Digili, kapena mteleshede? Dan Lu, Lombwe akusambulana uku
…Lombwe akuti nzakeyo anakhomera ku dowa “Lu-Lo my vote”: Kuli kusambwadzana za mkabudula uku pomwe mtsutso wa ubwino wokhala ndi digili kapena kungokhala ndi chilembwe basi, wafika pa mwana wakana phala pakati pa oyimba Dan… ...