Infuriated by the exercise by police to demolish their structures at Vigwagwa market, irate vendors caused havoc in Mzuzu city last night.
Reports say the vendors owning the structures at the market have overtime been told they are operating in an illegal space but have failed to give in to calls to relocate.
Due to the failure by the vendors to move out, police last night went on to demolish the structures but only sparkled an unprecedented reaction from the vendors.
In retaliation, the vendors rushed to Mzuzu stadium and city council where they reportedly set fire to some equipment being used by the National Registration Bureau (NRB) for the national registration exercise.
As if this was not enough, the vendors went to city house of the city’s Mayor in Mchengautuba where in the course of torching his house, community members came to the mayor’s rescue.
MORE TO FOLLOW.
Ntumbuka Sazatheka Kwao Kuja Nkosatukuka Ndikale Akumaononganso Tizikhute Tomwe Tilipoto Anazolowela Kukhala Nchile Awa
Apa palibe waku mpoto ndi wa kum’mwera tose ndife a Malawiiii
Vendors well done hahahaha
Malawi a moto
ઐજછખછઠટધઢ,ભ નઘઘૃથથથ,ઐઈગ ડઝડછઝ
Atumbuka panyero panu ndithu, mukusaukitsa dziko lathu la Malawi, kuli bwino mungokhala ndi dziko lanulanudi muzizunzana nokhanokha. Ndiinu anthu ankhanza monga abale anu mazulu ku SOUTH AFRICA. Mwayambaso akutotholeni ndi mfuti, muzidandaula? pano ndiyetu ine sindikumverani chisoni, mukuziyamba dala.
this picture was for university of livingstonia computer lab which got burnt last semester..Malawi 24 show the real building
Mbuzi!
I like it,,mwina angamangeko zinthu za standard,,,big upp vendors well done
ine ndikutukwana mchichwa chomveka bwino: matchende ako
atumbuka ndiinu anyani
sis,who is this one shouting in capital letters?
sis,who is this one shouting in capital letters?
Its not right its not wrong bothe the government and vendors are wrong what if the city council notify the vendors to move to a recommended place for market i min new place for them to do business.. komaso aboma mumalekwrela anthu akuik ma structures mukuziwa kuti sipoenera mpaka muthu kumaliza kumanga then later on kumazaphwasula instead kubwera the vry same time kuzawaletsa? Kodi tizingokhlora nkhani yake yomwei kumatiphwasulira ma businesses athu rather mumati tizipangore tokha zochita… find solution izizi zisazachitikoxo boma z a hope for development to community not a destructive development
Why the stadium?
Enanu mukamapanga comment be careful, APA takumvani achewanu mukunena monyoza, but don’t forget kuti kwanu Ku mwerako mwayamba kupopana magazi, nde apa mbuli ndiiti?
Mello so how about those things police destroyed???
Nthawi zambiri izi zimachitika kaamba ka umbuli amawona ngati akuwononga zinthu zaboma osaziwa kuti ndizawo, ana awo, makolo awo komanso mubadwa wawo wa mutsogolo
Anayamba ndi acity kugwetsa ma shop a anthu ndiye mavenda akanatani
koma zukulu iwe ndiotsutsa boma litsakonze kkkkk
Most of vendors of our mzuzu city they from chewa guys that’s the problem
people will always resist change…but eventually they will realize they fighting a loosing battle…pathetic
Job well done!!!!!!!
Chifukwa choti zachitika ku north nde enanu mufuna muoneke amzeru, muzaziona wina akazaononga malo omwe umapezelapo fees, fertilizer, daily bread and the like….
Let me know whether Mzuzu vendors and all people in the North, are they all Malawians or not? Northern region’s stories sometimes doesn’t impressed me as a typical Malawian
Backward mind
wats hppn in mzuzu is wrng u cant bite the same hand that feeds u . Durban
Iiiii mavenda ndiye podyela nanga atani?
Get the mayor to sort out the problm
Ndisamve kuti boma lakonza…kukhale choncho ubwinowake sikumalawi
These people they doesn’t like any development bcoz they used to stay in the bush like monkeys we must live them as such
Mind your speech, this is social media, see your comment it’s a clear indication of your brutality, if you were as wise as Solomon you couldn’t have raised that speech.
Ma savage
Mwaba kale amalawi mzomwe mmapanga ngati inaphya offence ya ulimi
Malawi ujayo
Alomwe ayawo, a sena ndi amene ali ma vendor akumupoto inu mwana wa mtumbuka samapanga ma bizimisi kwake nkugwira ntchito m’boma komanso kulemba a chewa ntchito mm kampani.
This is not about being a Muslim,what is the privileges of destroying infrastructures?? Its out stadium…The main problem of we malawians we owez politicize everything,
What have they gained after destroying government property. A Malawi let’s learn nzathu zomwe tikuonongazi. Kodi mukakwiya Ku nyumba kwanu olo mukayambana ndi akazi anu mumaotcha nyumba?
Tumbuka tsadzathekatso otsamagiralatso tsika wina please
Big up vendors!!!!
Mavenda tiyeni nawo wangatangwaniskanga yayi.Thats brilliant.Freedom!!!!!!!!!!!!
Conel Q Hammissih you have never experienced a set back that’s why you are talking shit. You are in Joberg now because you can’t stand problems that are back here at home. Peter’s property or not he is our president and protector. All the problems we have now …he will never avoid the blame. Vendors have expressed their feelings deal with it. Most them your fellow Muslims.
Ophunzilanu takaliphuzisani bomalo kukonda amphawi omwe zili nzika zawo street vending is world wide even if u go to uk mwinaso ndikunena pano magesi athima mukawaphunziseso mmene angapangile suply magesi nkaziko kakang”ono ngati malawi ndondomeko zake ziti? Malamulo ake ati? Olangila anthu osaukawa ngati amapanglia mmalo olakwika bwanji amawadulisa matikiti nkumalandila ndalama?
Wasted sperm,I thought you are old enough to say something better,whatever you destroy it’s not Peter’s property,
The mbwenu people!
Inu anthu akummwera ndamene muli ma vendor ku mzuzu osati atumbuka, pano mu mzindawu munadzadza alomwe
Hahahahaha tell them mpongozi wanga
Mphwanga Anthony ku Malawi kuno zinthu sizikuyenda, mavuto akuchuluka. Munthu sangango dzuka ndikukawononga pamene wina akudalira. Ndikulakwa kwambiri. Sicholinga kutukwana munthu mitima ikupweteka. Boma silikutipezera zochita anthufe. Tikayamba ka geni akubweraso kudzatiwinongela. Ndizomvetsa chisoni izi.
Koma nkhani yavuta, mpaka kutukwanana?
Smilesams Kestain mbuzi yaku mulanje.
A polisi adzigwirako ntchito asamangolandira taulere
Anthu a kumzuzu nzelu mulibe, nde muziti president sakukupangilani chitukuko pomwe mumaotcha zinthu!
too bad
Some Of U R Just Commenting Without Reasonable Points.If U Don’t Know What 2 Comment, Just Leave.If U R Brutes, Go Back 2 School Again 2 Wipe Out All Ur Brutality.Check The Economy Of African Countries On Opera And Find Out Where Malawi Is.If U R Thoughtful, Grief Will Arise.
your the most stupid I never seen,so what do get after all nothing, and ustand open ur fu***n mouth why don’t u find another way ,I can’t ask u the one
Chizete chamunthu iwe ndiye papezeka phindu lanji poyasa mtsika? Ati avutike ndi ndani pakati pa President ndi anthu omwe akukhala kumenekowo? Chibaluwa chonsechi ine ndimayesa ngati ukambamo zanzeru mxiii
Malawi Won’t Become Rich.Many Of It’s Ppo R Vry Poor In Thnkng.Vendors Torching The Innocent Stadium, Vry Sorroful N Shameful.They Don’t Sympathize With Their Own Poor Country.I Believe They Had A Premiditation Behind The Police’s Approach.Just Penalize Them Greatly.Don’t Persuade Them.Yes. Martha Kadyaudzu Pamela Butao Alina Hanock Sammy Samantha Luhana Khomanato Ulera Beehaaj Khumbo Kachari Grace Chiwone Tiffany Milanzie Bright Sibande Noxy Chako Essie Ntsako Maria Banda Zione Kwabata Rose Juwawo Emma Lumwira Mathias Ngoma Ireen Phiri Ephraim Kumbukani Nkhoma Memory Gwaza
kkkkkkkkkkkkkk ati ndie amatchukitsa kuti iwo ndi anthu ophunzira ndi odzindikira mmalawi muno kuphunzira kwake koononga nako zitukuko izi ndie zitsiru zotheratu mtundu otembeleredwa uwu kuda ndi mitima imene mbwenumbwenu
Aaaa iwe sudziwa kuti achewa ndiomwe adzadza kuno kuchita u vendor?
Ndikudabwa nanu achewanu coz if u don’t know, 70 % of these vendors are chewaz nde muziziwa kuti mungonena abale anuwo .
U r very wrong? What do u mean wen u say mbwenu mbwenu? STOP zat
These people are enemies of progress, stupidly at its best. We don’t want people
like them in this developing country.
Hehehe,malawi will never develop,,keep waiting
Even if you’re poor, you don’t destroy what
You only have. And people with the mindset like your’s are the ones that’re keeping Malawi under poverty line.
We want more of this, development without this can’t be called development….. we’re pple are…. this should be happening more should come….. we need this more of this and killing should go on too
Just bannish these ungrateful rascals.
Ku Blantyre ife tikufuna stadium, inu mukuithira moto,zanu izo!!!!
Shame shame
Ndichifukwa chake madela amenewa kuzakhala kovuta kuti kutukuke
Choncho ma donors omwe adaperka ndalama zomangira stadium angakondwe with this barbaric behavior? A Malawi vuto lathu ndi chiani kodi? Bwanji kusafuna kudzudzulidwa pamene tikuchita mosemphana ndi malamulo? Go back to school you barbaric vendors mukachotse umbuliwo.
Catch all of them and give them circumcision
Tonse timapsinjidwa ndi malamulo ena ake mwanjira ina. Koma solution singakhale kuotcha chitukuko. Tikatero ndiye palibe chingatsale mu Dziko lino. Tima stadium take tammanjati kuotchaso
stadium ndi mavenda zikugwirizana chan akufuna stadium ukhale msika azikagulisira pakapinga aaa!!shame dead north will nt end zausiru mpira azikasewelera kuti judge thm lyf in prison
if the city had to remove thos Timber sellers to new market,and share the vacant to small scale vendors,such damage would have avoided.to the stadium that is good development,we need MZUZU magnificant,international Stadium
Enanu amene mukupanga comment apa u dnt knw the story behnd, bwanj mukungowona side imodz. Mind u thse vendors hav families to look after so ngat a city akuwaphwanyra ma shop awo iyo akadyera kut?
are you trying to back these vendors on this development? ndie apezano Ndalama zothandizira mabanja awo mmene awononga infrastructure ya stadium mo?kuganiza mobwerera mmbuyo uku
If They Got Their Families To Look After So What??The Mulpractce???
nde ayasa stadium apeza zakudya ?
Mind you ths is not the first time kut a city kuphwanya ma shop ama vendor, anthuwa analowetsa ndalama zambiri kumanga ma shopwa pamwamba pake a city omweyo the come kuzatenga yamusonkho en yet a city omweyo ndkumabwera utsiku kuzaphwanya ma shop, does it make any sense? Ku stadium kuja kuli ma office a city that’s why ma vendorwo anakawotcha kumeneko.
Amangeni Amenewo.
U Savage anthu akumpoto muzithawa kwanuko kuti kulibe chitukuko muzizadzaza Ku L’s ndi Ku BT kupusa kumeneko
Mabulutu APA Mzuzu
Take the vendors to task its too stupid to behave like you not a Malawian,who are this vendors,don’t let them go free,may be they want mzuzu to a country on its on,no football in mzuzu kkk,mwaziluma dzanja ana a njoka
Eshhiiiiiii this is bad, if you have space in mzuzu prison, onse apite basi
Kulilongwedi zitatero koma mmm sanapange zimenezi well ana osuta chamba ameneyo agwidwe sionse mmene muja munali anthu amitundu yosiyanasiyana atonga ayayo achewa alomwe koma kungoti anasuta agwidwe basi
Tumaresources tyakusowa nakale utu mucharo chithu mbwendipo imwe mukaotcheso,Ndipo apa wamusankhilani nakale pankhani yachitukuko mukhale nthena,wachule awa
umbuli ndi vuto
Catch them and castrate them!
Dont look at one side plz amalondauto ali ndi ana makomo ofuna fees ndi chakudya zosezo zimachokela mmalo omwe awaotchelawo kodi mmafuna azikagulisila kumanda
Nde kuganiza mopeperako! Paliponse pali lamulo which must be followed.
I second u mr
I second u mr
I second u mr
Akuyenera kuchita malonda motsatira ndondomeko za boma. Mmene apanga chiwawacho apezapo fees ya anawo?
Amene ali ndi Ana ofuna fees ndi aku Mzuzu kokhako,amalonda aku BT ,LL ndi Zomba sanapange zotero.
Very good questions @ Mr Namwera and Numeri
Ena mwa ife kusamusidwa kwa amalonda ku Limbe zinatikhuza mpaka fees nkuyamba kuvuta nnazionapo my parents face dis be4 ndondomeko yanjii imafunikayo come here 2 R S A muzaloze komwe amawaunjika amalonda mkumapanikizana kkkkkkkk that iz whay malawi is the POORest country after 53 years
I can imagine an angry vendor shouting in Tumbuka. Must be a hell of a scene!
Mavenda akuno siatumbuka
????
kkkkkkk shouting in Capital letters neh
Zisakomele mbuzi kugunda galu,Tit for Tat
malawi
Why are we doing that canont help malawian verry soly.
Mbuli za anthu
after torching stadium and assaulting mayor, what is the benefit now!!!!!! kkkkkkkkkkk
kenako mudziti boma silikupangran zitukuko anyan inu agalu atokhwetokhwe stadium yalakwa chan…..
Mcp uahundika ku mporo rsopano
amangileni ndende
Aziti boma silitukula ku mpoto…
Stadium yanu, Kenako muotcha chipatala.
Ukanena kuti adziti boma silikutukula ku mpoto kodi mzuzu stadium idamangidwa mu ulamuliro wa Dpp?
Kaliba Ofatsa am from north koma zikuonetsa Kuti mind ili poor.
Felix….
You are right.
@ Kaliba Ndale zinakulowani mopusa kwambiri.
Mmmm Mr Kalimba Ofatsa, sizandale izi plz.Ndiye chipani china chikalowa m’boma tiziononga zitukuko zonse kuti tiziyambilaso?
Malawians with mypic minds
Kumpoto kosalira kale ngati uko tizinthu tomwe muli natoto mukutiwotchanso? Kuwuma mitu.
Ummm kuganiza mopelewera basi ndi gulu lija lot layambana ndi akazi awo limayamba kumphwanya mapoto
Vendors moti amaotchaso ma tyre lero
Shaaaa koma Atumbuka inu nde munazolowela ukapolo basi mukangoona kabwino koma kuwononga aaa ayi boma lichitepo kanthu osazazimangilaso zisilu zimenezi kumpoto chitukuko chisazapitekoso anthu ake ndi atumbukadi ndaziwa sopano iiiiii
Uziwona wakula watha
Children of devils always insults.
Guys kumanena bwinotu
I challenge you upite msika uli onse mmalawi muno ukapeza chiwerengero cha mavenda ambiri ndi ayao nda chewa nde musathe mau bambo nda che bale anu apanga zoterezi
ma vendor ndi achewa, ayao,, olima fodya kaya ntchito zapanyumba ndiwomwewo ma brothers ako, uchita uhule malawi yenseyi ndi achewa
Musanamizilepo apa iya nchewa yao mlomwe sangapite kumpoto ndikumakapanga zausiluzo inu achina simmbweni ndame mwaotcha mulibe chitukuko inu
Tizitukuko take tammanja tili natoti nkumatiyasanso???.
Ku BT ma vendor adasesedwa mmisewu ndi malo osayenera palibe chomwe adayasapo same ku LL what’s wrong with these Mzuzu vendors?.
Ineso ndudabwa nazo
Kumpotoku chitikuko nchovutavuta mmalo mozimvera chisoni ayi ndithu ???
Mbuzi za anhu zisiyeni ndiye chifukwa chake Dr kamuzu banda amati dead north
Simukunama. Tizitukuko tammanja. Ku Malawi kuti chitukuko chibwere mumachita kugubilaeeee.
U guys those are some bad comments
Choti mudziwe kuno kumzuzu mavenda ambiri ndi ayao ndi achewa ndiomweso apanga zimenezi
Maludha is rite
And wat u shld knw is a city anawachotsera ma bench omangamanga oti sanaliso mmbali mwa nsewu,,,nhati iwowo a city new kuti ma benchwo sali malo oyenera why did they allow them kuti amangepo in the first place???,,,u shold follow tje story first b4 commenting negative comments
MTUMBUKA sazatheka
Koma ndiyetu,Malawi of fire.(FRAMES)
not good
I was there very sad development.
what is the purpose of the world contact and dialogue, poor vendors what is wrong with the stadium. Investigation into the matter and punish them
what is the purpose of the world contact and dialogue, poor vendors what is wrong with the stadium. Investigation into the matter and punish them
We are poor Malawians and poor in mind as well why torching the stadium. Shameless people
umbuli uwu
Malawi following her nose towards the ditch mxiew
Send MDF
Maganizo opusa! Ndiye zomwe aonongazo a MDF akabweza
Ndiye muziti boma larephera kupusa
people stadium has done nothing wrong. why torching it?
moti aitanitsane wamkulu was ma vendor ndi a mayor kuti akambirane. why torch the stadium. Ndalama zomweso zikonzetseredwe stadiumyo bwezi atapangira chitukuko China.
These are criminals not vendors
So sad. Umbuli unakula ku Malawi
Coping South African style. Mukuiwala kuti maiko a anzanuwo chitukuko chimapangidwa everyday…musatitopetse atumbuka….mxiii!
You rarely find tumbuka vendors in mzuzu. Being in the north is not a valid reason of being tumbuka. Grow up man don’t sell your stupidity in public.
oooo malawi shiiii
Malawians with anti development mind! next aziti boma silikutithandiza pachitukuko yet you are torching stadia.
So sad