Madzi a ku 18 salibwino: a Water Board achenjeza kuti tudzi titha kuthudzukila kachikena

Advertisement
Blantyre

Mavuto a madzi ku 18 aja sikuti anapitilatu, atelo a bungwe loyang’anila za madzi mu mzinda wa Lilongwe a Lilongwe Water Board.

Wamkulu wa bungweli a Alfonso Chikuni anena kuti pali chiopsezo choti tudzi titha kuthudzukila kachikena mu madzi opita ku Area 18.

water tap
Madzi avutaso ku 18

Iwo amanena izi pamene bungwe loyang’anila za ufulu la MHRC linawaitanitsa pa kafukufuku wa umve umene bungweli linamwetsa anthu a ku Area 18 mu mzinda wa Lilongwe.

“Ma pipe a tudzi sali bwino mu derali, akhalitsa ndiye sakuchedwa kuphulika,” anatelo a Chikuni.

Iwo anati ngati a bungwe ali ndi mantha kuti ngozi inaoneka posachedwa yoti madzi anasakanikila ndi tudzi itha kuchitikanso.

“Padakali pano dera la ku 18 liri pa chiopsezo,” iwo anatelo.

Advertisement

145 Comments

  1. Zili ku malawi athu akumwa bibi koma tili ndi nyanya kulephera kukatenga madzi kunyanja akukatenga manyi kuti athu azimwa akamati dziko lino ndilimene satana anapangitsa ms

  2. Manyiwo akumwedwa ndi athu aku Lilongwe including ku state house ine ndimadwa kuti kodi president akungolalata misokhana wadya chani ngakhale midoli sangafike pamenepo mpamenendimamva kuti ku lilongwe athi akumwa manyi koma ndiye muli bhoo

  3. zikugwirizana bwanji pakati mapipe suwage ndi mapipe amadzi??zinakhala bwanji pamenepa mpaka kumamwa manyi? koma ndiye.

  4. Ndinagwira kachikheba ka ku 18 komweko koma ndakauza kuti chatha coz sindikufuna shude yemwe akuchokera dera lomwe anthu ake ayambanso kumwa nsete.

  5. Kkkk kodi tinene.kuti.vuto.ndi kukolola kwambiri nde anthu akudya kwambiri..mapeto ake kubiba kwambiri kokuti pipe zikumachepa?kapena pipe zatopa ndi.zomwe.zija.zakamuzu..53years pipe yosasintha kkkk

    Mundilakwira mwamva inu a water board.

  6. I hate such kinds of Reporters. What is “KACHIKENA ” Musationongere ana a sukulu. Am watching u. Tipatseni nkhani za mu Chichewa chathu chokhonzeka bwino. Mu chilankhulo cha lilime la amai.

    1. I even dont know if they are licenced to report. in other countries even online media agencies do seack permission to write.

  7. Most Malawians are too passive. If it was elsewhere, the affected households would have been heavily compensated and use the water without paying bills for atleast one year. Since it’s Malawi it is just business as usual

  8. hahahahaha mumanyoza area 36 kut ndkumudz kkkkk nde bolanso kumudz kwa ana osasamba kma timamwa zaukhondo inu ndiubwana wanu mukumwa ndowe za anthu mmmm nyansii

Comments are closed.