The Malawi national football team, the Flames which travels to the Cecafa tournament to hosted by Ethiopia from 21 November to 5 December will play Sudan in their opening Group C matches on 23 November before facing Djibouti two days later.
The Flames’s final group match is on 27 November against South Sudan. Sudan and South Sudan are set to play each other for the first time ever.
The current defending champions Kenya face 13-time winners Uganda in Group B, while the host nation will open the tournament against rivals Rwanda in Group A.
Groups in details
Group A -Ethiopia -Rwanda -Tanzania -Somalia
Group B -Kenya -Uganda -Burundi -Zanzibar
Group C -Sudan -Djibout -South Sudan -Malawi
The games will be played in Hawassa and Bahir Dar.
I wish them all the best during their games
I wish them all the best
Sudan idya monona
Akaluza
Sudan Woyeeeeeeeeeee Malawi 0-5 Sudan
Tikukufuniran zabwino,muononganso ndlama zambiri, komamukakaluza mukakhalekonko,osamangotchuka mom’muno,tatopanazo ife.
chikho anapita cho kim splisble
Bola tizikawina kumneko
za ziiiii
Koma djibout yakatiwina basi ntchito yita wina
Mukaluzenso
Kodi team yake ndi yiti mukuyichemelerayi? Flames kapena smoke?
tikango winako Djibuti yokhayo
Kodi guyz mtawariyu frank banda ndi swine sawatenga chifukwa chani
Koma tikawina
Coach mtawali here is my first eleven, goalkeeper(chipuwa R) 2=sanudi s,3= Fodya Y, 4=Lanjesi/kabango, 5=mkandawire s/mpachika c,6=kangunje N/kaira c,8=Mkacha H/ J phiri, 7=cj banda/kaliati I, 9=kaonga c/Linje J,10=chiukepo m/kuwali s,11=D Sailesi/chester y.
subs
zonda p
Gabeya m
chester y
kaira c
Jerard p
kaliati I
Kuawli s
Linje j
tough team
koma ndiye Sudan ikatikwapula
khulupililani tiwina kwapita mapuleya ovuta moga pita muthalika puleya mbambande tiwina
We gon lose …amalawi olo timu ingaphweke bwanj timayesesa kuloser bas
Point of correction: nyamilandu national team
Djibouti ndie izatibandula
wadusa pompa ….. ayesa tidya moni ife
Titenga chikho bas, matimu ovuta sanapiteko kkkkkkk
Mukanangotumiza Bullets mukanaona ikanakabwera ndi cup!
bwanji sanatenge peoples team(bb) kuti ikaimilile flames, heee
kkkk amalawi tingovomeleza kut mpira simbaliyathu ma playerz onse mwanenawa miyendo yonse nd yaku left ndye mpira amenya bwanj?? komanso mwina tiyeseko striker uyu: pitala muntharka
Kkkkkkkkk Paja ali ndi jeas ya no.9,yomwe anatenga asammoa gyan atabwera eti? kk ulamuliro wamukanika angoyamba mpira basi mwina tiziwina kkkk
kkk coz mutu umene uja utaheda mpira gole sangauone
chisalowe chi pitalacho::::paja amamenya wa mapazi kkk
nkhaniyi ndi peter zikugwizana bwanji?
a #thom nkhani ndiyakut chi pitala dziko likuchivuta kuyendesa ndye atayesa zina bola like soccer coz kkkkk ya
Aaaaah mesa mumati National Team yatha
Uku ndye Flames ikabwerako chabe bola ndalamazo boma linakagulila Kalongonda ndi2
flames imakhumudwitsa!
Kod national team ilipo?
Myne z a question is Chikondi Magalasi your reporter? If so nanga za cecafa snubs malawi wadzitenga kuti! Is she/he still in attatchement kapena mxxxxxxxxxxiiiiiiiiiiiiiiiiii mutisokoneza u want to bring kugawanikana mu province yathu ya malawiyi eti
Am wishing my team to become victorious there.
Macoach apa Malawi ambirimbiri mpaka osewera kuma coacher
Zachiziwikile iyaaaa
Its very unfortunate to see sudan in our group,,l doubt if we are going to make it
Eeeee tiguliretu panado et paja timu iyi imatipwetekesa mutu kumangokhalila kuluza bx
kkkkkkk! koma iwe!
Adaitana kala squad
atleast we got jibuti coach can smile,,,,,poor selection of players makes #flames to poor peformance living players that are perfoming in the ligi is just another stupid,,,,,silver is in number 3 in ligo tble but non of them in the flames,so mr coach you think number 3 comes from heaven kkkk
Martine squad ili ku camp inatuluka komano yomwe ipite paja amadikira performance yawo ku training nde kuti next week
Squad atchula liti tiyione
http://malawi24.com/2015/11/09/27-players-into-flames-camp-for-cecafa-cup/ Open that link Martin.
ok
We gon lose …..we always do
You said that they have been snubbed and not you say they will play which is which. Do you verify your facts before posting them.
All The Best Ma Flamez
You are always failing us, guys
Nde mpaka aluze ndi Djibouti? Osatibweretsera mbale kumeneko, tkufuna chikho….. O de best Flames
Open Cheque
but we must win this matches