Apolisi m’boma la Machinga akwidzinga ndi kutsekera abambo atatu chifukwa chowaganizila kuti adachotsa moyo wa bambo wina wa zaka 60 pomukhapa ndi zikwanje.
M’malingana ndi oyankhulira apolisi m’bomali Davie Sulumba, a polisi amangadi John Daudi a zaka 30, Henry Dawa, 19, komanso a Sinoya Petro a zaka 32 powaganizira kuti ndiwo adachita za upandu okuphawu.
A Sulumba anati ophedwayu, Jaison Thom, yemwe amagulitsa makala adakumana ndi tsokali mu m’bandakucha wa pa 23 Okotobala pamene adachoka kunyumba kwake ndi thumba limodzi ulendo wa ku Liwonde kuti akalitakate kwa kasitomala wake wa nthawi zonse.
Koma podutsa m’mudzi mwa a Chilonga, mwadzidzidzi kudavumbuluka abambo atatu omwe amagona panja pa nyumba ndipo anayamba kumenya ndi kutema ndi zikwanje a Jaison Thom modetsa nkhawa ndi mopanda chisoni powaganizila kuti adali okuba.
A Thom adatengeredwera ku chipatala cha boma cha Machinga komwe madotolo adatsimikiza kuti iwo adamwalira kamba kotaya magazi ambiri chifukwa cha mabala akulu omwe adali mthupi mwawo.
Potsatila kafukufuku, a polisi mderali akwanitsa kumanga atatuwa pa 24 mwezi omwewu ndipo abambowa akuyembekezera kukaonekera ku bwalo la milandu kukayankha mlandu wa kupha omwe umasemphama ndi gawo 209 la malamulo oweluzira milandu
Potsatila izi a Sulumba apitiliza kudzudzula anthu m’bomali kuti apewe kutengera malamulo m’manja mwawo popeza kumakhala kuzikalasulira makala a moto, koma kutengera oganizilidwawo kwa a chitetezo cha m’mudzi kapenanso ku police kumene.
A Jaison Thom adali ochokera m’mudzi mwa a Chipamba mfumu yaikuli Sitola m’boma la Machinga, pamene a Daudi, a Dawa ndi a Petro onse ndi mmudzi mwa Issa mfumu yaikulu Sitola m’boma lomweli.
Anarani kit aphedwe
Read #12
Too much killings in this country. This is destroying this Malawi. People should learn to forgive
Kodi 3 akutivuta bwanji? Azimayi atatu aku 25 aja kenako azimayi atatunso aku 24 then ndi amuna atatu aku machinga zoona Koma 3 utisowetse mtendere, Iwe 3 tisamale.
Akamange banja kundende
Achawa sanga kulimba ntima ngati mwala iiiiii
Malawi ankaziwika bwino pa nkhani yopemphela muno mu Africa kma wazaza ndizoypa …apa ndsaname Malawi wapanga apazi ndza agalatiya …nde chiweluzo chinawe pafupi koz unali ndicholinga posalisaina lamulo la okupha nzake aphedwe …unkafna anthu aziphana chonchi ngt nkhuku ..chenjela Malawi ndimasiku ano otsiliza…
pa maso ngati khosa mu ntima ndi mimbulu
Each&every Day Nkhani Zimodzimodzi?TheGvt Must Polish Up Lamulo Loti Wakupha Nayeso Aphedwe.
Let DDP ilamulire mwaufulu.bas chilichose choipa ndi DDP,sono chabwinocho nchandani?
Mmmm! Shame on them! Yalakwanj nkhalamba yogwa nkumina ngat iyiiii abaleeeeeeeeeee?
kkk kma abale dziko likutha ili.
Shame to ma country malawi
Kkkkkkkk fools still believe that Malawi was created by God shame
Say it again
What do you mean?
Nonsense
Ndanena ndanena
Kumachinga ndiye ndikwausilutu
Koma mtnthuyo analakwanji?
zinali bwino kale moti lamulo linali la mphamvu opha anzake nayonso aphedwe
Ooooh GOD forgive the sinner
I think the number of sinners is decreasing and the number of devils is increasing in the Warm Heart of Africa. The Devil cannot be forgiven because doesn’t know that language. A sinner can convert and forgiven but not the devil.
One Hausa man just called me I told him it’s wrong number, the man called me back and ask me if I know the correct number
It’s you who told him that it was a wrong number.So he had to ask you again for the corret one!kkk
kkkkkkkkkkkkkkkk. Wiseman
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Mwawona bwanji malamulo kuwadereratu kumeneko nanga mmalo moti angokhapa ndi munthu mmodzi koma onse! atatu,ndimanena ine anthuwa sasamala za moyo wanzawo inu simuva! akatero muwaona one week abwera kundende kuja pobweraposo ngati timabwana ataphuzira ntchito za manja alipheeee koma wa nzawo moyo atachotsa Eeee! koma ku Malawi!
by all means the have to rot in jail
Ana anjoka
Iwo Anapasidwa Udindo Oteteza Malamulo Sakukwanitsa Kuphunzisa Anthu Zakusatengela Malamulo Mmanja Mwao Look Innocent People Iz Dying
Analakwa Chani Kufika Mpaka Pomuchosera Moyo?
kwalowa chiwewe ku nyasaland
DZIKWANJE CREW MAMEMBA AJA I GUESS NTHIMPHIMPHI
Let them rot in jail
Anali bloodsuker? Nkani za mkachasu izi
Nde nkhaza tsopan abale mwatani kod?
Mateyu 24:12 “Tsono popeza kuti zoipa zizidzachulukirachulukira, chikondi chizidzacheperachepera pakati pa anthu”. Abale Yendani ndi Mulungu kuopa kugwera mmayesero.
Zikwanje si A DPP ameneo.
No sense!
Kmano Tsikuli Likuchedwa Atiweluze Bas Ambuye
Muchimva China chiziti ndi a DPP,
zowona chikapezeka ndekuti nchitsiru chilibe nzeru sukunama!
Ndi a DPP. ???Zamuwawa andipeze Ku nyumba,am ready for you.???
kkkkkkkkkkkk
Poor language
Zoopsatu izi
weluzan ambuye dzikol
mmmmmm
Koma ku Malawi eeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee kwandiopsya
nawo akhapidwe ngati mang’ina
Koma anzathu kumwera uko umbuli wanuwo ukugwira ntchito.blood sucker, ndinuyo kupha anthu osalakwa.each and every evil doing it’s you infront southerners why ?ignorance and illiterate at it’s best.kenaka tukumu tukumu anthu ozindikira ife!