M’phunzitsi adya ndalama za ophunzira 17 za mayeso a sitandade 8
Ophunzira okwana 17 ochokera pa sukulu ya pulayimale ya Chawe m’boma la Chiradzulu, ali manja m'khosi pomwe zadziwika kuti salemba nawo mayeso a sitandade 8 kamba koti mphunzitsi wina pa sukuluyi anawadyera ndalama yolipilira mayesowa… ...