‘Tulutsani wanuyo timuone: ngati ali nkhalamba, ife wathu ndi mnyamata’ – wakhazikitsa chipani Nankhumwa
Kuli kanthu mu 2025. Chipani cha People's Development Party (PDP) chakhazikitsidwa tsopano ndipo a Kondwani Nankhumwa abwela poyera: iwo akutsogolera chipanichi ndipo 2025 akulowa m'boma basi. Inu mufune, kaya musafune. Poyankhula pa mwambo okhadzikitsa chipanichi… ...