Adindo adandaula ndikusowa kwa zipangizo zochotsela zinyalala pa msika wa Namadzi
Adindo ena pa msika wa Namadzi ku Chiradzulu adandaula ndikusowa kwa zipangizo zochotsela zinyalala monga mawilibala ndi mafosholo pamsikawu. A George Mkwate m'modzi, wa mamembala a komiti pamsikawu wati mawilibala, mafosholo komanso zotchinga kukamwa ndi… ...