
Pamtsetse ndi MoFaya sanabwere kuzakhala
Wolemba: Gracious Zinazi Pamene a Malawi akuonetsa kuti anailandira mwa chimwemwe sevisi ya Pamtsetse kuchokera ku TNM komanso MoFaya kuchokera ku Airtel Malawi Plc, zadziwika kuti masevisiwa ndi a miyezi itatu yokha. Izi zatsimikizika pomwe… ...