Siyani musatchetcheso chimanga kuli njala – boma lauza khonsolo ya Lilongwe
Boma kudzera ku unduna owona za maboma aang'ono, umodzi komanso chikhalidwe lauza khonsolo ya Lilongwe kuti isiye ntchito yotchetcha chimanga chomwe chili m'malo oletsedwa ponena kuti kunjaku muli kale chiopsezo cha njala. Pomwe m'dziko muno… ...