Nobody can stop Mutharika and all those who think they will break him are wasting their time, that is according to musician Saul Chembezi.
In his latest release, Chembezi has joined musician Joseph Nkasa to heap praises on the Malawi leader.
Among other things, Chembezi praises Mutharika for constructing roads and opening community colleges.
He also sings that Mutharika is on another level owing to his ability to run the country without direct donor support for two years.
Chembezi has been known to be sympathetic to the ruling Democratic Progressive Party (DPP) and on the 2014 campaign trail he used to partner with Sendera sisters to sing for Peter Mutharika.
I lyk the guy, Dpp is in my veins. 2019 am coming home just to vote for u prof.
Kkkk nawo a VP .
.
Moti Azimupembeza Mulungu !
Nosense
Saul Chezembe is still alive?shame he’s trying to make himself relevant
Kikkkkkk chembezi mbolo yako ndiwe chitsilu cha munthu malete ahawu mutu wako siugwila ntchito upite ku chipatala
Musician wasauka
Sakunama, kugwa mmanja mwa Mulungu,ndi koopsya. Kusiya ndale kukayamba ubusa, mzonveka kma kusiya ubusa kukayamba ndale, mmmmmm very shem ,, ndikutha kuona Mutharika akuwina 2019 mosavuta
Akudyanawo
Amudyetsa chibini laden
Leka zimenezo wadumphila ngalawa yachabe ingopitiliza Music yomweyo
Phungu Nkasa , Soul Chembezi , osamalowesa ndale munyimbo zanu ,think about anthu amene amagula nyimbo zanu . Its not only DPP people, but each and every Malawian and yet si onse amasapota DPP, mind u, business yanu izatha DPP ikachoka muboma.
Anyway gold digging haa haa
Anasauka awa akufuna chithandizo
Another level yotani?yolephera kapena yakuba.2019 Nonse muntharika ndi Chembezi mukakumana kwa ngolingoliwa,chifukwa ndi kumene mutakakhale.
Kkkkkkkkk aaa ndidolo anthuwa akuimba koma sakugulisa obena achuluka.
Wangoganiza zoyamikila president pot ndikomwe ambiri akutola chikwama.
Walemba zosaveka’amalawinose! Patombo panu imeneyuso ndikhani yoti muzikangana
oyimba akuMalawi akatelo maluzi amenya ndie akufuna dollar
Kusasa ubongo a chembezi ayi mukuitha kupempha mwalus
He nids money he is like mkasa
hahhaha he has chosen a wrong way of coming back in e music industry
Mbuzi iwe president wa dpp
kkkkkkkk alipobe woyimba ameneyu,atachekera maluzi nkuona kuti mbali imeneyi zimadibwa mophweka
Munthalika is good for nothing. I have never seen any progress yet from him.
Kufuna kudya naye kkkkk
A big fool called chembezi trying to make fast money from the DPP.
Mwana Wanzeru Uyu!! Enanunso Aimbireni Nyimbo Anuwo!
palibe wapanga mtsongoleri wanuyo kaya akamamaliza term yake azati wapanga chani? mwina ma ID kapena mbalame ya munthu
angofuna adye nawo amene, ma style ndimomwe zinthu pa Malawi zavutira, kkkkkk
DPP yafumbwa basi
Olo apm-yo akamagona akudziwa kuti palibe chake game yalakwa basi
Chembezi uli mmaluzi iwe.
umphawi wsngomukuntha afuna adyeko ca 2019 campaign. useless malawi musician they lack vision, kutchuka kopanda phindu
Chembezi ukuona ngati ukukhoza umuuze zoonadi peter wakoyo kuti MCP ilowa basi anthu pano achenjera kubera mavote kulibe man uzasaza wadyazo wamvaaaaa!
He is singing in support of cashgate thieving the Dpp government is busy at , sewage pipe water supply to the people of Lilongwe, all Malawians are not fools like him
Chembezi as one of the Malawians have a freedom of expression as stipulated in Malawian rules. And you all who are criticizing him that is your rights of speaking and decision making. No one is bad here or doing wrong here
that’s TRUE come 2029 pipo will believe that he is un breakable
Watha ma plan Kkkkk
Useless person n i dnt knw dat he is going to hav for upcoming elections,
Bola usakumane ndi panel beating like Nkasa ku Dowa
Alandila zingati koma munthu okonda dziko lake angamasangalale ndi umbava onseu shame Malawian
changa chala ichi nkaviika nkuchonga pa DPP pooo kut chonguuu….. …kwathu amangako stadium,,,,,kkkkkk
Wadyetsedwa sikono,who can vote for DPP,may be bcz many Malawians are blinded
Chembezi is going mad and he still don’t know what is happening in Malawi.People are in great trouble because of peter muthalika.chembezi and mkasa are stupid Gueyes.
Akupatsa zingati kodi iwe Chembezi
Akupatsa zingati kodi iwe Chembezi
Saul Chembezi Ndiye Uti?
Kkkk wadya nawo lol
Is this worth a news? I doubt the depth of news you call news.
So even if Gwaladi praises Mutharika you’ll write. Blasphemy.
To some people democracy you are collected when you praise opposition parties…. PP did the cashgate but they have thousands supporters.. MCP Fed people crocodiles they have millions supporters… A chair adapakulanso zawo but UDF has supporters…DPP has also it’s weaknesses yes but is the ones on driving seat.. have millions supporting it don’t make mistake about that kkkkkkk
wise comment indeed with back up examples.
Mbuzi ya oyimba shit!!!
Soul Chembezi???!
Thanks for good roads our president northern region
Getting Fame Is Simple But How I Wish Wishes Were Horses Then This Small Rat Chembezi Could Ride To A Certain Extent…..Chembezi Feels Mutharika Is On Top Of Everything,,,Alas!!!!! Thats A Total Joke Of The 19th century….
chembez wasauka afuna ndalama kucoka kuboma.
After atawoona kuti sizikumuyendera wangoganiza zonamiza bwana kuti awadyere .udzabweza iwe ukuona ngati ndindani angavoterenso umphawi kuno kumalawi walemba m’madzi uzabweza utapatsidwezo
Umphawi ndiwovuta kwambiri umapangitsa munthu wamkulu kuzungulila mutu
Palibe chabwino kusekelera zosadziwika
ZA ZZZZZZZ
we dnt need ur opinion here we a nid facts and shut up ur wilthy mouth
Chembezi u do the same with Mkasa ?But do u know what was happening to Nkasa at Dowa? please quit it my coz u will face the music oky!
yeah time to make mula go on bra
Andale nonse ndi akuba
Who is Saul Chembezi
Saul chembezi ??son of bitch asatinyasepo
To Him It Is Right And What I Can Say All Politicias Are Liers Therefore It Can B Better To Praising Lord The Father All Fathers
Oooh ukunama iwe chembezi ukungofuna money
Thats dreams of poor sighted people
Just keep doing what you do best
Mbuzi yaoimba iyi ikagwere uko
He is recognised as a musician……… Yawn
Zoona it’s 2019 woooo boma iloooo….
A sell out pauper who has literally nothing to offer malawians for simple attention. oh poor Soul!
Angofuna kuwadyela bwanawa
kubwera kwa mai kukhala kwa zeru
kubwera kwa mai kukhala kwa zeru
Ndikukaika kuti Mia ndi Mcp kuno ku lower shire mkuzapatsa mwayi chipani chapa chigawo chapakati
Malemu Chembezi alipo kkkkkkk uyi ndiye anathadi ngati katani loooo zoti ankayimba ngati bodza
Thats his own opinion, and vote its a secreat thing, what is good for him isn’t good to everyone, so let him praise Dpp the way he want because its his human rights to do that. Hate it love it but he can’t change his mind of supporting Dpp bcoz of u, u can say whatever u want here but it won’t change or put chakwera in that position of head of state. Just waite 2019, then all will come to an end!
Hitting the nail on the head
Ndiye ndikamanena kuti malawians very stupid pipo wina aziti ndikulakwitsa eti? Omwe mukususana ndi zomwe chembezi wachita bwanji nanu osagoimba yanu kuyamikila tsogoleri wanuyo? Gd in criticism poor in doing very stupid pipo! Let Muthalika rule dis country. Inu amene simukumufunanu wait till his 10years. MCP can’t rule Malawi again, kodi mumasagalala komatigulisa makadi? Kumati manga nyakula, kukawadyesa anthu ku ng’ona? Inu maufi ngati mwasowa chochita pezani zina coz mcp will never rule Malawi again. Do u think 18million malawians can b developed by only muthalika? Inuyo what r u doing 2 develop Malawi? 18million r de ones which r stupid coz r waiting 1 person in de name of muthalika 2 develop them.
Ukafunse agogo amapanga zimenezi popeza Ku M.C.P kulibe anthu amene anapanga nkhazazo..
if malawians r stupid and u r stupid too
zipani zosezi kungotchulako Mcp sumagona nayo tulo eti ?
This another Chembezi.
Childish reaction from a typical dunderhead.
kodi iwe bwanji ukudana ndi mcp,ndiwe galu eti,chitsilu
Ndiwe Muhlomwe?
Kkkkk mcp ndiyomwe inazuza anthu kumalawi kuno. Inuyo ozitcha ophunzilanu mwapangapo chani kutukula Malawi? Which policies r u talking about? Gd in insult other yet u r doing nothing. Chembezi has done a very gd work polingana ndi mene iye akuzionera zithu. Nanu imbani yanu yoyamikila sogoleri wanuyo. Stupid pipo r gd in criticism and blaming without solutions.
dickhead,M.C.P was better than D.P.P mbava…
#luciano which better! Zoti kamuzu akamapita any where outside sanjika ana a xool around BT osaphunzirazo? Za makadi, kudyesa anthu ku ng’ona, kukwapulidwa ku erio was zat better 2 u? Kulesedwa kumaga nyumba za upstayer kuti ukufuna uziona chani was zat better u r talking about? Can u tell me zat during mcp era Malawi was rich?
mboliyako galu
Yes munthawi yakamuzu , zinthu zinalibwino. Kunalibe njala, Kamuzu ankapereka zipangizo zaulimi kwa anthu osauka kuti azikhala ndichakudya chokwanila.maphuzilo anali amphavu, ndipo munthawi yaulamulilo yake anthu amayamba kuyankhula English Ali standard 5.. Chitetezo chinali champhavu, ndi kuti munthawi yankuluyu kunalibe kuphana mwachisawawa ngati lero,ndipo anthu ankayenda mitunda italiitali chifukwa chitetezo chadziko chinali champhavu… Zomangamanga, ndi kuti munthawi yankuluyu anachita zitukuko zambiri zomwe ma president anthawi ya Democracy sanachite, anamanga maoffice aboma monga ngati capital hill, manyumba ambiri( Malawi housing) miseu,njanji,ndi steamer za Mmadzi (mtendele).. anamanganso university of Malawi like chanco komanso Polly ,bunda …mwachidule zitukuko zambiri ziliM’malawi pano anamanga ndi Kamuzu..
Stiff necked fool nde Ntchembele kaya Chembezi
#j-luciano i can see zat u r N0T stupid lik many malawians who r gd in insult on social network, i totally agree with wat u r saying, tell me kodi nkhaza zinja was it part of development? Nanga zokakamizana makadi? Kudyesa anthu ku ng’ona was zat part of security? Do u know zat anthu a kumwera anazuzika kwambiri ndi mcp? I always say chakwera can b a gd leader but de party mcp mmmm its too bad. And we can’t make zat mistake aloweso boma. Malawi watukuka kwambiri muthawi ya democracy compare how it was looking lik in 1994 and 2017.
#luciano thawi yomwe tikalandira chimanga cha yellow chotchedwa Kenya how old was u? Even mu thawi ya mcp kunali njala tikakalandila chimanga cha yellow ndi sugar plus nandolo and sometimes punga. By de way what r u doing 2 develop Malawi? Sitikuyenera kusiila tchito yotukula Malawi munthu modzi, and tisiye zondalira munthu modzi anthu 18 million kumatukwana munthu modzi kuti sakutukula dziko. Thus very bad.
ah a enock here in malawi if there big fool its u why i say so bcoz of vs things, (1) u do know the leadership of kamuzu we him ngwazi and here in we never find other guy like kamuzu (2) u dont know wat iz mcp coz 4 example chaponda anasokoneza kagulidwe ka chimanga kod pamenepa tingamati DPP inasokoneza (3) ukukamba za makadi kod ku malawi kuno sakupeleka msonkho ngakhale mwana oti sanabadwe alimimba mwa may ake kupeleka so dont think like tortoize
Malawians Ndi Anthu Ovuta Mukufuna Mutharika Azikupangilan Chan Kt Muzaone Kut Akulamulira Bwino Musaembekezele Kut Munthu Waulesi Azapindula Kukhala Olimbila Nde Khani Sizolozana Zala Pano
#yamikani ndikulephera kutolera zomwe walembazo. U r mixing 2 much, tandiuza pakali pano ndikuti komwe mwana akumamulipiilira sokho asanabadweko? And explain how? Issue ya chaponda isiyeni ambiri sakuivesa including iweyo. By de way what r u doing 2 develop Malawi?
People hate MCP because what Kamuzu did back in th 90s.
Like seriously ? you people are damm nothing but low thinking
#levison it was nt kamuzu alone, its mcp i remember kamuzu adalakhulapo pa khaza za mcp ndipo iye adanena kuti samaziwa kuti chipani cha mcp chimazuza anthu. Sikamuzu yemwe amakwapula anthu ku erio, sikamuzu yemwe amagulisa makadi kwa mwana osabadwa. Sikamuzu yemwe amalanda ng’ombe, nkhuku ndi mbuzi koma mcp
So tell me what is MCP kwenikweni?
Nthawi yanu inu oyimba kuti muwadyele ndalama anthu andalewa.
Achembezi nañu mukufuna mufanane ndi Mkasa? Ndale timayamba ntchocho. Mugwa nayo achembezi.
I have never seen IDIOT like this fool musician who knows nothing how malawians are struggling to find their basic needs in Peter Mtharika time and if there are many idiots around the World this musician is the first one (no 1)
Kkkkk..Oimba apa Malawi
Hah Ah ah ah ahhahaahha soul chembez !!!alibe kalikose ngati tili ndi oyimba omwe akumvq akuwala it’s him ndipo ndiwopusa bomqa Lake liti akuyamikilalo aaaaaa ukoooo
Kodi ngoyimba?
awa agundika chilichonse akuyankha ndiiwowa mmalo mwa dausi
makadet muuuunya ndithu mmodzi mwa iwo ndi uyu Ian Clarence kkkkkkkk
Papaa Jozee anthuwa akundinyasa akulimbana ndi munthu what for? Kkkkkkkk
These poor musicians are saying so just to fool MR President, unfortunately author(Peter) is unlike some other Presidents, will give him nothing
kodi saul chembezi ndi kanyama kanji kapena ndi ntundu wanji wa matayala a galimoto?
kodi saul chembezi ndi kanyama kanji kapena ndi ntundu wanji wa matayala a galimoto?
Lost sperm
soul chembezicho ndiye chichani ngati wasauka angonena ife ndiye amene tikuvutika ndi mbavazi voti ili muntima zupusitsanani choncho
Kkkkkk kkkkkk the so called musian!!!! My foot
He is just looking for sympathy……Koma its too late..
kod a bambo chembezi mulpo et?kkkk!!
Even if you call a musician I don’t recognise him, do we have in Malawi a musician Saul chembezi???.
Do you people buy his songs
? I don’t like him even if I got his songs
Who are u to know him ?? Dick head
Nosenu mungoti soul chembezi walakwitsa,ndiye kuti chembeyu galu zedi eti? ochembe-ochembe uchitsilu sudzakutherani.
Ndizowona zimenezozo anthu angati alephera kutukula Malawi? ndiye mukalimbane ndi munthu mmodzi! Why only Mutharika p? mumusiye munthu alamumure momwe aganizira, ma plan anuwo mukadzawina mukutinyasa makamaka a mcp sitikusowekera nzeru zanu munthawiyi!! ndipo simudzawina khalani pansi.
Zoona Ku Maphunzirodi Apm Sangafanane Ndi Adzinawo! Koma Ku Utsogoleri Mwina Bola Adzinawo! Be Frank !
Kodi choir ya Saulo chembezi idakaimbabe??? Anthu angaikondenso imeneyi masiku ano koma?? Tinyimbo take sitomwetija tinapanga chuku ngakhale pa radio sitimanvekanso, nanga angakambenso chanzeru chani kuposa kufuna kuzigulira ufulu ndi tindalama ta DPP. Ukhaula ada masiku ano anthu akuimba tofewatofewa wazidziwa???
Kodi choir ya Saulo chembezi idakaimbabe??? Anthu angaikondenso imeneyi masiku ano koma?? Tinyimbo take sitomwetija tinapanga chuku ngakhale pa radio sitimanvekanso, nanga angakambenso chanzeru chani kuposa kufuna kuzigulira ufulu ndi tindalama ta DPP. Ukhaula ada masiku ano anthu akuimba tofewatofewa wazidziwa???
Fortune seekers .If Mkasa did it,Chimbezi is following suit .I am a Thief myself,if I give Chembezi ,Mkasa,5m each, it will be all praises.
Mabanzi amapangitsa oyimba kuti ayimbe zabodza
That’s what happens nowadays. This guy wants to be recognised and gain something at the end
Kkkkkkk wakupweteka ulovatu wangoganiza ndikungolowa ndimeneyi kkkk
Umphawi sizinthu idiot chembezi
Chelsea 2-3 Burnley
And that is why he is not famous as Lucius Banda, kukula mopusa, is he blind enough ?
Singing tchekera maluzi hahahahah!
pa Nyasa?Lols
Anthu oyimba inu mukaona kuti sizikukuyenderani mumakhala busy kuwombera mmanja chinyau chomwe sichikutha kuvina!!Dyera la ziii osabwelera kumudzi muzikalima bwanji?Nzako Nkasa wasanduka nazo chitsiru!!Osaona anzanu a Lucious Banda aja akuimbabe ndipo zikuwayendera!!!!Ukanakhala wanzeru iwe Saul ukanangoyamba kutumikira Mulungu osati zomwe ukunenazo!!Ukapatsidwa ndalama ndiye ukuona ngati tonsefe tapatsidwa?Anzako akupita kumakaimba mumatchalitchi akunja iwe waganiza bwanji????Osamawayamikira amai ake amene anavutika kuti iwe ufike pamenepo bwanji?Mukasauka kumawapempha atsogoleri adzikowa mwabwino osati kuwanamiza!!!
GOOD POINT….. Inenso ndinayiwala kalekale kuti paja kuli oyimba Saul Chembezi.
He is just on point.. Apm all za way….
Maluzi penapake siabwino ndithu,,ndaonera Saul chembezi
Amalawi akasowa zoyankhula,chomwe amaziwa ndi kunena zawina.Inu pangani zanu ameneyi ndiye Kaduka.Taonani zamene mukuwanena ngati Peteryo,iye akupanga zake ndipo zikuyenda.Amalawi tikatenga kwambiri zandalezi ndithu palibe chomwe tingapange pamoyo wathu.Mwachitsanzo: Boma kungosintha,muzaonanso ena omwe ali m’boma pano alinso m’boma linalo.Malawi zuka tsopano.
Anali kale nyimbo zawo zimayikidwa proglam ya make dzana.mukanati Lucious banda bola.
Awa ndi manyaka oyimba inuu iyaaa
just wailt ma poem
When you are bloke your brain is corrupted to clap for dirty things.
Adyapo koma angodzinamiza sanayende Malawi yonse
Who is this idiot Saul Chembezi?
Fools praise useless Ideologies like this so called Chembezi
Chembezi akuyankhula ngamo. Oyimba ngati awa amaona patali
owoo Sol chembez!even his songs does not make sense to,
Mbuzi imadya pomwe ayimangilila
Useless creature on earth. Never seen such poor musician in Malawi. Sorry for u chembezi….may be u r looking for sponsorship for video shooting….
Mxiewwwwww inunso nde ati hahahah busy minding peoples business osamapanga ZANU buanji
Mr, we are in a democratic world so mind your word.
That’s am free to say it coz it’s democratic world
Tidikire tione, chilipo chimene akufuna kupemphetsa. MMalawi timamudziwa samangoyamikira kumakhara kunyengerela.
Aaaaa siuyu amati kanyenya chips kunyumba kuli thelele kkkkkk afuna atapileko naye ku dpp angatiuzenji iye uyu azingogulitsa akanyenya akewo
We r about entering campaign period, it’s time to make money from these politicians. Therefore Mr chembezi is trying his lucky. Not all of us will get from the ruling others will get our mteleshede from the apposition. What we need is to be very clever.
At the very same time he is demolishing his career coz naturally people hesitate to support those who support their opponents
This niggar he is broke
after failing to source enough money through music now you want peter to sort out your financial problems,,, bt peter himself knows that he is afailer and ind is desperate in winning back peoples support
That is how he, Saul Chembezi, has seen it. He could be right after all or wrong. Still, he is within his rights so let none condemn him. He has a right to opinion as everyone is.
I don’t think it’s right to condemn Saul Chembezi and call him names. He has got a right to his opinion just like you!! Politics is a game of having different opinions/views and choices…. Period!!!!!
Well spoken sir.
Democracy???????
Yes Andy Andrea Andulu, I just mean that. In democracy one has got a right to express and stand by his/her own opinion/view as wrong as it doesn’t injure on harm others. That’s why we have different political parties with different ideologies and all of them have got members. In this case Saul Chembezi is exercising his right
That’s a stupid opinion, if u have nothing to say u gone better shut up
I believe there is no issue of bringing up such bad words please. I’m sorry if I have spoken anything hurting Mr Samson Brighson.
Samson Brighson has a Dick head don’t mind him
Well said bro
Mr bad do you waste time with people without brain… what you have written is 100percent correct.. 18million can not think the same and any sane person my bear in mind that and ready to respect other people’s choices or opinions hahahaa
tikanakhala ndi anthu azeru ngati inu ochuluka,bwezi mdziko muno zithu zikukoma…mwayakhula mwazeru mr oster elijh banda
Because of money people have been channeled to wrong parking. Chembezi has gone insane and we know what is behind him
Even Judas Iscariot was thinking it was wise to betray Jesus without knowing that the majority of the disciples were not with him in his wayward thinking so too is this bootlicker musician!
Attention seekers
Nyapapi mbuzi akona ngati alandila anasuta chochuluka kkk
Shame on him ndipo siwoyimba uyu manyaka awa anthu omwe sangathandize dziko ma gulu ake ndi awa chitsiru cha munthu he is blind
imbani mene mungaimbile vote ndi mumtima.
Palibe chanzeru apa
Aona ngati kulamula dziko ndi magatala
I dnt evn know u who z soul chembezi
Umakwana soul and Peter nyimbo zako zili booo 2019 bomaaaaaaaa!!
Akupatsani zingati?.
Akufuna ndalama chembeziyu sakudziwa ndindani kodi
Money hungry you idiot, standard 3 for sure, no brains at all Mr Chembezi . Just keep on playing your useless music.
Useless music indeed hhhhhhh
Dick heads, power hungry idiots 2019 APM boma kuti pyooooooo mulira simunati
you too your dick head,iwe ukuona ngati wabwino wabwino,iwe chi dick head..
When did u study political science?
Ingolowa politics.usatisokosele
kwacha ili paminga.ukamufunse mkasa
Kkkkkk….even ma cadets ali ndi ufulu oyakhula zakukhosi kwao…
Kodi is it wrong for a cadet to dream akumwa wa mkaka mpaka 2024….?
After all ndi maloto basi….
Sikuti kulota utakwela ndege nde kiti ukwela ndegeyo kkkkkk
Kuyankhula mosaphyetira palibe munthu yemwe amakhala 100% kwa munthu wina chimene mumakonda sichimene ena akonda ngakhale ife tomwe sitingachite chili chonse chabwino kwa makolo athu, ana athu, kwa mkadzi kapena mwamuna wathu,boy frnd olo girl frnd wathu China chakebe chikhala cholakwika basi pamaso pa wokondedwa wathuyo A mutharika achitako ndithu zina zabwino koma chifukwa ena tinabadwa ndikungodana naye munthu olo atachita zabwino zochuluka bwanji singaysangalale nayebe chifukwa nzeru zathu umunthu wathu tinaziika kuti munthu yu siwabwino nchimodzimodzi Yesu mkhristu mtendere ukhale kwa iye m’mene anali pansi pano anayetsetsa kugwira ntchito yotamandika komabe ena anadana naye ndipo akudana nayebe pana pano nde munthu ameneyo bravo chembezi
malawians are very politically biased.the ones that were madly praising jb when she was plundering the country are the ones hating pm.udf stuppoters hated pm before dpp/udf venture,now they are quiet.just becoz jb is married in the north many northerners who are noisy were quiet when she was shocking this country’s economy.if chakwera comes & doing nonsense,the chewas wil remaing quite as they did whe tembo/ was subbotaging sub-sahara electrification program.now lomwes are happy praising the cold governance of pm,when someone comes they be busy snooring.generally,we malawians are political robbots of the political elites.shame on malawian democracy!
musician? kkkkk what type of music?
Au drunk or what chembezi? Can u please shut your Dirty mouth…. Coz u dont know what your talkng about son of the bitch dmn it.
Wanena Maganizo Ake Musiyeni,kuganiza Saletsana
Thunder fire him
kkkk
Who is Saul chembezi? You’re talking about broke ass nigga, come on ..he straggling with poverty.ndiumpawi ukuwapangitsa ,achina Tay grin, fredokiss ndi Lucius Banda samapanga nao zopusanzo chifukwa Ali ndi ndalama..ati Saul chembezi sinzake wa Joseph nkasa ameneyu..
Kuzisaka oyimba.market yavuta
umphawi umapangisa anthu misala..
Nkhan nd maluz bac
Is he God himself?stupid moron
Bwampini adzawona zakuda 2019.And dpp idzatheratu. Amalawi akakwiya sabwereza zithu. Anthu mukudziwa.
ZOONA
Kodi akulu amenewa nyimbo zawalaka even composing a song akukanika ndiye mukuganiza kuti angayankhule za mzeru?
hahahahahahahah akupasa zambiri kape iwe
#pitaa levo ina remix u gat da swaggs……
No doubt Muthalika is especial oneeee
Zooona dpp boma
chembezi what do you know?go to hell
Umphawi Sizinthu.. Saul Chembezi Alibe Kanthu Pano Ndiye Akufuna Azipanga Za Nkasa.
akufuna ndarama basi
Thanks Mr Chembezi for speaking ur mind. Even though others r seeing it negatively.
Money is talking here NOT Saul Chembezi
akudziwa alibho
His fellows are praising God, while this ujeni is busy washipping Idohs. Maluzi awa.
Umphawi sizithu guyz. Chembezi ndi ku malawi?.
napamenepo ndalama wazipeza iwe umayitha uli bho
Chibanzi chili mkamwa
He Is Right Muthalika Ndi Level Ina. Kkkk
Ingotpasani nyimboyo tivere tonkha
Yah he is right no doubt about that
Muthera limoz muona kkkkk
Kodi a Saul Chembezi alipobe hehe lol
Woooow is first time to hear about Saul Chembezi involve himself in politics
Osamuphera.ufulu.mzanu.ndimene.wawonera.iyeyo.mukufuna.azinena.zomwe.mukuzifuna.inu?inuso.kamban.momwe.mukuwonera.inu.kungozolowera.kumangotukwanizana.basi.shame.on.u
Maluzi akamugagada munthu umayankhulatu ngati kwanu kuli maliro. Chembezi nkachaniso
Kaya abale…
Maluzi amutikita #Saul Chembezi akufuna awabele aPeter style ndiwekha yayandikira nthawi anthu atchene zaulele zachipani
paja unaimba adzisiya this time udzisiya zimenezi
Anali kale pano anatha ngati pant Chembezi
Thats the only way you may revamp,what else munatha
AKUNAMATU
Who is Chembez after all,a broke boot licker looking for money
Dick head, useless comment what’s wrong for him to choose his side, mind yo own business n learn to live the life
Auze chembezi.
Just beg than talking nonsense
What do you expect a musician who enjoys mapwevupwevu from DPP to say?, If DPP is out of government he will change the chorus.
In fact he is DPP sir even when it was in opposition. Most of the campaign songs for DPP were done by him. Blessed afternoon boss
kkkk Mr Mike Charles Banda do you think he can deny 10 milion kwacha if he can be asked to compose a song praising MCP? kkkkkk mwinanso 10 milion iyi yachuluka.
What’s wrong 4 him to choose his side u idiots n idiotess, u wanted him to sing praises for Lazalo?? Beside who gave u the guarantee that Chakwera is better than Mutharika???? Whether u need or not 2019 APM Bomaa muti nyoooooooooooooooooo
You are true Mr #Ian clarence# because ndikhalidwe lanu you will steal th the votes again we never wonder
Palibe zakubera ayi peter adzawina ndimavote migolomigolo mcp idzasinthe dzina kaye
ha ha ha nawe ufuna uwone cholowa ngati mkasa? Bring back good music stop acting as apolitician sizimatheka go n ask Soldier L banda
Saul chembezi nawo zazii
Kkkkkkkk who is saul chembezi abale inu
Tell that boy called Shembezi to shut up
lol broken brain Niggaz ar busy praising Stupid things
broken like bones or what?? R.I.P English
You did get me well. Broken brain
Mxm u think we did not see your Edited comment Levison Banda
I did edit yes so did I change anything?
lol bt dis country iz progressing though u say senselesly n nudity. linkupbwauy
Ma Graduate ?? apa Malawi ?? lol ?
a very very short cut to fame lyk kkkk
democry ndi ntchito zake!!!
Whatever you may say but its true that this silly blute like you is praising stupid things instead of praising God… critics are welcome
Whatever you may say but its true that this silly blute like you is praising stupid things instead of praising God… critics are welcome
Oyimba dyera zikawavuta kulibwino kumangolima basi
Who is this kid chembenzi
Afuna ndalama wausilu
Let him be, he has the right to support / political praise any party he want, what is good for u isn’t good to every1
kapolo wachabe chabe ameneyo ,anayimbako chani zooneka uyu,akutha ngati nkhumba ya masagwidi ija…
I can’t wait to Vote DDP again on 2019 general election coming
Thomas good Lucky
Mbuzi zokha zokha limodzi ndi Nkasa
kusapota chipani chomwetsa anthu sewage / manyi mmalo mwa madzi a malawi tidakagona tulo ndithu
akufuna ndalama ameneyo paja oimba akamaona kt czikuenda pamsika amathawira kundale bac
Stupid propaganda…