“Mukanamva ndamfera mu ring’i!” — walira wankhonya wa ku Malawi atagagadidwa ndi zibakera ku Zambia
Mkwanda (L) Mawu a malemu pazisudzo John ‘Izeki' Nyanga oti ‘zina umangowona waziyamba' akuyankhulidwa mobwelezedwa ndi anyamata atatu osewera nkhonya mdziko muno kwinaku akuziguguda pachifuwa kuti unkalinda izi moyo wanga? Kaamba ka zibakera zomwe agagadidwa… ...