Bushiri amangidwa
M’busa amene amaziti ndi mneneri Shepherd Bushiri analowa mchitolokosi cha a Polisi m’dziko la South Africa usiku wa loweruka. Bushiri amene akufufuzidwa pa mlandu okuba ndalama ku South Africa kuti azizabisa ku Malawi kuno, anaitanidwa… ...