Wakwiya ndi mfiti. Amene sakusangalala pano ndiye mwina ndi neba basi.
Kuli chisangalalo ku banja la nyerere. Ku manoma lero amwa wamkaka, kusamba wa mkaka ndipo chilichonse kwa iwo chili tayale.
Patatha zaka khumi ndi chimodzi, lero nyerere za manoma zaphulapo ligi ija imene pena imaoneka ngati neba atha kuwaphumitsa.
Pa masewelo amene anachitikila pa bwalo la za masewelo la Balaka, nyerere zinaonetsetsa kuti zisasunge mkute kuti zizamalize sabata la mawa. Zinali za papsa tonola basi.
Ena amakhulupilila kuti mwina anyamata a Masters Security ndi kuchitapo chamuna lero ndi kuphumitsa nyerere mwayi wawo koma zakanika ndithu.
Zigoli ziwiri za mnyamata Peter Wadabwa, chimodzi chochoka kwa Foster Namwera ndi chimodzi china chochoka kwa njoka Esau Kanyenda ndizo zatseka mpikisano wa ligi lero.
Manoma anapita mu masewelo akufuna ma pointi atatu basi. Ndipo atatuwo awapeza atakhoma Masters Security ku Balaka.
Ngakhale anyamata a Masters Security anakokela umu ndi umu, kuthilamo ka chigoli kamodzi koma ngati ka thumba ka mchere kothilidwa mu nyanja yaikulu ya India sizinaphule kanthu.
Pamene oyimbila amaimba pinto kuti mpira watha ndi pamenepo pamene opambana ligi anadziwika kuti ndi nyerere.
Umafuna anene chani?
Nde take imeneyo good team must take the league
The blues 4 evar
Eeee nkhuku yodulidwa chala agwira ntchito
Thank U for being champions this year.Am wishing U all the best in Champions League.Am aBB supporter.
11 years kuchigubira komaso kutenga movutika kwambiri neba kkkkkkkkkkkkkkkkk!!!!!!
Mbuzi
Palibe akunena eti
bola,
Chipepeso
WAKULA NEBA 11 YRS NIPATALI OSATENGA LIG KOMA MWENZE KWAMENE UKO KU MALAWI? 11 YEARS OSATENGA LIG KUNO SITILUMVETSA KOMA BB NIMORE FIRE INE ONE THOMZY CHIPATA ZAMBIA MAULE MULIBWANJI?
Mmmm great
NBB MANYADZI BWA?! (WIA THE NOMA FAMILY) KKKKKKKK!
Kkkkkkk wanderers have performed wanderers …sorry neba angotsogola chabe chikwama ndi chathu adathera pa# 2.
Search me @ http://www.11yrs.com.
Noma yachotsetsa over stay Ku sulom
zabhobho basi but don’t stop kupemphera guys bcz I taking league with mulungu
nomadz for life
Kkk yose bho manoma neba adzipsa mtima
Nyerere manoma enanu mukunama! Garason Gerald Jah Man Jonathan Genesis Franklin Loftus-cheek Chitenje Lloyd Mzeke Simion
nyerere zikumva kukoma
ULAKWASO ANOMA UKUPATSAN MWAYI SILVER IDANGOKUSIYAN KUT MUTENGEKO CHOFUKWACHOT LUCKY MALATA AMADANDAWULA MUSAMALE MWAYI NDAMENEYO
Akuti shame on them. Since 2006 Agima ali form 1
Cathy Ngulu wapsa mtima
Angoti noma woyeeeeee
Kumva Kukoma Heavy
Wayenda Mchipururu neba, dzaka Eleaven simasewera, Izopadera Koma Neba Zake nde Zayela, Ndipo Zake Ziri PABWINO.
neba wapsad mtima
ligi yomweyi mpaka kuzumza mkhuku yosalakwa
Mumamuvela peter 40!???
kkkk bro mulipo eti
Eya ine ndilipo ndifuse inu? Kkkkk
aaaaaa kuesa ķuthamañga big
… once God say yes, nobody can say no. Aaaah aneba, bwanji? mutiyankhulitsa pambali tu inu…
Ma fillllll NYELELE WOYEEEE
Nyerere ndi fire.
Nyerere ndi fire.
Neba wakwiya
Kuno onse zisoti avula. Ulemu kwa manoma. Akutiso kuli zaka seven kusogoloku Manoma Akutenga izi mosatizana. Koma ena akumayankhulaso za Neba.
Ati zikuoneka kuti wasala pang’ono kufika pa white Eagles. Sure.
Nyelele yomweyo kut wawawa!!!!!
Zaka 11 zikungowoneselatu kuti teamyi ndiyaying’ono
Sing’anga uja ati mmuyenjezere ndalama munampatsa IJA wainyanyala ati yachepa
Kkkkkk iiiih koma the hatred in these comments…ayayayayah!
Neba wanvadi pain!
Nzopweteka mai makamaka ikakhala team ngati imeneyi kuti isatenge kwa 2 yrs ngati zachitikilamu even kumangalandeko Man U panopa ili pa vuto masapota awo mngokwiya zedi malingana ndi momwe zikuyendera. Chinanso chofunika kwambiri kwa masapota nchoti adzidziwa kuti iyi ndi league and pamakhala ma team 16 or over and onsewo aim yawo nkutenga chinkho so asamadandaule kwambiri ndimasewera awa
Kkkkkkkk koma yeah munayisowa Ligi mpaka pamenepa ayi musanyadile kwambili 2018 tikulanda zimenezo ife
Zako izo ife ndiye tiri kale mu Canaan
Neba wachita bwino kutenga league,Amuna titasiya kuvala ma pantie pano tikuvala ma boxer short kkkkkkk and atsikana atasiya kuvala ma half pitcoat Muhahahahahaha Neba
Inunso ni a Noma eeet?? I thought you were suppilosed to be neutral as a page,,,, how will you post then the victory of the so called Nebaa,,, Shame
Kaya balalatilanani ine ndili pheeeee pambuyo pa ma Bankers
Musatisokose ndi ligi yotenga after zaka 12! Kkkkk
koma manoma inu… aaaaa
“mwina wakwiya ndi neba”that is bad reporting.
Mutengenso caf
Kumva kukoma, wankaka tikumwa
akuti sing’anga wa kumchinji amadziwa ncthito yake
Wakwiya ndi mfiti bas
Congrats Nyerere it has been along way you deserve
11 Yrs Fc
Stand up for the champions. Season yamawa ndi ya Nomanso. Chingambwe bullets inatha
AKUTI AFTER 11 yrs from std1 to form3
Akuti noma imadziwa kulera mpaka 11 years
Chikwama adatenga ndi mwini ulendo.
Nebayo źimuwawe
kkkkk ndi mfitidi, komanso mfiti yake yotamba masana
Agogo fc awona mwana koma ndiye kwatelera..zamanyazi uchembere adathelatu mpaka 11 years osawonako ngakhale wadiso limodzi..anyway congraturations! nomadzi family being champions elect.
Kkkkkkk uzingothera pa number 2 Neba sorry ukumva phain
after 11 years ayi ndithu congrats…mulaweko chikho
champions elect???? 100% not correct.Edit the post coz sanachite kusankhidwa as in election, pls
kkkkk ine wamaule koma elect mupakana mumachita kuvota bwez team yanga yitawinatu bullets
Mukamba za 11yrs kafuseni a Chelsea anatha zaka zingati
Kanyeleni Dzikhumba, paja mwakhalitsa osatengako ligue eti? mpaka za 8? tnm yophwekai??
Kulila uku neba
Kulila kwa chani? mukukhalangati mumapikisana ndi bullets yokha bwanji mu ligiyi
Uku kunali Kulira kwa namfedwa zikomo
after kalela 4 11 yearz mkumazitolela mogwilitsa ntchto mikodzo ndi mafuta a nkhumba
Congrats neba!!!
kkkkk ife kwathu kuno akuti Master security ndi ana,
ndikanapanga delete account yanga tikanapanda kutenga chaka chino… if it breaks your heart go and dry up the sea…nyerereeee,!! boma ilo…..
mmm kusangalala kokhakokha wakwuyad ndimfit kkkkkkkk
maka ichi amati Chi Williams Banda nde chagwa nayo chilibe ndi manyazi omwe
Malawi24 sikuyenera kunyozedwa lero page iyi ndiyanu ndipo admin wa page iyi sanasangalare. Titapatsidwa ma game otsogozana timkadandaula ndi page yomweyi idayambitsa kunyoza inu mkumathandiza kuchokera pachiyambi pa league page iyi sidalembepo nkhani yabwino yaife ndiye ngati ndikunyoza munyoze ife chifukwa next season tikuonani muli limodzi mibwebwe inu admin tikudziwa kuti zakuwawani kuti league yatha chonchi koma paja ndidanena kuti chaka chikakhala chokolora olo utadzala gaga umakolora chimanga
Wakomoka neba
So , battle for the League still continues
SULOM has nullified the results of Noma game today. Breaking news
Zoona??
Guyz ngati tilibe comment kungosiya osalembapo kathu social media singakudandauleni kuti simunalembe mpala kutukwana zocheza zomwezi iiiiiiii koma yes yes mwakulira kuti?zampirazi mwaziziwa okulakula kapena?
Ife kuno ndichisangalalo basi noma moto moto.
Neba akwiya ndichani popeza chakachino wakolora kale palibe anganyadire mzake aliyese wakolora
Nkhumba fc.matama. 2 much. Umapanga fumbi.amakonda aliyenxe.
WOYEEE NOMA
kodi migwanya ya bullets muzavomereza liti kkkkkkk amzanu akupita chisogolo nde zikuyabwe2 usova
Chaka chanu a Nyerere ozaaaa!!!!
Wankakaaaaaaaaaaaa basi
Choka iwe admin amasangala choncho ulenala eti zakupezani mutakula kale
Noel Aonenji Nkhoma
Akuti conglats mwayandikilako ma banker
League ñdiye mwateñgadi after 11 years koma musamalimbane ñdi bullets, size zanu ñdi achina Mzuni, Masters ñdi Dwangwa.Moñgoķumbutsana; super league bullets:13 times Noma 6
Kutenga sikovuta koma kuchiteteza
Lets agree malawian football is low Kanyenda was not perfoming well in SA but here regarded as a star kkkkk shame country
Amene zamunyasa amwe paint basi!!
10yrs plan! conglax noma!
Dzuko si lero,noma yawina basi
Akuti zaka 11 zachuluka zedi,zangoonetseratu kuti mpira umawavuta
After 11 years neba keeping up
Amalawi tidakhala bwanji? Tiyeni tidziyetsa kupanga zathu ndimene zinthu zathu zikuyendera, tikambe ndimene Nyerere zachitila bwino pa league imeneyi osati neba no! Noo! Neba watani sizokwiyitsana
Mwana wazaka11 ujasopano ayamba kuyenfa
Mwana wa zaka 11 ndiwakulu
NOMA YOMWEYO MOTO KUTI BUUU, CHAMPIONS.
Ukamati wokwiya ndi mfiti mmm nesa ndiwo mpira
Paja mwana akankhoza kumene kuyimba linkhwelu amayimba mkutulo komwe,ndiye zachitika apazi.kutenga league kwanoma chaka chino kuli ngati kutulo ndiyenela kuwawata kwambiri,koma musayiwale kuti mwankhala mukunthela panumber 6 zaka zambiri bullets ikutenga league koma bullets simakunyozani!!
Yaunami yereyo njomba!
Koma ndiye, amalotadi alindi anzake akusewera. Ndiye ndizimenezi, kutereku akuwona ngati alowa ufumu wakumwamba anyapala amenewa.
mumanyoza koma kuti fb inali ndi anthu ochepa . komanso inu munatha dzaka 8 osatenga olo charty imene,mpaka munadikira kufika kwa gabadinyo muhango kuti mutenge muyambenso kutenga zikho
Ndine wa BB koma zabwino zonse kwa Neba,Enjoy and we will meet next season.
Iwe ndie munthu!
Wakula neba usiye kukodza pagolo komaso usiye kunyoza BB
Awinira mankhwala
Mukaswedwa mu CAF tikuonani kuti mutani.
Congrants neba all the best
#palle fun#
Mudikilenso 10 kapenanso 15 zaka kuti muzamveso fungi la lig
Aaaaaa kodi ka page aka ndi ka noma Eeeeti ndikatula kachikape
Kampopi kumvetsa chisoni,,,musachulutse zokamba apa ingovomerezan kut anzanu awina mukanakhala inu mtown mukananyasa osat sewero nde pot ndaanzanu mwat munyoze,,,,hiyaaa chikho tatengabe no matter how you talk
who cares za noma?
Wakwiya ndi mfiti
neba deka adzanu anatopa nadzo
Nyerere zokha nzomwe zimakwanitsa kutenga ma cup awiri kapena kuposera apo, koma sitidakhalepo osatengako chikho. Choncho, this year’s strategy was to grab super league and not a cup.
After 11 agonizing years hahaha
Ndizampira Izi Mpaka Kutukwana ?Umenewu Ndiwuchitsiru Ngati Sindiwe Sapota Ungoreka Noma Inyade Rero
The best team of all times is manoma
Nyerere for life
Zampira izi ndine wa #Bullets neba watenga basi tonse nga #Blantyre palibe zonyozana ingosangalalani basi osati kunyoza #Mapalestina iyayi Zampira izi zimadana nkulalata
Aaah zaka 11 nde munthu ukataye nthaw ndi kumukwiira neba….muli class imenei inali mbuli mapeto kapena tinene kut mbutuma kkkkk zabwino zonse gogo wanthu noma wayamba kukwawa pamenepa hahahahahahaaaaaa
Vomereza inu inu otherwise Bullets inapita ndi Atcheya Muluzi basi
Mbuli ku Malawi kuno ndi za noma plus nbb y mukulimbana Malo mosangalara,, all day are not Sunday
Heheheh….all day are Sunday yomweyo
Munthu wa nkhaza amadziwika ndi malankhulidwe ake kutenga league Kwa Noma mpaka kuisandutsa mbuli, gogo ine ndakululuka ndi malankhulidwe oipawa ndikudziwa ena amangozindikila atayankhula udyo chifukwa cha mkwiyo
Paja akazi abb amakhala oduka mitu amangolakhula zopepela
Walasaaa walasaaaa #Grace ???? truth hurts!!!
exactly #sadick
Kkkk olilara satola mau
Admin wanzeru ndimaona ngat sukuziwatu zot neba wanga wakwiya moti lero mr Lipipa sanadye msima
Akazi
Kkkkkkkkkk koma nebayo akuva bwanji muntimamo kkkkkk tikasambe ku nyanja. Christmas imeyi. Noma ndi Tim ya fuko kkkkk!!
Maule Sangakwiye, Noma Mpaka Zaka Ten Olo Kutenga League, Amamvetsa Chisoni Koma Mpira Sumakoma,,,, Maule Maule, Every Year, Tipumeko Nafe.
Dont You Know Dat In Football there Is One Winner We Have Already Congratulate Wandrels.
Lastly Malawi 24 Ur Idiot
Abullets uchifwamba kunyumba kwa kamwendo nyerere kuva kukoma mwemwe mwe Nyasa nyani bullets
Abullets uchifwamba kunyumba kwa kamwendo nyerere kuva kukoma mwemwe mwe Nyasa nyani bullets
Kuno akuti yatengako after zaka 11 pa dziwe la bethsider
Akut yangogwera!
Nebayotu alibe vuto zake Zikuyenda .vuto ili ndi inu munali MDI mamtha ndi Nebayotu
Koma ma player ake angokhala ngati akwamanje kikkkkk
i dont tnk u r professional zoona kumalemba zopusa ngat izi wake up Malawi 24 stupid adminstrators
Kusazindikira kuja nde kumeneku sukudziwa kut ntchito imeneyi ndiyautolankhan n game yi ukundiuza kut isn’t newsworthy???? Come on osamatichititsa manyaz neba
kazigona iwe zaziii
Ndimakapedi a 24 mmalo momalemba khani zikulu zikulu zochitika m dziko lathu kumalimbana ndi zopanda pake
tachokani apa abullets, mufuna 24 wo adzilemba za dzimipira dzaphuphuphu dzam’mwamba dzija mumamenyadzi? shame!
Sanje simanga mudzi a bullets bwanji kusayamika
Titenga lig fc fodya bas.
zako. ife nde zikutibebelatu
mfiti ina ndiiwe
Malawi 24 Thumbs Up Mumatha Nkhani Zoyenera Kulemba Ndizimenezi. Nyerere Woyeeeee
Love Noma and Live Longer
timuyo inali kuti kuti muziti yatha zaka leveni?
inu a malawi 24 pamtumbo panu ok izi ndi zampira wina amawina ndikuluza ndiye kumalemba zot mtundu wa a malawi akuveren mwabwino mxiiii
kkkkk mulira simunati, kkkkk ha ha ha ha
hahahahahaha…uko mkulira kwa cadet
Aaaaa zomweziii kuchita kupsa mtima choncho zomweeeeziiii
Kuwina kwa noma wina pakana wanyanyala chokudya ndaonela pa uyu kkkkkkk
Kkkkkk koma yah mpaka phuzo
Hahahahaaaaa Hebdreson waganiza bwanji aise??
Ine kundinyatsa
Chimwemwe chokhachokha.
Stand up all the Champion ndi nyimbo yomwe ilimkamwakamwa
Nkhani ndiyoti Noma ndi akaswiri a 2017 TNM Super League basi, koma poti olira samuseka pakamwa, neba zilira. Mission accomplished.
Wakwiya ndi mfiti.
Tatenga zikumunyasa akakolope nyanja kkkkk
Neba panotu uli iweyo koma too much day dreaming
Neba usaiwale kuti std bank cup inathelamo osailawa bola ife league tinatengako kumayambiliro kaya zatha zaka 11 koma macup timatengabe
Alawek 10yrs were ayi akhalisa
Neba ndiamene akusangalala kwambiri. Congrants neba, u deserve it
*Sichipongwe koma chilungamo* *Beforward wanderers Nyerere inatengako league WhatsApp kulibe, , plasma TV kulibe,tablet kulibe, Facebook kulibe kkkkkma 4n tiku user ma ground 4n kuli ma 4n azidina kkkkkkkk Noma sizatheka ⚽ izo ndizomwe akunena anthu akuno
Zaka leveni mwana kubadwa mpaka 4mu 1 osainunkha super League
Neba wapita ku court .kukatenga chileso kkkkkkk
Amawona ngati tigwetsa chikwama walira mawule Ife nde takafika nacho MIGHTY BEFORWARD JP WANDERERS
Mwana anatsogola ndi chikwama uja wafika nacho pano
Eti mpaka mwini ulendo sanafike hahahahaha
Wakwiya asamuke chaka chose.kkkkkkkkk moto kuti mbuuuuu!
inu mwatikwana mwava? iyaaa! tamva kut atenga chkho zomwez mpaka titsekule mmimba? kkk
Kkkkkkkkkkkk usowa .ipsani mtima zenizeni
Kumatenga tenga league kuti Neba azipsa mtima zenizeni. Kkkkkkkkkk zampira izi.
Kkkkkk neba jelasi….
Mtima ukuwawa neba kkkk upse mtima kumene tizikamba kamba izi
Hahaha wangoyenera kutsekula mmimba nebaaaa
Ipsani mtima zeni zeni ????????
kkkkkkkkkk
Ndiposo sunati mpaka uphwisidwa iwe neba
Akampopi inu tisiyen tisangalale mmene mumanyasira mtaunimu mukawina iyaaa get out
Gloria u r ryt
Zachilendo ku banja LAthu
Olira sitimutapa mau ndiolira basi zamuvuta kkkkkkkk
Nkas anati asiyeni olira alire,poti misozi imatuluka ulele sitigula, Neba congrads,see you Next season
mfitiyooo
Iii!!! tilaweko abale nanga mudzingotenga nokha?11 yrs sipano tisiyeni tiusumane.Ndkudziwa kut nebayi watisiya dala kuti tilaweko chaka chino chokha chaka cha mawa timpatsa.Asaaa tiyeni tinjoyeretu Nyerere chaka cha mawa chikubwerera ichi neba atilanda.
Ungofa chitsilu iwe wamidoli fc, tikukwana sunati
Kwa 11yrs tikuyembekezera kukwatira popeza tinalonjeza kuti tidzakwatira pokhapokha neba akadzatenga ligi chaka chake ndi chino. Eee congrats
I don’t think alipo wakwiya,Noma inayambila kutali kukonzekela ndiye season ino zaonetsadi kuti anakonzekedi congratulations neba.
Akunena kt ndizacilendo nyerere kutenga lig bola asapenge nazo pot ena adatopa nazo
Wakwiya ndi mfiti wakwiya ndi mthakati nyerere woyeeeeeeeeee moto kuti buuuuuuuuuu
Nyerere, nkhuku, nkhumba fc
Malawi24 z indid a disgrace & unfortunate page in ever since.
Ife a silver sitikusangalala koma conglats
Zabwino zonse NOMA
Kananji akuti league sinathe adikila game yomaliza kkkkkkk
Kkkkkkkkk mwati Kananji akuti chiyani? I think mwina sanamve kuti Noma yatenga kale hahahaha.
KO’d inu munatha zaka 6 osatenga league, manyazi bwaa, lester city inakhala zaka 150yrs, kudzatenga mu 2015_16season
Ndiye ukuzilimbitsa mtima? ??? 6 ndi 11 yochuluka ndi itiyo?
Manyazi bwanji nanu tikukamba Zapano ungandiuze kt panene noma inatha 11yrs simatengako cup ndekt inali focus pama cup games nde chaka chino apa za league zo mkona atenga
Zonsezo ndi zaka basis olo chikanakhala chi modzi komaso big NOMA imatenga macup
Ndinkadabwatu ine ndi page imeneyi 11yrs yosei Siimapeleka ma update koma lero eee maloto azaka 11 abwera poyera lero
Hahahaha,ndani safuna wamkaka,ananale basi
NAPHIRI wasangalalatu, koma ndiye wadikilira kwa nthawi yaitali alemekezeke wamwambayo
Wakwiya ndi mfiti
Nyerere woyeee! Its time for Nyerere!
wamkaka Noma moto ndipo kuno kubwangwe kwayaka moto kuti buuuuuu
11 Years Osatenga Lig? Anthu Kuno Akuti Ati Ndimaloza.Akutinso Mwina Chaka Cha Mawa Kukhala Njala Chifukwa Izi Zachitikazi Ndi Mwikho.Atinso Bullets Izi Za 11yrs Izi Saziziwa. Yewooo!!!
Nanga inu mukadzatenga ngati anzanu mukuti mmene atengelamu ndi malodza, inu nanga chidzakhala chiyani?
kkkkkkkkkk kuno akuti yangotsogola ndi chikwama cha alendo :p :p :p
Kuno akudikila chikwama chigwe kkkkkkkkkk
Kkkkkk neba sakumvetsa ndi ma penalty ake
kno fans ikut league snathe bb mkumazulo
Fans kuno ingoti AKA 11 yrs FC yatenga .League kuikonzekera kwa 11 yrs??
Maule sangakwiye koma kumufunila zabwino neba kut wakula asiye kukodza pa golo
Kkkk inuso musiye kusuta cz kusuta kumaononga timuuuuu kkk
Fodya atati asasutidwe kamwendo angadandaule kkkkkkkk
Mmmm mapeto ake ndiamenewo kulepher kutenga fisd nkumat mutenga tnm kkkkk! Kayambeni kuokera fodyanoooo!
Bro zocheza2 iziii osat mpak tikwiilane zmweziiii plz!
Umaziwa bro ndiye yake munthu okwiya sawoneka bwino panopa tikuwokela fodya kut tikwanilitse malonjezano
Kkkkk mamuna aziter bg man! Umakhar kt nzang??
Kkkkk mamuna aziter bg man! Umakhar kt nzang??
Yemwe akufuna track yomupepesera Neba aponye whatsapp line yake. Ndi chi nyimbo chovinika bad!
share kkkkkk 0882293207
0881812223
0881721225
0995120602 ponya ada kkkk
0717051149
Nyerere woyeeeeeee!!!!
Neba akumwa kaye 10litres ya alovera
Nyerere woyeeeeeee
Kodi ndi wanjerere eti!