Tchimo kuzuza: Namadingo abisa botolo la mowa
Yemwe anayamba maimbidwe ngati oyimba nyimbo zauzimu Patience Namadingo, watekesa pa masamba anchezo kaamba ka kanema yemwe akumuonetsa akubisa botolo la mowa. Kanema ina yomwe anthu akugawana pa masamba anchezo ikumuonetsa Namadingo ataima ndi mzake… ...