, ndimmene zidzakhaliranso pa tsiku lomaliza, mudzakhumudwanso, msanati.hehehehehe! Ine pheee mwayesu
anthu opusa ndi amene amamutenga TB joshua ngati amaziwa chili chonse ,inu mwini dziko lapansi ndi mulungu iye ndi amene amaziwa chomwe chingachite mawa osati munthu olongedwa .
Vuto la atolankhani komanso ma prophet alero amakhulupirira kuti chipani cholamula sichiluza koma imeneyo ndi mbiri ya kale zakachitika madera ambiri ngakhale kuno ku africa including malawi 2014 dpp inagwetsa pp komabe onsewa adali m ‘boma kungoti dpp inali pa bench kwa 2yrs zikanakhalabwino ikanawina mcp?????????
ili nde dziko,ukapanga choipa chimodzi chimayenda nakulankhula momwe afunira.Koma zabwino olo tapanga ma thousand munthu sayankhula
Plz guys tisakhulupilile munthu koma mulungu yekha basi
Kkkkkk. Prophecy. TB
Tb joshua akanayamba,kusalakudya ndikupepha mulungu kut amuthandize, Iye anazitengera kuthupi osati kuzimu ai,shame
I thought we should preach about God’s kingdom, kodi zaumulungu nzogwilizananso ndi ndale? always prophesis about politics, osamvako zakumwamba why? guys, lets open our eyes and see….
Kodi mavuto amagesiwa adzantha liti?
vula ikagwa
anthu timatengeka ndi zinthu zopanda pake. Ati uyu amapanga zozwizwa akandipemphelere mmmmm mumabvutkiranji? Lowani mu chipinda chanu Gwadani pansi pemphani kwa mulungu wanu azakupasani zosowa zanu. Masiku osiriza kuzaza aneneri onyenga azasamusa phiri kuchosa uku kupitisa uko anthu nkumati uyu ndi mwana wa mulungu uyu. Ai ndithu ndithu Tisapusisike. Nanga Taonani ulosi uwu . Zikugwirizana?? Ngatidi amalosera mu zowona nanga zatani? Mulungu salakwisa. Mwina uyu anaiwala? Tisatengeke ndi zinthu zopanda pake. Tizakhumudwa tizasiya kukhulupira mulungu Titakhumudwa ndi zochita za ma prophet
Guyz we r in the days of the end read (2Timothy chapter 3 by the ves of 1 to 5)
Abale Thandizeni Kodi Trump Ndiwa Chipani Cholamula Kapena Chotsutsa?
Ma prophet a satanic awa
prophets of today kkkkkk
KKKKK mukundiuza kuti nthawi yonseyi simumadziwa kuti Joshua ndiwabodza I don’t believe in these guys so called Prophets ena ndima drug dealers inu kumawatcha men of God kkkkkkkkk and why prophets are always Africans? Tell me!!!
Wadya zochuluka uyu
ng’anga nyengo zose yikufumba dankha chikaya,pano ninjani fwiti in private,TB Joshua ning’anga panji tchimi
kkkkkkk, Aneneri/Atumiki a Mulungu enieni amaphunzitsa za Boma iri: DANIEL 2:44
Timakuudzani nthawi zonse awa ndi aneneri onyenga dinadzo zimangolingana basi
Kk pali mulotsi mmozi yekha ndiye mwana wamulungu amene tsanama.amene tikumu dikila kuti akati konzele malo bas zonamiza apa ay.
Kikikikikikiki…..akuti he was just trying to predict whats gonna happen, it wasn’t a prophecy, kikikikikikikikikikikikikikiki zinakati zatheka anakati it was alrdy prophesised but coz zavuta akuti it was just a prediction, it wasn’t a prophency as you people thought…..kikikikikkikiki
tb joshua is my prophet, mnyoze msanyoze sindizasiya kumkonda ndipo kuvera ulariki ndi uneneri wake
Mukuchedwa a sisi
mkuchedwa ndinu woweruza
Victoria Mithi ndiwe wamisala or u were born prematurely.Wouma mutu ndipo sudzathekha !Pepa!
zabvuta zabvuta basi kodi iyeo ndi mulungu wanu?
mmm
who are you defending lies,@ he said we should pray against that,so which means he was saying people should pray that the woman shouldn’t win?
kodi tb mudakakhulupililabe? Mbuzi zawanthu bwanji osakhulupilila yesu mukuchedwatu.
Joshua amanama nthawi zina,nanga tiziti mulungu wamnamiza iyeyu
Only this time God he used me to prophecy about this just look on my wall you will see what I mean God bless you people of God amen
Thats prediction not prophecy
https://m.youtube.com/watch?feature=share&v=zQGRQY6ke_M
It doesn’t matter how much you will try to back your con man, he lied and goofed big-time and there is nothing you can do about it! He never said anything about praying against it. The clip has just proved to you that you are liars trying to justify a lie. Hahaha zavuta ku SCOAN!! Sorry blind followers!
woolman not woman . akutelo
Ndikugwiridzana ndi frank chitule .abale ndi alongo choyamba ziwani kuti nthawi yomwe tili ino ino ili ngati extra time .yesu ananena kuti anthu adzakhala okonda ndrama aukali mtundu ndi mtundu udzaukirana.aneneri ambiri adzabwera mu dzina LA yesu.ndipo izi zikuchitika ndi nthawi yoti tilimbikire kupemphera komanso ma prophet onyengawa tiziwapempherera kuti adzapitiridze kusocheretsa anthu a yehova nthawi yatha
Ena APA anena kale kuti tike mtima wanthu kwaorenga dzuwa yekhayo sadzatikhumudwitsa, not munthu.
Bas manyazi kwaotsatila joshua’nu anthu opanda mzimu Ana anjokainu bwanji chikhulupililochanu mumaoka kumunthu??
Chaonetselathu mkazi sioyenela kulamulira dziko
Like this page for latest news https://free.facebook.com/Malawi-aziwe-chilungamo-995613277224198/?v=feed&_rdr
Akanakhala maliro ndiye adakalondola koma izi aah zavuta
Apa ndi pamene mungadziwe kuti prophet ndi wonama, wotsogozedwa ndi ziwanda komanso wa satanic ndiye ndi zanu izo nonse mumamvera oipa ameneyu
Kkkkkk!!!! Baibulo zonsezi zikuchitikazi linalosera kale.
Aneneri onyenga Yesu sanaloserepo za dziko ngati zimenezi! Lol .Kuli uchimo wambiri womwe ukuchitika padziko lapasi bwanji osalalikira za chipulumutso, koma ngani ingokhala kudalitsika ku dziko lapansi, you will be blessed! Successful messages only.
Aneneri onyenga Yesu sanaloserepo za dziko ngati zimenezi! Lol .Kuli uchimo wambiri womwe ukuchitika padziko lapasi bwanji osalalikira za chipulumutso, koma ngani ingokhala kudalitsika ku dziko lapansi, you will be blessed! Successful messages only.
Nanga zamtengo wamkuyu unanyala uja. Nanga za Jerusalemu ndi kachisi ndi mwala yake? Mauneneri onse a prophet T. B ndawaona akuchitika and ndimamukhulupirira Mr John Ngwenya
Pali zinthu zina Mulungu amafina muone chilungamo koma mumachita kutseka maso ndimakhutu, chifukwa chilungocho chikukuwawani.
Asaza pangeso predict koma azingo phunzisa zakubweranso kwaYESU, alarikile ndiku phunzisa za kuti anthu atembenuke mitima. Osatiso kuma khala akulimbana ndizadziko lapansi.
Atumiki amatsiku omaliza
Shame on you demon
Coment reserved
Kkkkkk.. Donald Trump has won the electoral vote while the popular vote has gone to Hillary clinton…. according to US policy, electoral vote takes someone to the white House… wht ever the case.. Ibelieve Prophate TB Joshua 100%.. and ucant compare TB Joshua with Bushiri the childish fake prophate…
Za mawa azidziwa ndi Mulengi basis!
Amalawi kupusa basi,osamalimbana ndi president wanuyi bwanji,mmalo molimbana ndi pitala kuti athetse mavuto a mudziko lanu but ur busy talking nonsense about the man of God, wat is ur benefit from this story while ur sleeping without food in ur house? kupusa basi,n some of u u even dnt anything about this man of God but busy talking shit.
I knew it…!! Ku ulusa za imfa nde saphonyaa…wakumana ndi eni dziko lapansi baba…Try again leta, mbali yakwathu kuno 2018
Haha haha
Ine ndili ndi video yake ananenadi kuti awina mzimayi akuifuna hit my inbox.
Plz do send me
Zopanda ntchito izi Mulungu anatiuza kale aneneli ake mma holy books kuyambila bible mpaka Quran mulibe mayina awo
Zaursiru basi
heeeee! ndiye Mulungu ameneyo alibe chibale phwanga, amakwangwanula tima plan nditi nzeru tonse tamamina ta woyipayo ndikutiyika mmaja mwa tiyana ngati pamenepa kuti wuwonekere. Ndie ana amagwiradi nawe tchito kukumoka ngati mmene akubebera ma comment wukawa browser nkumati koma nzedi. take care ndi boma lina kumwamba and I think wakhalaso winayu iweso usamale ndi boma limeneli lakumwamba. YEHOVA ndie mwini ma plan ubweraso poyera naweso ngat nzakoyu. wekha osati ife. Ndiye poti ndiwe kaleso m’bale ayi mmwemo ine ndidzango kukhululukira koma sindikudziwako ena kuti adzakutani.
heeeee! ndiye Mulungu amene alibe chibale, amakwangwanula tima plan nditinzeru ta woyipayo ndkutiyika mmaja mwa tiyana kuti wuwonekere. takje care and I think wakhalaso winayu iweso usamale ndi boma lakumwamba. YEHOVA ndie mwini ma plan ubweraso poyera nawe ngat nzakoyu. wekha osati ife.
Akriritu ndi abonza heavy INE NDEKHA NDIYE NDIDATULUKA CHIKHRISTU MPINGO WABONZA WA PAULO.
Ama ngona maenawa
Business man…zivutikani iye akupanga ma profit.
Ana a Njoka amamutchula kuti ”Man of god” Kupepela basi!!!! Koma nkumazitcha kuti ndi Achrisitu pamene BIBLE simulidziwa.what a Shame!!
Amalawi muzitengebwino mumawonjeza ndizotengekatengeka apondiye mwaziwonelanokha mwanunokha mulisoutumiki komamumazikayikila mumagosatila zilizose mulungu alipalipose matumiki enawa samalani amalawa musapusike ndkutchuka amalawi mulungu amakukondani ( ambuye pitilizani kudalisa malawi ameee )
Manyazi bwanji pamenepo
Aneneli onyenga mmasiku osiliza.
He is not prophet of GOD bt rather prophet of gods,,,so if u olwz listen and follow his doings u r part and percel of their evil
Munthu yemwe amamukhulupilira TB Joshua nd otaika kodi iyeyu ngat amaona zatsogolo nanga bwanji sanalotsele zoti church yake izagwa pa chifukwa chan? Uyu nd wapansi pa madzi
Guyz choti muziwe anthu awa amalotela za ifa osati zinazi
mistake. Bible limaletsa kunyoza azitumiki ake sindikumubakira Joshua koma yense wakunyoza ntumiki wamulungu azalangidwa. simukudziwa chilungamo yet mukunyoza apa kupalamura gahena ya moto ndithu. yense amene akutumikira dzina lamulungu wether nd ntumiki wabodza or ndiwowona musanyoze. who r we to judge? abale ndi alongo samalani Mulungu azalanga ekha zikomo kumpando
Linatitu kunyoza ntumiki wamulungu linapatuliratu kut alikonso ena satumiki amulungu.Alimbanabwanji ndi za ndale ngat kut zugwilizana ndi umulungu?
Muzimunchabe mtumiki wamulungu
Ma prophet Enawa Amandidabwisa Avekele Mwezi Uno Miracle Mabanja Kaya Ku tchito. Miracle ikachitikad Aziti Ndye Walosela!Kumatenga Petrol Mkumasakaniza kaya Ndizichani Mkumati Anointing Oil Ati kumazisila Pamutu Pawo cholinga inu Poona Muli Ndiziyenda Ndimadaliso.Ayi Ma prophet Osewa Ali pa Busnes Bwanji samanena Za ufumu Wakumwamba?Amangolimbikila Muzapeza Banja,Ntchito,Busnes koma Amaiwala Zaufumu Uli Mwamba Kuutchula.Chongofunika Anthu Ngati Awa akungofuna Chuma chanu Basi. Wakuva Wava! Osava Kaya Atsate Uzatiuza!
Mmmmmm ,yaa mwayamba kunyoza ndi atumiki amulungu?
Apapa tonse tatsimikiza kuti mkuluyu ndi wabodza. Manenedwe ake ndi #False_prophet_must_fall. Mkuluyu watipusitsa kwambiri…
Khalani kumaweruza azanu mulungu ndi amene adzawereze inu stana anayamba ndikale kulimbana ndi TBJ Koma ndikuwuzeni ichi satana alinanu cholinga mukapanda kusamala mumutsatadi
Izi sizinandikhutsa or pang’ono..
Thanani ndimavuto anu kaye.Dziko lingosaukirabe,magetsi tidayiwala,njala ndiimeneyi,pano tafika pozolowera kuunikira makandulo nde muli busy kulimbana ndi TBJ mmalo molimbana ndiakukuberani ndalamawa.
Vuto chizungu chimakuvutani ndichifukwa mukutelo and munakakhala kuti TB Joshua mumamutsata bwino bwino sibwezi mukutelo
Atumiki amasuku ano ambiri siatumiki amulungu koma ongokamba zofuna zathupi chonde tiyenera kuwapewa chifukwa akutikopa kudzera mudzina la mulungu. Zolosera zawo zazii zongofuna kudanitsa anthu. Always believe in God not a person!
Koma nde zivutadi tisaname, a world prophecy, failing to materialise? I’m failing to understand this. Very confused.
ine ndabwela pano kapunzila nyanja ndimachoka kuZimbabwe anzanga dont laugh
Nda aneneli onyenga awa musamaiwale mabuku oyela ananena kale zazimenezi
abale tiyeni tizingolimbikila kupemphela TB J ndi munthu obadwa muthupi lanyama tiyeni tisamukhulupilile.GOD Z GD O THE TYM!
chonde guyz zomanyoza atumik sizabwino kwa amene timamukonda TB joshua tien tipitilizebe kumukonda chfkw amene akumunyozawa amadana naye ndikale nde asatipangise kut tizinyoza atumik kut muone amene akudana nd tb joshua nd anthu ot sapephera ndkomwe azizanga tisatengere azizathuwa zikomo powerenga
To canal minded is death but to be spiritually minded is life
Utumiki wausatana uja, mzake nd uyu wathuwathu akhala kujon yu, mukamapita kwaana anjoka amenewa skut mukapemphera koma mukatenga zwanda. Zopusaaaa….
I don’t believe prophecy….
Munthu ndiwokhumudwitsa ndawonela neneli wabodzayi kkkkkkkk mulungu yekha ndi amene amadziwa za mawa
Palibe kuvuta kulikonse
TB dog
Wabozatu ndalayu, anapitanso ku Tanzania mkuwanamiza kuti lowasa ndiamene angazawine paxisankho analephelanso.
Mmmm you guys why are you behaving like that? Fighting against men of God?
Frankly spearking Mr Elia, if TB Joshua had that prophecy then it means that that Prophecy wasn’t from God, because God can’t reveal lies to His Messangers. Its not a fight, people are talking what they heared from TB J, so they need an explaination about that Prophecy!
R u not man of god?
Prophet wabelezebule uyu, nzake ndiwinau.
Don’t hesitate we’re in the last days now all the holy scriptures must revealed Jesus himself prophesied about these days Matthew 24:1…..
TimakuuZani ife kuti PROPHET silimabwela kwamunthu yemwe wakhuta kondoole kungoloweza ma ves awiri basi uprophet umabwera pokumana ndi mgero live sati zanuzo musazakhulupilireso
Hahahahahah guys why can’t we concentrate with our own country on how we can remove poverty in our country….. We are just talking about american president as if we will gain something at the end… Grow people of malawi shaaaaaaaaa
Zisiyeni zimenezo wonani utumiki wanu ,pangani zainu .
Tawauze samamva chizungu awa kuyambira lero amene simumamva chizungu musamayakhure china chili chonse mwamva
Koma asamaname ngati mene amanamidzila anthu mu church lake lija kumawagudubusa anthu ndi masenga ake aja ife ai sitimakhulupilira munthu timakhulupilira modzi ndye yesu khristu basi osati izi
Mulungu wapanga dala zimenezi kuti mbava za ma prophet zi zionekere poyera.
kaya zanuyizo
Kkkkkkkkkkkkk koma Joshua awulephelatu u neneli
nayeso ndimunthu amalakwa ndithu,
Kkkkkk..kulibe prophet muziko lapasi,,believe me!
Uyyu ndigalu waboza satana onyenga wakuba kwabela athu nyan
TB Joshua timing inamuvuta akanangotengera mene zisankho zinaendera kumalawi pano bwezi anthu akumutengabe dolo nkumawapusisabe koma apa yalakwa
Mpaka timing?…kkkkkkkk
kkkkkk ma profet abza
Ziwan kuti Satan’ wakuponyekasi ..mwenecho waboza ndi we mu wanthu anyaki
Zachamba josha wachaninso mulungu ekha ndie amadziwa
We are in the last days as prophesied by Jesus Christ,many will come in God’s name,wearing the name ” lamb” but they are wolves or heyanas
Kodi zikutikhuza KT wawina ndn????amalawi muzamunena munthu Ali mtumiki weniweni…chengeran ndi pakamwa
Usamunya or kumuikira kumbuyo kungovomereza TB Joshua is also a human being
Zamanyazi
A prophet is a human being not all prophecy can come from God coz he is human whether u like or not TB Joshua is a man of God in addition l don’t believe he prophesied like that if he did let us believe is human being but believe that is a great prophet in the world
Kkkkk
mmmm,Asopan tafusani pa google akuuzani zimene ananena Tb
Wabodza uyu ndi a chslongo akews
Joshua Waloseraso Kuti Thini La Chimanga Kumalawikuno Lifika Pa K12,000 Mu December..
Comment Loading …………
Elijah Adapha Aneneri Onse Abaala Bcoz Of Bodza, Nanga Iyeyu Timutani?
Kkkkkkkkkk Ndiye mkuluyu kusonyeza kuti mumaganiza kuti nkumutani kkkkkkkk eeeee! Ndangidutsamo ine….
Dzimachitika
Khulupirirani Mulungu osati munthu chifukwa munthu amakhumudwitsa! Mulungu atayang’ana kudziko la pansi, anaona kuti palibe ndi mmodzi yemwe ali olungama. Kotero tonse ndife operewera ndithu pa ulemerero wake. Pamenepa sanasankhe kuti uyu ndi mneneri kapena ayi. Ndiye tikhulupilira bwanji munthu pamenepa? Chipulumutso sichidzaona chuma kapena kutchuka kwa munthu, mchifukwa chiyani azineneri ambiri ziphunzitso zao zimasamira pa chuma? Ambiri apa akhumudwa ndi ulosiwu kuiwala kuti iyeso ndi munthu ndipo ali ndi zofooka zakeso pa Mulungu.
Mulungu Akudalitse Ndi Moyo Wautali
Ukawerenge 2 Mbiri 20:20 kapena ukamvetsako zokhuza a neneri kukhupirira ndi nkhani ya chumanso.
Plz tikamawerenga bible,choyamba tikuyenera kupempha Mzimu Oyera kuti atitsogolere. Kupanda kutero titha kuwerenga koma osatolapo kanthu. Kodi mchifukwa chiyani Yesu za ufumu wa kumwamba adayerekezera pa tiana tating’ono? Kodi mchifukwa ninji Mzimu Oyera umaonekera ku anthu kudzera mu mbalame yotchedwa nkhunda? Kodi mukawerenga nkhani ya Lazaro waumphawi ndi Wachuma uja zimatiphumzitsa chiyani? Taonani Hanania ndi Safila adalonjeza Mulungu pa chuma chao mpaka kugulitsa munda koma chisoni sanapereke chonse mpaka awiriwo anafa. Kuti tipeze chipulumutso tikuyenera kudzichepetsa monga tiana,kukhala ofatsa mtima monga nkhunda. Munthu amakhala waulemu,ozichepetsa komaso kudziwa Mulungu pomwe ali osauka koma kungopeza chuma zonsezi amaiwala mkuyamba kuzikweza,kuzitamandira etc. Zotsatira zake timasemphana ndi Mulungu mchifukwa chake panabwera mau oti ndi kovuta munthu wachuma kukalowa mu ufumu wa Mulungu. Naneso ndine yani pamaso pake? AMEN!!
This devil he got lies, he think God is his brother I hat u
Zakumidima izi
Ndasiya mpingo wake wachulutsa bodza bamboyu.
Tembenukani ndipo mukhalenawo moyo osatha Landilani Yesu mumtimamwanu lolani machitachitaanu afanane ndi a Yesu mwana wa Mulungu! Kuuzimu kuli zochitika zambiri koma Zitengera kumvetsetsa ndikudzipeleka kwa wakufunakuzimva! Ndani amene adzapezeke dzaka 60 dzikubwelazi? Tifune tisafune kudzakhala tonse amene tikuwelenga uthengawu tilipansipanthaka kudukira chiweluzo ngati tingachitike mwayi mkatimwandimemomwemu Yesu akhonza kubwera kudzatenga(oyera mtima) mwai ukadalipo koma siokakamiza
Mmmm!This is powerful,,,thanks for the word,iam realy touched togather with my soul amen and amen,God bless u my brother
muli mbali iti?
this true,I like this words God bless you brother.
Amen!!Powerful !!!
Mpaseni frozy aziziritse ku khosi
Remember, naye satana alinso nd atumiki ake amatchedwanso maprophet,nde maprophet omwe akukambidwa apawa ali mbali iti??
Koma ndiyetu tiri busy ndiku states mmalo motanganidwa ndi mbava zoba misonkho ya amalawi.
Sananene kuti mulungu akuti Clinton awina.
Anthu mumamalephera kumvesesa sananene mukuneneramo plz kkk paja mumayang’ana zolakwika osati zolondola god must forgive the admin of this page
Amanena zamaganizo ake osati amulungu.
mistake imodz, kulira ndi zaka.
Aphedwe Tb joshuayo iyaa kkkkkk
We shudnt be worried about TB Joshua unfulfilled prophesy here. Donald Trump has won, congratulations to him and Americans for their wise choice. As for us malawians we are still stuck with our peter mutharika who is slowly but sure driving us to the grave. I hope DT will help africans drive out these corrupt leaders like peter mutharika.
Za ziiiiiii
Lembani zanu za nzeru.
Senseless
You say sensiless but u cant write something sensible urself
Pita iweyo ukalamulire tone ngat ukwanise. Chili kwa mzako osamasewera nacho.
Apa nde wandifika pamoyo,wayankhula zoona kungoti chilungamo chimawawa.
kodi izinso ndiye ziti a #synet? TB Joshua yemweyu?
Nkhani zake nzogwirana, Trump ananena kuti akazawina azathana ndi azitsogoleri obera anthu aku africa. He has won and hopefully athana ndi anthu ngati achina pitala oonelera katangale. Munthu akamabisa anthu akuba ndekuti iyenso ndi mbava.
I thought you are clever but the opposite is true.
kkkk ma coment enawa? akathana naye in wat way? eish,nkhan ina koma kuipotola mpaka ikhudze peter
Prophecy ya Yoswa yakhudza bwanji pitala wathu? Nayenso amapikisana nawo kumeneko?
Apange zakwao mxiiiiiiiiii
Pitala yamukhuza bcoz he is a corrupt leader, Trump will deal with these corrupt leaders. Prophesy kwa ife ilibe nctchito chifukwa analosera ndi prophet waku nigeria, zisankho zaku America. Ife vuto lathu ndi pitala amene akuteteza mbava za cashgate bcoz iyenso ndi cashgater.
ndikungowerenga nawo chonde siine olakwa
Mmmmm zinazinazitu basi chilichonse Peter chikumukhudza nchani pa nkhani imenei mulekeni munthu!
Kkkk once u write something about peter mutharika u attract lots of attention and replies. Koma ndipemphe nao kwa inu ondinyoza. I did not ask for ur opinion on this comment. Keep ur rath to urself.
And you are corrupt as Well, from Nigeria to USA, to Malawi…… Kkkkkkkk corruption at its best
Those who talk about just show how they fear him. There is no way trump can deal with other leaders. That’s a total lie. Akulephera a ICC. Iye ndye ndan
Trump promised regime changes of some countries in africa, i hope he will do just that in Countries like zim, uganda. Azatithandizeso ku malawi we lack gud leadership.
Synet wakamba mbwerera
Mr mkandawire palibe mbwelera apa. Ndakama zoona zokhazokha.
Pitala sazatheka mpake anakomedwa ku ameleca mpaka kuyiwala mbuyache ku ndata fam.
Pitala dziko likumukulira nchifukwa chake akungolimbikitsa katangale. Chitukuko ayi.
Adziwika ndi zipatso zake mtumiki wa Mulungu
malemba adalemba
Crazy talks, this is a human being were worrying about.
Kodi mulungu wayamba kumunamiza? He must only do Godly job not including politics. Theres nothing like that to the creater
Nothing to gain chisankho ndi cha Ku America, TB Joshua 4m Nigeria inu kuno Ku Malawi mungojijilika yet you your own problems to solve shame on you
Lekani mazgu gha Chiuta ghakuti ungabona uli chiswaswa mujiso la munyako apo iwe mwako muli chigodo
in case you don’t know America affects the whole world
fuck TB j ur a motherfucker
May God forgive you, you don’t the power to jugde, that belongs to God alone. You have been cursed the solution is repentance. Ur blind and you don’t even see or here what is in the spirit. Devil is behind your back
I don’t think so, ur sucking his Dick for shoooo
odi apa ndbamwa chibuku super ine…
Haahahaha!!! Anyambuti Muli kut??? Nthawi ya nkhondo iyi! !! Aneneri onyenga tithane nawo kkkkkkkkk.
Uyu amangotha kulosela malilo basi……Galu wapasi pa nyanja
May the Lord forgive you
4give u2!masatanic ngati amenewa nkumawaikilanso kmbuyo
Chiwaya. …
My God has forgiven Josua for his misleading prophecy….Mulungu sanama….sono wa josua uyu akunama bwanji
This papa said mr lowasa oposition candindate in tanzania will win the election, but nothing
Koma Ndiye Zawavuta Ambiritu Amene Amasewela Ndi Mulungu Pomazitcha Okha Alosi. Wabodza Buchiri Ndi Nzake Kuno Amamuti Makuta
Amalawi kodi tinakhala bwanji ? Basi paliponse kufuna kulakwitsa . Mumvetseleso ndiye mumve kuti anati chani . Ngati mukufuna popangila ndalama Koma ndiye zakukanikani chifukwa mwini wake wakumwamba akuwonani ndiye tsiku lina mudzayaluka ndibodza lanulo.
Wati uilembe mchichewatu cholinga anthu anyoze utumiki wa joshua mokukomera? Shame on u! Besides, palibe chavuta ku sunagoge
Pajatu analiseranso kuti president wa Malawi amwalira. …Peter
hahahaha odi ukoo ma prophet enawa chiletso ndthu
Kkkkkkk….Malawi News tsopano
Kkkkkkk sasamba uyu
May God forgive you.
May He not curse you, bt ruther be gracious to you
mind you! !! Readers of nowadays doesn’t chosen by God but the Devil
Zako izo.joshua ngati ali bambo ako wagwa nayo
That very true
If you vote then you are devil tiinnn
True
Munthu ngati analephera kulosera zakugwa kwa church yake nde akalosere za chisankho.ndipo amalawi nchifukwa umphawi sumatichoka kupepera too much.mmene zilili apa munthu nkumabakila joshua??? ¡aaaaaa zakuntoso basi
Zoonadi anthu akwathu vuto lilipo zinakanika a Mrs banda kuwina timawaona ku scoan koma alikuti manyazi
Tikamati analephela kulosela zake zomwe, tizikumbukaso kuti, nthawi ya Yesu ena anamuuzaso Yesu kuti adzipulumutse yekha ngati ali mwana wa mesiya koma sanatelo. Zinthu zina amadziwa yekha Mulungu ndizolinga zake.
That doesn’t make him a false prophet!, Tb Joshua is an anointed servant of God.Don’t play with men of God otherwise you’ll kindle God’s wrath upon thy very self. However, Jesus Christ loves u & HE wants to save your soul. God bless u!
zokunva nkumachuluka nzelu ndi usatana wanu.let us pray agaist …. thus the prophecy u dunder head
I will always like pastor Chris he always emphasise that everyone is an anointed as long as he/she has Christ Jesus he/she can do everything through Christ who gives strength…You are a prophet of your life————————–
Aneneri onyenga mmasku osiliza.
Some time to say bad kwa athu osakhika amulungu umatengerapoatemberero note that
Kaya sikundikhuza poti kwathuku kuchislam kulibe nyasizi mumat zaulosi timamvera kwainu koma munthu wanzeru sangaganize munthu akulephera kulosera zake zomwe ndiye akalosere zaena.kumaganiza pena pake
fake man of God.nde ena inu mudagundika like page lake ngat akupasani ma RAND KAPENA MA METICAL KAPENA MAKWACHA,apa mbiri zaulosi zamvuta and people will never trust him,adalosera zot by october to april malawi and zimbabwe will lose apm,so mene apm wathu amadwala timati mwina josua walotadi,ooo mulungu wanga,apm adati “no any person will cause his death.”and pa malawi 24 this story posted and mudamunyoza kwambiri apm kumati iye ndindani pamaso pa mulungu,ngat atumiki alosera that mean its from god,padali foto ya josua,bushir and wina wake nkhwangwala osaziwika bwino,lero president ali moyo,dzanja la mulungu lamukakha kt ayi mwana wanga bwerera,awo ndi asatana a josua and bushir,zamanyazi.so today same same fake story kkkk zachamba.
Comment Loading……. Kuwopa kulakwa?
Fake prophet
Ndikanakhala TB JOSHUA ndikananena kuti sumunave mbwino ndinati a wine ndi mzibambo osati mzimai, kutheka anthu anachita haki account yanga ndikusintha.
Most of people trust untrusted thing but me, I ‘ll never trust any person accept God
analephera kuteteza sinagogi yake ija mxm
Nde kuno muzitivuta ndi Chakwera kut man ov God ! Aaaa uyo namandwa kunama poyerayera kkkkkk
kkjjjk tb joshua mmalere ulosi kudutsa pansipa wasala bushiti kaya mmati bushuri kaya bullshit naye ayaluka pompano pompano anthu munyanya kutengeka
Usalimbane ndi anthu odzosedwa aise even nthawi ya Nowa anthu amkati wapenga koma ukulu wamulungu unawoneka
Nkhani ilipamo ndiya #TBJ chonde mulekeni bushiri asakukhuzeni ayi plz
eti kuphatikiza nkhani bwanj
afiti kuikilana kumbuyo asatana inu ana anjoka .mukalangidwa pamodzo ndi aneneri anu onyengawa.zitayani nthawi
Palibe woyenera mwa inu kunena ngat Tb joshua ali true prophet or not only God so dnt judge him kut ndiwonyenga
onyenga uyu tb joshua
Ma prophet ena nd by name stupit prophets #mustfall
Am not like to heal someone saying that #joshau is man of God,kodi iweyo ukunena iwe simuthu wamulungu?who are u,if u are not belong to god and where are u coming from.munthu wazelu angapite kwamuthu kuti amupephelele iye samaziwa kupephela kupusa kwa African kkkkkkkkk
Palibe Chimene Mupindule Olo Mtaipitsa Munthu Wa Mulunguyu. Anthu Oipa.
aneneli onyenga aziwika sopano mwazione samalani mungazaonongeke
Nde tikamati sibwino kukhulupilira ma #Prophet wa coz sionse omwe ali owona,lero ndiziti,,,,,ndizimenezi nthawi ikukwana yoti ma #Prophet onyenga ayaluke
Kodi Zili Chonchi Kaya, Ine Anthu Omakonda Kuloselawa Amandikayikitsa Kwambiri.
Iwe ndiwemunthu wonama kwabasibasi kudziti ndiwe munthu wa Mulungu.
people are worshiping devil ignorantly.
apa wachita bho kuyikadi chichewa…kkkk ameneyo wagwa nayo ndipo ma bp ashuta..alibusy anthu kumuyikila kumbuyo…yesu pamateyu24v24 ananena kale zaneneri onyengawa..pano olo nkhope ikuonesa kuti njamatenga Achikulile aYoswawo.mwina DJ wawinayo ndishemale pano.omwe mukumuyikila lumbuyo munali kuti pazana akulosela kukana kuti sananene..lelo zakuvutani.
Maso anga ninachonsa kwa azineneri ndikuyang`ana kwa ambuye yeka
Ndi verse liti limene limakamba zoti muziyang’ana azineneri osati mulungu mmmmmm munamatu inu
Maso pa Yesu basi ,enawa amangofuna kutchuka ndi kudzilemeletsa.
Ambuye yesu amandikwanila amwene
Maulosi Enawa, u dont have to believe???
Iwe joshua!! Ndi azilongo akowo…ndati ndikuuzen kut zomwe munachita 2012 chaka chino mulephera. ..kodi iyeyo Joshua ngt amaona zakusogolo analora bwanj tchalitchi chake kugwa anthu 90 mkumwalira….bwanj sanaziimise zimenezo? Kusonyeza kut munthu uja ndi wabodza kkklkk #hashtag_ndinamva_kanyamakaz_pang’ono
Kkkkkkkk koma yaaaaa
Kkkkkkkkkkk mavutotu amwene
Kakakakakakakakakaka ana apasi panyanja
Lero nde wapoila hub…..nsembe sizikuyenda bwino
Mulungu amapanga chili chose simulungu ameneyu odya sima wamupatsa chitsanzo mulungu kuti adziwe kuti anthu ali ndi munuwake
Mulungu Sapanganika Sijemus AI Zimachitika.
Ineyo sindimawamvetsetsa a Malawi ena amene amawatenga ma prophet ngati Mulungu komatu Bible limanena momveka bwino kuti masiku otsiriza kudzauka aneneri onyenga… Tiyeni tigalamuke
Akulu apa ndiye mwatipangisa mayazi basi
Komatu iyeyo salalakwitse zimach itika ndithu muthu kulosela koma zithu osachitika ndiye musaone ngati zachiledo apapa komaso ma vote sanaponyedwe ineso ndili mbali ya TB joushe yemweyo sananame ayi clenton awina ndithu
Sibwino kumupepusa Mulegi samalani man
Prophesy ya Mulungu salakwitsa & Mulungu salakwitsa.Zaonekelatu kut prophesy imenei siyochokela kwa Mulungu,munthu ndamene amalakwitsa nde a prophet anuwa alakwitsa coz mphamvu zopangila prophesy yawo sizichoka kwa Mulungu.
Munthu uyu amangufuna kutchuka ndie Mulungu wafuna kuwayalutsa akuluwa ndipo Mulungu simunthu.
Chiti muziwe ndi ichi munthu umalakwitsa kumene iyeyu sikuti amanama ayi koma pali zithu zina zomwe zikumuyenda pa nthupi lake ndithu ndipo tiyeni tinkhale tiziona zomwe zichitike kapena kuziva kuti ku America kwachitika zakuti muonaso
Thanx mwavomela kut iyeyu amapanga ma prophesy ake mu umunthu osati mu uMulungu,nde ma prophesy aumunthu its blasphemy.Pitani mu Bible lanu,simungakapeze zoti prophesy ya Mulungu inakanika.Mutaya chipulumutso pokhulupila mneneri onyengayu mmalo mokhulupira Yesu khristu mamuna wa mtanda.
Iwea vote aponya kale wawina trump iwe ukunena mavote ake ati sanaponyedwewo kkkk
Kkkkkkkkkkkk ndikuziwa kuti aponya kale koma muziona
zichaniso nanu a Prisca Kaya mumazitcha a priscilla!!…..zoti mumupweteke Trump apa ayi kulibwino mupange za peter munaloselaso zija….
KKK munthu pano ndi president @ prescilla..kkk
eeeee people mumanva chizungu kma???????? he said ‘i c a woman becoming the president of america,we should pray against that” nde wea a u getting that info yot amat clinton awina??? vetseranson prophecy ija!!!
It makes me sick wen people talk bad about Tb joshua ,,,they talk things they do not know
mudwaladi koopsa kkkk kodi iwe akamati woman analiko angati mawoman ku zisankho zaku amerika omwe anayimila???inu ndembuli wachizungu..muneneri waboza Yoswa mateyu24vs24 wagwa nayo…kodi ngati u prayed for that bwanji mapemphero anu athela munjila osakwanilisidwa…ngwabodza..ma bp akwela kumeneko mwakhaula.
eee anthu sazatheka aixe……kumango wamvesesa
tachokani asatana inu mumangoikila kumbuyo ndi satana yemwe. TB,joshua galu wa munthu
nemar kumanvetsesa chizungu mpaka tikalowe nklas zomwez??? tawelenganson ndalemba pamwambazo zkuoneka simukumva what am saying!!
Paja Ndiwe M’ngelezi Ife Akuda Mwinasitavese
Paja Ndiwe M’ngelezi Ife Akuda Mwinasitavese
Nde wachotseranji status yakeyo ngati zinali mmene mukuneneramo? Simanyazi amenewo?
Ukanenela konko ndi chizungu chakocho with your father TB…
Ma prophet akumidima awa kkkkkkkkkk
Apa wosanva chizungu ndi ndani?
I don’t believe in that midiocre prophet called TB his cheater
Amalawi chizungu bwanji??? kumalowako mma nyt xul,kumvetsetsa bwanj??
zopusa eti TB Joshua’yo mukukhala ngat agogo anu bwnji…ur backn em as if anakupatsaniko ya cupon bwanji??? eeeeeh kume amat Clinton awina.! hihihi nde bolaso mukana backila bushiri asopan Rather TB..chifukwa bushiri mukhoza kupemphako madzi akumwa kwawo cz ndiwakonkuno evn naeso mabodza too mch
Akuluwa ananama chizungu chosavuta kupembeza ziwanda kwavuta false prophets
TB adanena straight and kutsindika pa fb page yake kuti i see woman winning in US election with narrow gap.And status waifutapo,panalibe mawu oti we have to pray njeee and if you still doubting i can send you his status.
i hope u saw it from his real page. komanso if i heard emmanuel tv properly they said they dont communicate through Facebook
iwe ndiwabodza ndithu. ukuona ngat sitinawelenge ife? mbuz yanuyo mukapsa nayo. inaleka bwanji kulosela zakugwa kwa tchalitchi chake chija
Mbatama imenei I think ndiyakumidimaso pagulu osamaoneka ngati ozimdikila kwambili umazakhalaso chisiru chenicheni sindimafuna kuperekako maganizo koma zandikhudza kwambili masiku omaliza muzaona izi. …
wadilita comment yanga kkkkkk zakuwawa ngati Yoswa paja ndinu odilita eti ndemukukana chani…yakumenya patima wagwa nayo na Yoswa.
#Mphatso on fb was to inform other ppo who couldn’t afford to watch him on TV and it is him who wrote that massage on Facebook thats why he have deleted it.And it is not first time for him to tell ppo lies.He prophesied last month about Nyovest that ppo will die at Orlando stadium but nothing happened, why you backing him? the whole world knows that he have lied about election and this news is everywhere now.
thanks sopani wathandizira ndithu anthu amqngopanga makani koma osamva
Do not follow false prophets nor false pastor…The Punishment of false prophet and his followers is just the same
The guy Lied!!!!He said “I see a Woman president in U.S.A,we shld pray for it”,meanin Hillary ryt?Did she make it to the white house?No!!!Meanin he lied
kkkkk…..mwaga nayo ndika mtumiki kanuko
Kikikikikikiki…..amuchesula2, my uncle was telling the same thing what TB Joshua told the people about elections!
Iwe ndamene sunamve aise
Iwe ndiwe wabodza pray against what? Nde y didn’t he do so?
Let’s not bit around the bush
The prophecy was fake and he is fake
Iwe ndiye wosokoneza wakufikapo
Inu tisakangane ndizoona TP JOSHUA ndiwabodzaa, nanga bwanji amangochotsa utengawo umene anatumiza pafb???azipanga za Mulungu zinazo zasatanic kkkkkkk
https://m.youtube.com/watch?feature=share&v=zQGRQY6ke_M
It doesn’t matter how much you will try to back your con man, he lied and goofed big-time and there is nothing you can do about it! He never said anything about praying against it. The clip has just proved to you that you are liars trying to justify a lie. Hahaha zavuta ku SCOAN!! Sorry blind followers!
panga search pa mugabe quotes alka video yake umvetsetse
A Luhanga mbwelera. Why goofing? ” I c a woman… ” , is Hillary a man or a woman?
Watch again on Youtube adha. Sananene zoti pray against that…kkkkkk I watched it again n again coz even himself he was bluffing
Wamkonda chabe mtumiki wakoyo, ife tingoti pepa wakukhumudwitsa, tsiku lomaliza adzakukhumudwitsanso chimodzimozi . hehehehe! Uluuuu
ndinapanga chisakho chosata YESU poti iye ndi choonadi,njira ndi moyo, my bible assures me so.
no matter what pple say against the man of Gid but note that, this cnt change him so dont waste your time saying bad things about him kuopakuutsa mkwiyo wa Mulungu.
Watch out prophecy has no time flame. You can dance today and weep tomorrow. The holy spirit does not lie. One day a woman shall take charge of USA. Dont blame this man of God.
choka iwe sukulu yake unapita iti.worsted sperm.
#wellington nowa there will be a woman president as well as Chinese president a Latino president any one can be a president to claim to prophecise that is dumbness.
ine nkhale mbuli pa izi
Masiku omaliza..osamawauza athu xachipulumutso bwanj
i dont beileve hes deeds.#zambia
Wa 4nkong uyu
Munthu wamulungu wachita jenkha ulosi utabaunsa kkkkkk koma yaa.
Apa akanangolondola akanasanja koopsya anaimwaza kutekeko kkkkkkkkkk iiiiiiii kuba mudzina la Mulungu
Mulungu sana kuteleko mulungu amangofuna kuwaphunzisa akuluwa kuti palibe amene amadziwa za mawa. Tsibwino kutengeka ndi anthu ngati awa mudzakhudwa koma Mulungu sakhumudwisa.
Tili masiku omaliza even bible linanena kale
Mulungu Si Tb Josua
Amwene awa anayamba bodza
Comment Errer
TB? wabodza uja.
Paja amanena zowona nda mbuyako
He is not a man of God.Mulungu waonetsa ukulu wake.
kkk! zavuta zavuta basi!
Wachinyengo amenei
NDIYE CHANI AMATI TB JOSHUA NDI MULUNGU NDANI MWASOWA ZOLEMBA ETI KAGWERENI UKO OSAMALIMBANA NDI ATHU A MULUNGU ALIYENSE MUMALIMBANA NAYE OLO ATABWERASO YESU KHRISTU MUZALIMBANA NAYESO GO TO HELLL NDI NKHANI YAKO YOPANDA MUTUYI
zimachitika
Zavuta
Kma Yaaa
kkkkkkk, i dont understand people esp ladies who believe this asshole
Mulungu siJames
ok dziko lapasi ndimene limakharira sindikuwonapo chachilendo apa