’Pano’ ndi Driemo

Chuluke chuluke ndi wa njuchi koma umanena yomwe yakuluma, a Malawi ochuluka awonetsa kugwa mchikondi ndi nyimbo yomwe yatenga kale malo ’Pano' ya Shaffie Phiri yemwe amadziwikaso kuti Driemo. Munyimboyi yomwe ndiyachikondi ndipo yatulutsidwa la… ...