Si zampira ayi. Apa zikungokhala ngati anthu ake ndi agalu achiwewe chenicheni oti akufunika kuswa ndi miyala.
Anthu ena ochemelela timu ya mpira ya Bullets akuononga masewelo a mpira kamba ka khalidwe lawo lokonda ziwawa.
Anthuwa ati asandutsa bwalo la za masewelo la Chilomoni kukhala ngati ku dipi ya agalu komwe kuli kukuwana, kulumana ndi kunyindulilana mano.
Masapotawa akumaonetsa khalidwe lawo loyipa kukabwela timu yina kuzakumana ndi Buletsi.
Dzulo laliwisili, agalu a chiwewewa anamenya mkulu wa timu ya Karonga United imene imakumana ndi maule mu chikho cha FISD.
Malinga ndi mtolankhani wathu, agaluwa analumphila mu bwalo la za masewelo ndi kumupeza wamkulu wa timuyi ndi kumuchita chipongwe. Apa ndikuti akuluakulu a Buletsi ndinso a ku FAM akuona.
Iwowanso ati anapita kukatsina atolankhani a za masewelo amene anali ku mpirako. Ojambula vidiyo wa ku kanema ya Joyi ati naye anatsinidwa ndi zigandanga zodziwika kuti agaluzi.
Malinga ndi akuluakulu a ochemelela Buletsi amene ponyadila amaziti ma Palestina, iwo akufuna kuthana ndi mkhalidwe onunkhawu.
“Pompano, mayina a agalu amenewa atuluka. Tikatelo tithana nawo anthu amenewa,” atelo akuluakulu a ma Pale.
Malinga ndi otsogolela ma Pale, anthu a khalidwe lonunkhali akuyembekezeleka kuletsedwa kupita ku mpira kwa zaka ziwiri.
Ife tonse a Maule tisiye mnchitidweu
Vendor wa maule sazatheka tiyeni timuzolowere
Kungot ambili ndioitanira ma minbus ku BB
Iwe mapale amakuvetsa kuwawa neba
ndi ma supporter a bb omwewo ayamba kupopa magazi.
No wonder many are ddp cadets,
Ukhaula Ndi Sanje Yakoyo Neba Wakalamba Musiyre Mwana Ali Njoy Zko Lake Maule Mpakampaka Manoma Mbalame Za Anthu
Mpila si ndeu muziwe lero,azilandila chilango ndithu,anthu ake ndiomwe aja omwe savomeleza kuluza komanso kusintha kwa zinthu
Our poverty is deep and thus worries me. It’s deep inside our white matter. No wonder we back sliding
kodi iwe ulibe nchila nawenso galu? uzilemba mozetsa bata fyoko
The fools team
kusazindikira baasi, zoti pa game pamakhala winner and looser they dont know, The Dog’s Team Not The People’s Team
MUKUDANDAULA CHILATA NGATI CHIMENECHI
Team ya Anthu osowa umunthu kwambiri
Mukatopa Nd 24 Wanuyo Bas Kukamba Zaife.Bwanji Osamalemba Za Mages Kapena Za Madzi Omwe Akusowa Mumadera,ife Ndife Sitizasiya Kusapo NBB olo munene mwatundu wanj ife nd nga, nganga maule,gule supangira kwa en matama
a nbb ndizisilu zosazindikila
Bwino nazotu ndikuva tiwonana lelo
Akumachepetsa zilango Ku timuyi pakufunika 3.5 Mita n above
Olo akambe dzambiri maule ndi maule
Zigandanga zimenezi
amalawi 24 palikundu kuyambila bwana wanuyo osamalimbana ndi team yotha mpira
hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email [email protected] , pardon me i offend you with this post, but i must share this good new
Zomwe akuchita a BB ndi zosokoneza nichifukwa chake amasowa ma Sponsor, Chifukwa palibe Company ingasekelere zopusazi kuti aziwaonongela mbiri
@Arinze zonga apapa this too much bro,,,idiot
NO wonder team yawo imatchedwa
Kanunu fc
Bus yibwera friday fc
Ma vendor fc
Kamogo fc
Saveji fc
Nyanga fc
Ka mpopi fc
Agontha nkutu fc
Bibi shit fc
Midoli fc
Kandeu fc
Ka mpopa fc
Ma kape fc
Ma hule fc
Ma skin fc
Agalu amiyendo yiwiri fc
Ma pale tiyeni tisute poti kusuta kunasiya kuononga moyo
Nde team ikalephere kukhala agalu choncho?? Team yokhalira kusuta ndi kumwa midoli zknthu zomwe zili zosonkhezera zisokonezo
Anthu opusa zedi ndiye ku Lilongwe mukukagagadidwatu mukachiteso ndewuyo kuti okuthandizaniwo azikapsya mitima zedi
Galu ndiweyo panyopako konso pamodzi ndiwomwe akutuawo mbuzi
Ukungonenapamenepo.Mawule mawule motokutibubuu,ilokotitamasuta sindingaisiye!!!!!!!
Ana…a…mu…ndix…ndioipa…monday…lapitali…apolice…anagwira…mafana…atatu…akuti…amaotcha…kanyenya..wa…mbuzi..kuphatikiza…ndi…nyama..ya…galu..(dog)…ndikunena…pano…ali…pa…shamba..(true..story)
Zimenezo…muzipanga…ndimateam…ena..ife…ndiye…musayerekeze…tikubandulani…mmawali…ndatola…kale…myala…yanga…ndaikiratu…mu…cooler…box…tikaonana…ku…bingu…konko…ma…pale…nde…kuti…chani?…
maule moto kuti buu!!!!!!
ma supporters a NBB alipo ochuluka kuyerekeza ndi team ina iliyonse mmalawi muno tsono zikuoneka kuti ndikuchuluka kwa anthu kumeneku kukupangitsa kuvuta to tame these supporters
Mungayembeke
Mungayembekezele chani kuchokela kwa anthu ogulitsa ma memory card anyimbo kale komanso masachetia midoli
Magayz Kungot Kuno Kumarawi Athufe Sitzava Kukhan Zapir Zochitika Zake Bor Zokhazokha Komano Inu A24 Nanuso Kuri Bwino Muzikangorima Kumadimba Muzikadya Zigumu Komweko Tatopa Nanu Ife
Komaso timu iyi ndi yambuli bas achuka mavenda ayitanila komaso osuta chamba muone ma timu enawa kulibe yopota sisi ndiye awa ndi amisala mkalasi sanapite so plz asiyen bas
Reporter iwe usaonongetse ntchito ya company yako chifukwa cha kuti bullets umaida,if u want to advise them do so,koma apa mmene ukulembera kudzetsa udani kunyuziyo ndi masapota kapena team ya bullets
chilungamo ndi chowawa
chilungamo ndi chowawa
Galu ndi amako nyani iwe eti…!!!
Pamalo pakachuluka mbuli ndichoncho agalu mavenda fam signathanenawo amenewo amafunika tiergas
pa mtumbo pamako admin udzpanga zandake ku nyini kwa mayako
Zikukhala ngati kuti FAM ndi SULOM imachita mantha ndi NBB, zomwe akuchita ma supporter a BB kukhala ma team ena a Fam akanakhala atachitapo kanthu. Fam ngati siyichitapo kanthu ndiye kuti mpira mdziko muno suzapita patsogolo. Kukubweraku ngati vuto iri siritha mateam onse Mmalawi muno samazalola kusewera ndi team yopanda descipline. Mpira sinkhondo wina amawina komanso wina amaluza. Chonde inu a Fam ngati Malawi mumankonda musachedwe muchitepo kanthu, koma ngati mukufuna kupha mpira dziko muno ndiyekuti muzingoyang’anira zomwe zikuchitikazi.
Musamale ndi masapota anu a bullets akuonongeni mbili
Agalu sangakhale a BB.Taonani ena.
Ubwino kuti muonesetse amayambitsa ziwawawo si a BB.
Zilango zina afam amaona khope, noma ndi silver, anawa choselapo ma poit,poti ndi bb
Team iyi mwachuluka zifwamba .
Or munyoze mutani ife ndimaule bas moto kt buuuuuu amene zimunyase asamuke.
Mukamanva zoti time yanu ikupanga ndewu mumanva bwanji mumtimamo
Imapanga ndewu siteam ai kma a2 osokonekela maganizo mukanena team ndiyantendele.
Kkkk agalu fc
Vikuwinabe…….chimtima bwaaa!!!!
Antola nkhani kukokomeza.
pamtumbo pako malawi 24 muthu angakhale galu
Even mutalemba zonyatsa bwanji abt the #Peoples_Team mungozivutapo apa ,,,
mbuli zija anthu ake ndi inu.. post iyiyi akufuna kuthese mchitidwe umeneo….may u don’t know in England nawo amaika waya kalelo koma panopa anachosa waya uja …koma kunoko sizingatheke chifukwa cha ma savage a bullets ngati inuyo….
next tym when you to talk someone learn to respect am not even at ur Nkhumba weti,
A herbalist in Africa has been curing hundreds of HIV patients using natural herbs. He has on countless occasions after curing patients presented lab results both positive and negative, together with the cured person. with joy in my heart i will like to inform the general public. i never knew there was a cure to HIV until my sister was cured from the virus after four years of battling the virus with ARV. She took his herbal medicine for a month and some weeks and when she went for a test and she was diagnosed to be negative. you can contact the doctor on WhatsApp or call +2348147299781
Team ya ma savage.
Kodi tiziti ngachipani chanji
Imeneyo nde bullets matimu akamamenya pachilomoni azichita mantha kuwina powopa kuluza miyoyo?
akasitha rebo mapale or kwaondi aziwawa kuyambila kale.
akasitha rebo mapale or kwaondi aziwawa kuyambila kale.
When people didn’t go to school enough this is a result. Poor understanding is equal to brutality
#Namapopa Fc
Osamawaputa dala , inu nomwe mumawanena kuti amagulitsa ma memory card anyimbo kale koma nkumawaputaso angakusiyeni…? Ndi ma Palestina paja amagomera mwala musayiwale
Agalu ABB Nthawi Zonse Tizingova Za Bb Team Iyi Aithetse Bas
Anoma Ndinu Akazi Anthu Timangolowesa
Akuipisa Dzina La Nyasa Aboncholi Amenewa
BB team ya #mbava
Mwasowa choti mulembe,post ndinaiona kale kale pa game ya nbb ndi wandres ,mumatida chifukwa chani
Agalu amenewa sadzatheka.
Kuwina or kuluza kwawo ndikugenda.
This behaviour is commonly associated with a certain grouping notoriously known as ‘ cadets’. R U sure BB is not infitrated???
Katenge chikwapu nsanga FAM anawa akuzolowela zaugalu kkkkkkkkk
Ngati mukunena kuti ndi agalu ziwani kuti galu nd galu samava,mvuto lili ku fam kumbukilani kuti noma ndi siliver anapasidwapo chilango pa zomwe zidachitika ku balaka mpaka lero ma teams awa sadachiteso maphokoso koma bb sinalandilepo chilango chowaminisa. why? Afam amadyela momwemu akamati a bb mulipile ya bonya chifukwa cha zomwe mwapanga kumbaliku akuwauza ma lifali kuti msamalole kuti teamyi iziluza chonde tima freekick,mapenati ndi makadi muziyesesa kugawa chifukwa ali ndi athu ambr ife timapeza za mbr pa gate ndimmene timadyela.wasaiwa kuti zulo asewelesa playr wa mayelo awiri yet afam analipopo.
Nthawi zonse simungakhale mukupambana ayi, chofunika ndi kuvomeleza basi osati ndeu, Koma na sapota wa NBB umbuli, uchifwamba, kuba, ndiye zake,,,,,,,,,,,,,,,,,,,.Punish them may be they can learn how to support
Unyaa gulu iwe ukuona ngat uzimenya ndi abwiyako uona ndi noma yakhoyo tikumenyan zisiru anthu osasamba ngat inu
agalu inu mumalimbana ndi BB
Marcopolo fc hahahaaaa
Ziwawa ku ma stadium sizizatha chifukwa ine nkawononga chinthu ngakhale anthu andiwone imalipilitsidwa ndi team. Ndiye opangayo sangamve kuwawa iyayi. Afam ndi sulom akhale pansi agwirizane zothana ziwawa polanga uyo wapangayo wina azawopa kupanga nso
Agalu football club,agalu akenso achisika
Kugenda fc again??????
Tingawatengele sukulu yake iti mbuli zimenezi?
Mwina ku box 1 ku zomba
Makape awa
koma azolowela kobasi timu yongwilizana ndisatana imeneyi
Zoyamwila musadabwe amenewa ndi adzukulu #Nimulodi omwe amawelenga malemba akudziwa chomwe ndikutanthawuza
ine ndisupporter kuyambira kale koma zimenez zimandinyasa kwambir pankhan yamasewelo.mwana wanga azathesa umbuli umeneu
anthu a NBB ndi ma terrorist kapena bundits zochitika zawo ngati za DPP ndipo ndiamene akusokoneza mpira mziko muno akufunika azangopangidwa ban kwa zaka ziwiri osatenganso gawo pa za mpira
Masaveji
Chenjerani ndi agalu olusawa poleka kutambira team yafukoyi. BB the ruling team in Nyasaland
Chenjerani ndi agalu olusawa poleka kutambira team yafukoyi. BB the ruling team in Nyasaland
Agalu fc
Timenyaso inuyo anoma paife simungawine ndewu ndinu ochepa
kuyambila kale zigawenga katangale musaiwale alibe mbili yonveka bwino agalu olusa
Munyera tkukauswaniso lowelukali msunu wa nyoko
ndi zosiyana kwambir ndimaiko akunja pankha ya okonda matmu.kodi ndinu supporter wosazindikila?mbuli kapena?pls ans me
ndi zosiyana kwambir ndimaiko akunja pankha ya okonda matmu.kodi ndinu supporter wosazindikila?
a malawi24 ndnu zitsiru kwambiri,pangani zanu musalimbane nafe,news zanu sitimazisowaso
Ambiri ndiokonda azawu…. ndiye sichachilendo kuona akumenya anzake olo kuononga zinthu
Malawi 24 ,,,,ndi iwe neba ,,,have midlefinger,,,,
Malawi 24 ndinu zslu kwambl… Bwanj mukulola kut aliese azngoponya ma post alionse muno… Ngat mwatopa nditchto ndibwino kumakabunyula uko… Mbuz za anthu inu
wakwiya ndimfiti! wakwiya ndimfiti!
Ankolo point of collection zslu??? Zitsiru
Alànge chingambwe fc ndipo iyo ikamva kuwawa ikamangilira agaluwo poti ndi ake
Pachuluka agalu zolakwika sizisoweka
Ubwino wake aliyese galu amamuziwa
timu iyi ipatsidwe chilango,chosasewela mu tnm kwa 2 years,kapena kungowapititsa ku division basi! atikwana kwambiri,chaka chatha amkagula ma ref,pano ayamba uchifwamba!
Kkkkkkk,nkhumba,fc,ndiimene,ikufunika,kudivision
Just imagine football without Bullets
Poti olo FAM ikhonza kutha ndalama aziona kuti poti ndalama amaziona chifukwa cha team imene iweyo ukuinyozayo izo udziwe wamva koma kalidwe loipa ine ndakhana komanso a police agwire ntchito yawo coz si masapota onse amene Ali ndi kalidwe loipalo
Kkkk mwana wa nyau
KKkk Agalu Inu,agalu Inu
Pano ndi agalu fc
KOditu team imeneyi pano yalowa uzigawenga heavy kuteloko ndamvaso kuti agaluawowo akuti awatengeraso Ku LL kkkkk
Sindine galu koma alipo mukamba naye ndipo mukapitiriza kutero mupedza posiyira kuwanena anzanu kuti agalu
Akufunika kuwabaya jakisoni amenewo aleka kkkk
Amzathu fodya adawalowa mu ubongo ndiye mitu yawo simagwira ntchito
ZAMANYAZI
Its the peoples team, not dogs team! Big up mapaleeeeeeee!
Muzasova
mpakana agalu fc
Daswhy munthu ozindikira sangamasapote macopolo fc. Zomwe akupanga agaluwa ku chilomoni ground sizampira. Kukhalira kumenya ma official avisting team ma team doctor, kulowa ground, kupanga nyanga pa ground. Ayi ndithu midoli fc sizithu. Ndikanakonda afam atawalanga agaluwa zenizeni
Kkkk mpaka macopolo fc? Mamamamamam
Kkkkkkkk mesa akumati marcopolo ikubwera friday matsiku nkumatha
Koma aaah
asiyen azingoweweta msawatukwane msavutke nao akwera yakumphwa
asiyen azingoweweta msawatukwane msavutke nao akwera yakumphwa
Ungoti palobenso team yomwe izakhale ndi unyinji monga ilili BULLETS tikadati muzanziona coz m’banja mukachuluka mafana ndewu kapena milandu sichoka pakhomo big up Agaru pachiyawo ndi Mbwaaaaaa kkkkk
ndi zowona athu amene samava game ina iliyose mwawozeza agalu inu
Zitsilu zosowa zochita mtown zimenezi
Fam Sulom achitepo kanthu even magame asalawa asamenyere pa Chilomoni
Mbuzi zimene””
agalu achiwewe kusokoneza bas
Aaaahh…Nzanuso Izo. Alekeni Anzanuwo Atenge Chikho.
Panya panu amalaw 24 mwayamba kutijaile et
Even ur family members alinapo
Eya Ngat Sapota Wabullets Waonetsa Zntchto Zake Tm Ya BB Imadzwika Ndmasapota Ngat Iwe,ot Palibe Chomwe Walakwa Pot Ndzomwe Mumadzwka Nazo.
Wa bullets sasowa shame
Sindikuziwa kuti chomwe amaibelekera ndichani chaka chatha anatchuka ndikugula malefu pano ndiizi angowachosamo muligi azapita kubokisini .
nde ukuona ngat league ingakome without Bullets????…Super League imakoma coz of BB ndi Noma
nde ukuona ngat league ingakome without Bullets????…Super League imakoma coz of BB ndi Noma
Ndiye azisunga zigawenga?
Umangonziwilatu kuti voice iyiyi ndi wa next door samationera kukondwaaaaaa
Kkkkkzampira man Alick osakwiya
by saying zigawenga what do you mean??unaonapo ma player a BB akupanga violence???Ban imapita kwa ma supporter…Tiziti simunaonelepo ma UEFA games opanga ma fans coz of violence???
#agalu fb
Kkkkkkkk agalu enieni
Ndiye zitinso mwayambazi
Iwe sukuona kuti ndinkhani ya agalu apachilomoni kkkkkkkk
Agalu fc pa Chilomoni kkll