Ogwira ntchito zaumoyo awopsyezanso kutengera unduna ku khothi
Gulu la anthu ogwira ntchito zaumoyo omwe sanalembedwebe ntchito, awopseza kuti apitilira ndi ganizo lawo lokasumira unduna wa zaumoyo pa zotsamwitsa zomwe zinachitika pa ndondomeko yolemba anthu ntchito ngati undunawu suwalemba ntchito nsanga. Nkhaniyi inayamba… ...