As the economic crisis continues striking Malawi, Illovo Sugar (Malawi) Limited has been forced to hike its sugar prices by 10 percent in response to the depreciation of Malawi Kwacha.
Confirming the development, Ireen Phalula, Illovo Sugar Limited public relations officer told the press that Malawi Kwacha has depreciated significantly since the last price adjustment last year hence the increment.
She explained that the weakness of the currency negatively impacts operations of the company since some of its production inputs are imported from abroad.
She also explained that a weak currency impacts key inputs and any imported expertise required to complement locals in maintaining the factories and overseeing agricultural operations.
With effect from Monday, 50 kilogrammes (Kg) of brown bulk per metric tone (MT) will be at K495, 900 ($886) and K28, 886.18 ($52) per bale while white bulk will be at K508, 300 ($908) per MT and K29, 608.48 ($53) per bale.
Consumers will pay K506, 500 ($904) per MT and K11, 801.45 per bale for 20 packets of brown pre-pack at 2 Kg and K504,100 for white pre-pack per MT and K11 745.53 per bale for the same.
Vuto la amalawife,timayiwala nsanga
These are last days as writen in the Bible,ogulitsa adzasangalala ogula adzadandaula!
Zawo Ndi zimodzi away Ndi malemu bolansotu amayi sugar adamutsitsa
Kaya ZANU izo komko akakhala abale anga za ilovo adasiya kutsekemeretsa tea wawo amangomwa hullets.sugar waku southafrica
basi tea tasiya kumwa tizithila dothi
Mmmm kuli konse zinthu zimakwela mtengo basi chilichonse kumangodandaula
tiyen tisawse makap
Galu uyu
This Malawi taste good to peter and cabinet ministers and M.P.s but not to us as local people.
Kamuzu akulamulira sugar unali bwanji?
its like stepping on an injured toe..Malawians are already injured economically and you are raising the price of sugar….What do you want Malawians to do know?yet you know that many people in the country live below the poverty line.Thats being selfish
??? dont forget thats a company. Which has employees and it also needs to make a profit
thats selfish reasoning ..the fact that u can afford to buy it does not mean anyone can do so..If a packet of sugar is @ 700 something and many Malawians live below poverty line which is less than a dolla which is 520(not sure)how will they afford it???
BOMA ILO
Dowry Guys ndikuyetsetsa…..kusintha zithu…..
Zosa ndi chifukwa cha mec sanaganize kuti a malawi ndi anthu ovutika polengeza kuti dead people party (dpp) ndiyo yawina mulungu akuwona mnene .mtundu wa malawi ukuyenda mnyengo yowawa.
mubwira mitchenga chakachino ku mw kwanuko
Aaaaa tseee mukamakhara anthu olemeranu dont think that every one is rich as you are ok taganizira anthu akumuzi mwanvaaaaa DONT TAKE ADVANTAGE ON POOR PEOPLE remember moyu siwokharisa evryone wu die whether you like or not
Iwe munthu iwe siwudziwa kuti pa mitengo ya zinthu boma limayenela kuyang’anapo?
Koma sugar kukweza mtengo,koma malipiro a anthu anu ogwira job osakweza.pangani mwa kufuna kwanu ndani angakuletseni.
Tinalakwitsa kupeleka boma kwa matchona.
ndiye ati azimwa tea ku Malawi ndiangati/kachasu? coz nawo ophika kachasu akwezaso.
shugar kumalawi ndiotchipa patheba tikugula 1kg 18.50cent ndie muisukunule ndikwacha mupeza kuti itha kumapyola 700 ndie sidzachilendo ndi world wide ndie poti kumalawiko zimabwera mochedwa mkona tikuona ngati zachilendo
Ukunama
sindimalimbana ndi mbuzi
1kg pa theba nd R13
mbali yomwe uliyo mwina komanso mitengo imakhala yosiyana mmashop choti uziwe nchimenecho
mmmmm nde tiximwa tea? jst imagine pea nut sarries
tsekani company shatap
Mwina moyo winawo zidzayenda
Mavuxx pa mpanje shaaaaaaaaa!
Ulamulilo waukadaulo umenewu DPP umakwana kweza chilichonse
Diesel Petrol Palibe DPP,Ziyambanso koma amaliza term yawo abwanawa?
illovo sugar company kkkkkkkkk basi zavuta siyani kupanga suga anthu adzidya mizimbe coz every day sugar wakwera eeeeeee anthu alibe ndalama komaso kukutetha tea sakoma wakwera muthawi yake ife tikudya mango
Masiku otsiliza,ngakhale bible linafotokoza momveka bwino kuti ugulitsa azasangalala koma ogula ayi ndinthu.
Tati uzani 1kg sopano koma yah
kusonyeza kuti ku Malawi sugar ndiotchipa kusiyana ndikumene kuli ine kuno.
Mavuto tilinawo ndithu
mwa wanthu kasi tikhalenge uli kwambula tiyiiiii. hawe ise chitima.
This is not a surprise to us.We knew already about this.Government will put a blame on JB.#DPP must fall.
Magesi,transport,sugar,madzi,school fees,passport,driving licence zonse kuzakwela koma salary chimodzimodzi mxxx!
Kenako tinva kti Fuel wakwera nawo ma land lord akweza nyumba zao.Tikuyenera kulimbika kupemphera kti mwina Mulungu atichitire chifundo.apo bii zovuta.
Where is our country heading to ? school fees has gone up,Medical bills , Transport fares everything is up eish. No hope for DPP.
Tingopempha kwa mulungu ngati tinalakwa atikhululukile
Lusungu wanawangu tea amwengicha suga wajumpha ndalama ya dendi kkkk
Ndalira A Kamuzu $ Timapikisana 1 to 1
Guyz zovuta izi
Now by 10% it will cost how much now .Mwk500.00 or more ? Mavuto alipo.
kuno tikumagula K650 nde zikhala zingat pano ?
KOMA kumalawi zithu zavuta
Its Dpp Dont 4get Kunya Kulipo
does dpp manufacture sugar?
U Kno Nothing Chapangitsa Sugr Akwere Ndi Cha? Ikanakhala Kut Kwacha Ili Ndi Mphamvu Sugar Akanakwera?
Ndizomwe anthu amaembekezela zimenezo.
ndiye sitimwa tea zachamba et
Bora mungoiseka campaniyo gyz