Aphungu avala ziguduli ku nyumba ya malamulo
Kunali chipwilikiti ku nyumba ya malamulo lero pomwe aphungu otsutsa boma anavala mayekete, madilesi ndi mabuluku opangidwa kuchokera ku masaka ati pokwiya ndi ulamuliro wa Lazarus Chakwera. Malingana ndi aphungu ena, iwo anaganiza zovala ziguduluzi… ...