Kwachuluka uchifwamba ku maule: ‘agalu’ awo akusokoneza pa Chilomoni stadium

Advertisement
Bullets FC

Si zampira ayi. Apa zikungokhala ngati anthu ake ndi agalu achiwewe chenicheni oti akufunika kuswa ndi miyala.

Anthu ena ochemelela timu ya mpira ya Bullets akuononga masewelo a mpira kamba ka khalidwe lawo lokonda ziwawa.

Bullets FC
A Galu a Bullets

Anthuwa ati asandutsa bwalo la za masewelo la Chilomoni kukhala ngati ku dipi ya agalu komwe kuli kukuwana, kulumana ndi kunyindulilana mano.

Masapotawa akumaonetsa khalidwe lawo loyipa kukabwela timu yina kuzakumana ndi Buletsi.

Dzulo laliwisili, agalu a chiwewewa anamenya mkulu wa timu ya Karonga United imene imakumana ndi maule mu chikho cha FISD.

Malinga ndi mtolankhani wathu, agaluwa analumphila mu bwalo la za masewelo ndi kumupeza wamkulu wa timuyi ndi kumuchita chipongwe. Apa ndikuti akuluakulu a Buletsi ndinso a ku FAM akuona.

Iwowanso ati anapita kukatsina atolankhani a za masewelo amene anali ku mpirako. Ojambula vidiyo wa ku kanema ya Joyi ati naye anatsinidwa ndi zigandanga zodziwika kuti agaluzi.

Malinga ndi akuluakulu a ochemelela Buletsi amene ponyadila amaziti ma Palestina, iwo akufuna kuthana ndi mkhalidwe onunkhawu.

“Pompano, mayina a agalu amenewa atuluka. Tikatelo tithana nawo anthu amenewa,” atelo akuluakulu a ma Pale.

Malinga ndi otsogolela ma Pale, anthu a khalidwe lonunkhali akuyembekezeleka kuletsedwa kupita ku mpira kwa zaka ziwiri.

Advertisement

152 Comments

 1. Mpila si ndeu muziwe lero,azilandila chilango ndithu,anthu ake ndiomwe aja omwe savomeleza kuluza komanso kusintha kwa zinthu

 2. kusazindikira baasi, zoti pa game pamakhala winner and looser they dont know, The Dog’s Team Not The People’s Team

 3. Mukatopa Nd 24 Wanuyo Bas Kukamba Zaife.Bwanji Osamalemba Za Mages Kapena Za Madzi Omwe Akusowa Mumadera,ife Ndife Sitizasiya Kusapo NBB olo munene mwatundu wanj ife nd nga, nganga maule,gule supangira kwa en matama

 4. hello everyone am happy sharing this with you, am not suppose to be doing this but i can’t hold back my joy so i have to share with you, you too can be help just as i was helped by Dr Odudu who cured me the HIV virus after suffering from it for some years and CD4 count was very low i was depressed, i was desperately in need of getting rid of it, but the ARVs were not helping so i was eager to contact Dr Odudu who gave me his herbal medicine, today as am posting this i am HIV negative, don’t hide your sickness or else your sickness will hide you, contact Dr Odudu today so that you see a reason to back through the years of your depression and smile to yourself, you can call or whatsap him with his number (+2349067902914)or email [email protected] , pardon me i offend you with this post, but i must share this good new

 5. Zomwe akuchita a BB ndi zosokoneza nichifukwa chake amasowa ma Sponsor, Chifukwa palibe Company ingasekelere zopusazi kuti aziwaonongela mbiri

 6. NO wonder team yawo imatchedwa

  Kanunu fc
  Bus yibwera friday fc
  Ma vendor fc
  Kamogo fc
  Saveji fc
  Nyanga fc
  Ka mpopi fc
  Agontha nkutu fc
  Bibi shit fc
  Midoli fc
  Kandeu fc
  Ka mpopa fc
  Ma kape fc
  Ma hule fc
  Ma skin fc
  Agalu amiyendo yiwiri fc

  Ma pale tiyeni tisute poti kusuta kunasiya kuononga moyo

  Nde team ikalephere kukhala agalu choncho?? Team yokhalira kusuta ndi kumwa midoli zknthu zomwe zili zosonkhezera zisokonezo

 7. Ana…a…mu…ndix…ndioipa…monday…lapitali…apolice…anagwira…mafana…atatu…akuti…amaotcha…kanyenya..wa…mbuzi..kuphatikiza…ndi…nyama..ya…galu..(dog)…ndikunena…pano…ali…pa…shamba..(true..story)

 8. Zimenezo…muzipanga…ndimateam…ena..ife…ndiye…musayerekeze…tikubandulani…mmawali…ndatola…kale…myala…yanga…ndaikiratu…mu…cooler…box…tikaonana…ku…bingu…konko…ma…pale…nde…kuti…chani?…

 9. ma supporters a NBB alipo ochuluka kuyerekeza ndi team ina iliyonse mmalawi muno tsono zikuoneka kuti ndikuchuluka kwa anthu kumeneku kukupangitsa kuvuta to tame these supporters

 10. Magayz Kungot Kuno Kumarawi Athufe Sitzava Kukhan Zapir Zochitika Zake Bor Zokhazokha Komano Inu A24 Nanuso Kuri Bwino Muzikangorima Kumadimba Muzikadya Zigumu Komweko Tatopa Nanu Ife

 11. Komaso timu iyi ndi yambuli bas achuka mavenda ayitanila komaso osuta chamba muone ma timu enawa kulibe yopota sisi ndiye awa ndi amisala mkalasi sanapite so plz asiyen bas

 12. Reporter iwe usaonongetse ntchito ya company yako chifukwa cha kuti bullets umaida,if u want to advise them do so,koma apa mmene ukulembera kudzetsa udani kunyuziyo ndi masapota kapena team ya bullets

 13. Zikukhala ngati kuti FAM ndi SULOM imachita mantha ndi NBB, zomwe akuchita ma supporter a BB kukhala ma team ena a Fam akanakhala atachitapo kanthu. Fam ngati siyichitapo kanthu ndiye kuti mpira mdziko muno suzapita patsogolo. Kukubweraku ngati vuto iri siritha mateam onse Mmalawi muno samazalola kusewera ndi team yopanda descipline. Mpira sinkhondo wina amawina komanso wina amaluza. Chonde inu a Fam ngati Malawi mumankonda musachedwe muchitepo kanthu, koma ngati mukufuna kupha mpira dziko muno ndiyekuti muzingoyang’anira zomwe zikuchitikazi.

  1. mbuli zija anthu ake ndi inu.. post iyiyi akufuna kuthese mchitidwe umeneo….may u don’t know in England nawo amaika waya kalelo koma panopa anachosa waya uja …koma kunoko sizingatheke chifukwa cha ma savage a bullets ngati inuyo….

 14. A herbalist in Africa has been curing hundreds of HIV patients using natural herbs. He has on countless occasions after curing patients presented lab results both positive and negative, together with the cured person. with joy in my heart i will like to inform the general public. i never knew there was a cure to HIV until my sister was cured from the virus after four years of battling the virus with ARV. She took his herbal medicine for a month and some weeks and when she went for a test and she was diagnosed to be negative. you can contact the doctor on WhatsApp or call +2348147299781

 15. Osamawaputa dala , inu nomwe mumawanena kuti amagulitsa ma memory card anyimbo kale koma nkumawaputaso angakusiyeni…? Ndi ma Palestina paja amagomera mwala musayiwale

 16. This behaviour is commonly associated with a certain grouping notoriously known as ‘ cadets’. R U sure BB is not infitrated???

 17. Ngati mukunena kuti ndi agalu ziwani kuti galu nd galu samava,mvuto lili ku fam kumbukilani kuti noma ndi siliver anapasidwapo chilango pa zomwe zidachitika ku balaka mpaka lero ma teams awa sadachiteso maphokoso koma bb sinalandilepo chilango chowaminisa. why? Afam amadyela momwemu akamati a bb mulipile ya bonya chifukwa cha zomwe mwapanga kumbaliku akuwauza ma lifali kuti msamalole kuti teamyi iziluza chonde tima freekick,mapenati ndi makadi muziyesesa kugawa chifukwa ali ndi athu ambr ife timapeza za mbr pa gate ndimmene timadyela.wasaiwa kuti zulo asewelesa playr wa mayelo awiri yet afam analipopo.

 18. Nthawi zonse simungakhale mukupambana ayi, chofunika ndi kuvomeleza basi osati ndeu, Koma na sapota wa NBB umbuli, uchifwamba, kuba, ndiye zake,,,,,,,,,,,,,,,,,,,.Punish them may be they can learn how to support

 19. Unyaa gulu iwe ukuona ngat uzimenya ndi abwiyako uona ndi noma yakhoyo tikumenyan zisiru anthu osasamba ngat inu

 20. Ziwawa ku ma stadium sizizatha chifukwa ine nkawononga chinthu ngakhale anthu andiwone imalipilitsidwa ndi team. Ndiye opangayo sangamve kuwawa iyayi. Afam ndi sulom akhale pansi agwirizane zothana ziwawa polanga uyo wapangayo wina azawopa kupanga nso

 21. anthu a NBB ndi ma terrorist kapena bundits zochitika zawo ngati za DPP ndipo ndiamene akusokoneza mpira mziko muno akufunika azangopangidwa ban kwa zaka ziwiri osatenganso gawo pa za mpira

 22. timu iyi ipatsidwe chilango,chosasewela mu tnm kwa 2 years,kapena kungowapititsa ku division basi! atikwana kwambiri,chaka chatha amkagula ma ref,pano ayamba uchifwamba!

  1. Poti olo FAM ikhonza kutha ndalama aziona kuti poti ndalama amaziona chifukwa cha team imene iweyo ukuinyozayo izo udziwe wamva koma kalidwe loipa ine ndakhana komanso a police agwire ntchito yawo coz si masapota onse amene Ali ndi kalidwe loipalo

 23. Daswhy munthu ozindikira sangamasapote macopolo fc. Zomwe akupanga agaluwa ku chilomoni ground sizampira. Kukhalira kumenya ma official avisting team ma team doctor, kulowa ground, kupanga nyanga pa ground. Ayi ndithu midoli fc sizithu. Ndikanakonda afam atawalanga agaluwa zenizeni

 24. Ungoti palobenso team yomwe izakhale ndi unyinji monga ilili BULLETS tikadati muzanziona coz m’banja mukachuluka mafana ndewu kapena milandu sichoka pakhomo big up Agaru pachiyawo ndi Mbwaaaaaa kkkkk

  1. Eya Ngat Sapota Wabullets Waonetsa Zntchto Zake Tm Ya BB Imadzwika Ndmasapota Ngat Iwe,ot Palibe Chomwe Walakwa Pot Ndzomwe Mumadzwka Nazo.

 25. Sindikuziwa kuti chomwe amaibelekera ndichani chaka chatha anatchuka ndikugula malefu pano ndiizi angowachosamo muligi azapita kubokisini .

  1. by saying zigawenga what do you mean??unaonapo ma player a BB akupanga violence???Ban imapita kwa ma supporter…Tiziti simunaonelepo ma UEFA games opanga ma fans coz of violence???

Comments are closed.