Wapolisi m’modzi watisiya ndipo angapo ena avulala dzulo usiku ataombedwa ndi galimoto pomwe anali akugwira ntchito pamalo ena a chipikisheni m’boma la Dowa.
Malingana ndi malipoti a apolisi omwe nyuzipepala ino yapeza, izi zachitika dzulo Lolemba pa 17 July pa mphambani ya Dowa (Dowa turnoff), nthawi ili 19:30.
Apolisi ati mzawo omwalirayo ndi a Brown Selemani a zaka 34 ochokera m’mudzi mwa Kacheta m’boma la Kasungu.
Apolisiwa ati panthawiyi, mzawo omwalirayo komaso ena awiri anali akugwira ntchito pa malopo pomwe galimoto ya mtundu wa Mekisedesi Benzi inawaomba.
Galimotoyi yomwe nambala yake ndi BU 4897 imayendetsedwa ndi a Clement Wyton omwe amachokera Ku Mponela ndipo amalowera ku Lumbadzi mumzinda wa Lilongwe.
Chifukwa chakuthamanga kwambiri komaso chifukwa choledzera a Wyton atafika pamalopo analephera kuongolera bwino galimoto yawoyi ndipo anaomba apolisi atatu omwe anaima pa malo achipikisheniwo.
Apolisi oombedwawo anatengedwela kuchipatala cha Mtengo wa Nthenga komweso a Selemani analengezedwa kuti atsamira mkono.
Pakadali pano apolisi awiri omwe anaombedwa limodzi ndi malemuwa akulandira thandizo lamankhwala Ku Kamuzu Central Hospital mumzinda wa Lilongwe.
Apolisi amanga bambo Wyton omwe akuyembekezeka kukaonekera kubwalo lozengera milandu posachedwapa kukayankha mulandu wokupha kamba koyendetsa galimoto mosasamala.
Thupi la malemu Selemani likuyembekezeka kuikidwa mmanda lero Lachiwiri pa 18 Julaye kwawo, mmudzi mwa Kacheta, mfumu yaikulu Njombwa bola Kasungu.
Amalawi ndcan?musanapange post muzlngalra kawiri,anyway rest in peace amene wafawo.
THIRD CLASS JOURNALISTS!!!
THIRD CLASS JOURNALISTS!!!
Malawi 24 , this is just nonsense u can’t use the picture of a gun for car accidents
Very bad
Ndiye kuti Mgalimotoyo munali mifuti
Yrs
WAPOlice kuti amungunde amapanga chain nayese ndiwatulo ameneyo ; kupusa basis prembrem Malawi 24 does no gun that is prombren its better me a mus buy gu n and give everyone l got too much many hhhhhhhhhbh
TSONO MFUTIYO IKUGWRA NTCHITO YANJI PAMENEPA?TINENE KUTI NDI ZIZINDIKIRO ZA MKALEMBEDWE?KAPENA OLEMBAYO AKUDWALA NTHENDA YA KUIWALA?
Zithunzi mukuikazi nzamufilimu tayikani zakonkuno???
Imawomba mayesa ndi mfuti? Galimoto ilibe trigger
Imawomba mayesa ndi mfuti? Galimoto ilibe trigger
Pepan
RIP
Zimachitika guys
Azifa nchoncho ma road block ndi malo osafunika kuika amene amathamangila kopempa ndalama ziphupu RIp tikupeza komweko
KODI WOMWALIRA NDI NDAN DZINA LAKE?
NAKHALA ine driver uyu moyo analibe
Ndimawada a police athu kumawapha choncho posachedwa I will take saucide mission ndizingoomba ndi fraightliner they should learn to work mwa proffession
inu nde atinso inu u gabbage basi..pamenepa chanzelu nchani?
Hahahahahahaha kandabwati
apolice anyañya amafuna kumapanga źiphuphu kwa amaminibus asowa podyeŕa ndiye waluza ndani ?komanso pa dowa turn off malo pali road bloçk ndimalo añg’ono amaonjeza apolicewa mmmm hasi zachitika
Auzeni aphungu anyumba yamalamulo kuti akambilane kuti kusakhale police musasowe mutendere
Nanga mfuti mwaika apayi ikugwirizana chani ndi kugundidwa ndi galimotoyo
koma malawi analemera mpaka kunayamba kupezeka galimoto looneka ngati mfuti ngati yomwe ndaiona pachithuzipa
What is the gun portraying?
Muthuyu waombedwa kapena waombeledwa chifukwa tikaona kutsogolo kwa mfuti kuli unsi kunsonyeza kuti waombeledwa.muwauze athu zoona zenizeni
MHRIP (KOMA NKHANI NDI PIC SIZIKUGWILIZANA)
ause muntendele ndithu
Rest in peace
Rip our law enforcer
sometimes amabisala pa zimitengo akaona galimoto amathamangira mumseu kukaimitsa ndiye ndizimenezi
The one who passed away wasn’t shot. It was accident . Take out this Toy here
Com on malawi 24. You are so stupid ! How can you this stupid photo here?
pa 6 july a police anaphesa anunthu a mbili zinthu zizitero inu pepa khoza
Roadblock of that matter & the passenger died on the same spot.
Mfuti NDE ukutani APA .mesa mati galimoto
R.I.P
ofa lero safa mawa……linali tsiku lake limeneri RIP
Imfa yamtundu uliwonse ndiyowawa koma a police akakhala paroadblock azigwiritsa nzeru mitu yawo cifukwa amaiona galimoto ikubwera mwaspeed mwina driver analuza control koma iwo kusaganiza zothawa pamsewu mwina akanangotseka r.block driver akanagunda r.block.wapolisiyu wafa ndizinthu zoti akanazipewa.ok RIP Moyo usamalireni banja ndi ana pepani mulungu akutonthozeni sorry
Aziona Atapitiza Uima Pobisalika A Police Amewa
Eee ndie wakumoto amanyanya kugejetsa tikawapeza abakasonkha moto kumwamba
Koma ine I blame that roadblock ili Malo achabe kwambiri akanakhala ena aPolice bwezi ataisuthapo
Nkhani za bodza ,ngati nzoona bwanji mukanaikapo manja amunthu wakuda
Takana kutinamixa mtolankhani iwe
I aint cerebrating a mans death but sometimes a police amazafatsa kwambiri pa msewu as if njale kuwaomba sangapweteke or even kufa….
Ku Mw Malz Afka Posauzana Eeeee!!!
A police amanyanya amakhala ngati mseu nd wambuyao
Atitengela wabwino kusiya abalaba samativuta ife mkuluyi amatikonda…tiwasowa.
Mbuzi Zosaziwa Kufotokoza Nkhani
Kkkkkkk tsono futiyo kkkkkkk
Iiiiih Sorry Mzimu Wake Wuuse Mmtendere
What about the gun? Does it depict the nature or cause of the death? Poor reporting by our learned journalists.
Sorry guys. Anamuwidwa anali pa Chanco Reporteryi ndiye poti adya chani patawuni ananoyamba zimenezi koma kunena zowona wakulila ku Mzimba ndiye sakuziwa kanthu pepani ntawuni muno wangobwela. Mzake ndi baby yayimuna yamangidwa ija ndi ma best friends
R I P
Photo ndi nkhaniyi zikugwilizana eti.
Who was ur Lecturer at University, I want to talk to him. If a deceased was hit by the car, then what is a reason of putting hands holding a gun as if he was shot. And if u r reporting on Social Media, and what is a reason of talking about newspaper as if u r reporting on newspaper, is this a paper?
Bwanji osatumiza aja amangodya nyama yang’ombewa kumeneko mwalakwira ccter Liz Boma inu kumeneko ckumafunika a police
sorry
apolisi amanditenga mtima kobasi amakonda kuima malo obisala ati azilandila ndalama kwa anthu ndiye atengelepo phuzilo chifukwa mowawo ndiye tikuumwa ngati sasamala aphedwadi sanati
Risk allowance ija akudandaula a prison a police ndiyofunikaso.
kkkkkkkk a Malawi 24 sitiwamvesaso penapake amakamba nkhani zosemphana penapake
So sad RIP
Rip
Malawi24 mwafikapo pa utolankhani,,,
Chipikiseni chabwanji? U say Galimoto bt u a showing a gun hw do these things relate? Ine ;( ndingoti pepani ana padzuwa.koma uyo wina wacibale ndamuona akutsekelela mkazi wa malemuyo.hahahahahaha sole.
Zomvetsa chisoni kwambiri Atleast adziika MA signs osonyeza kuti Kuli road block 2km away
this is what we call schooless!!!
Rest in peace komanso ovulala akanangomwalira amusatile mzawoyoka
Even a traffic pa nsewo kungoti balabala akakuimika wina iwe kusowa pochita park galimoto
Sikuyankhula kwabwinotu kumeneko ifa siizoloweka
Koma pakavunda khola ndiye apolice bwelani.Kagalimoto ukunyadilako kakachita ngozi uzipita kwaamfumu.Born antpolice saluting munthu okupha munthu umuziwe yesu.
nanga mukuikapo mfuti ngati wachita kuombeledwa bwanji?….koma Malawi24 eishhhhhh simuzathekanso
Awa sadzathekanso ndithu
Ndipo
Zikuchita kumveka bwino kuti waombedwa ndi galimoto osati zoombeledwa ndi mfuti….tisamangopanga criticise zili zonse…. anyway REST IN PEACE mr Police man
Zovetsa chisoni zedi
Rest in peace komaso ovulalawo tikuwafunila kuchila mwachangu
nanga mfuti mwayikayo apolice akuno sanayambe ayigwilapo ndikuwona komwe malawi 24 banji
nanga mfutiyi ikutanipo pa pic
ndizimenenso ndikudabwazi ine apa
Boma Licitepo Kathu Rip.
walemba nkhaniyi ndi pumbwa kuombedwa ndikuombeledwa ndimawu awiri otsiyana. ngati waombedwa ndigalimoto paonesedwa bwanji mfuti? umbuliwu ndimatenda ndithu kkkkkkk
ndekuti nzabodzatu nanga waombedwa ndi galimoto inu muika nfuti ma joke’s anuwa ku makhala nawo seriously
Malawi24.com kkkkkk
Nkhaniyo ndiyowona munthu wawombedwa kugundidwa ndi galimoto inu mukaikaso futi. komaso apolice zomaima malo obisika kuona galimoto ndikumangothamangila mumsewo sibwino mumaika moyo wanu pachisye. ma driver ena mmaimidwe otele amayesa akuba. ntchito ndi ntchito komaso moyo kumaukonda.
Komadi apolice akuonjeza maimidwe ake mu mseu.
NDIYE AKUTHA KUGUNDIDWA MMENE NDIMAPADZIWILA INE DOWA KUFIKA PA MVELA MSEWOWAKE NDI WA MAKONA MAKONA. SIUNGAIME MUNTHU MOBISALILA KUTI UGWILE GALIMO AKUMANGILA MA BRAKE MIYENDO. NTCHITO KUMAIKONDA KOMASO MOYO SIUBWELA KAWILI.
Nde uthengawu mudziwauza malemuwo coz ndiomwe anali ndi mkhalidwe umenewo
eich! ndasimikiza kuti kuti maphulisa timadana nawo aMalawi why??????????
uthenga siukupita kwa wakufa ai koma kwa apolice amoyo ndiwena amene akuti avulalawo ngati amamva amve. ~~~~~~~~~~~~~~~~~~~~ iweso nawe sitidana ndi apolice koma magwilidwe antchito kuwaunikila galimoto ndichinthu chosafuna kusewela nacho. ndati ntchito kumaikonda moyoso kumaukonda moyo siubwela kawili.
Eti zikugwirizana ndichani kugundwidwa ndigalimoto koma mukuonesa mfutu.0 pa ten
Komanso ena onse atengelepo chitsanzo maka tima roadblock tosadxiwika bwinoti
Ma roadbrock ongoika masamba galimo akuyesa njinga?? anthu yawa chimapweteketsa sichina yafanta kaya thumbalawo lidzadzala liti? dzuwa lose mpaka kuweluka kupempha yafanta.
Er
amchita bwno
chipikisheni amapanga mu dress ya munthu wamayi
Yafanta imawapweteketsa sangaimike galimoto zose zili zokwana osapemphako yafanta, anangokhala mwa matendawawo.
No safer place on earth
MMM too bad
oh! sorry 4 that
Sad
Mfuti Aikayi Ikuimira Ntchito Za Manja Ake Mukufusa Cinyezi Ku Bafa Bwanji Anthu Inu
Ndiye mfutiyo????
Mmmmmm no comments cos am on free Data.
kkkkkkk koma
2 bad
malawi 24, you want to tell us that a gun is a car? can’t u see that u are misldading young ones on the part of learning through matching and association?
even you,you “misldading”young ones with your english kkkkkkk!
a mofolo nanunsotu apa “you english” sometimes it is typing error not necessarily the information or the fact.
2 bad
Nanunso olemba nkhani kakhalani s r s pa imfa yamunthu kodi wakufa amagwira mfuti ok RIP.
amalawi24 muziikachithuzi cholingana ndinkhani ndieapa zenizeni ndiziti mfuti kapena galimoto
Tsono mfutiyo ikutanipo koma 24
Okuba aphana,ntchito za manja ake zamuchitira umbuni
Very sad
Eishhhh zina ukaona kamba anga mwala fundo ranga nali a womberedwa or aombedwa which is which be??? Sinfikutha kumvetsa nkhaniyi
aombedwa(hit)
Nde mukaoona photo yo Pali mfuti ndikhaniyo zigwirinzana bwanji????
forget about de photo! kkkkkkk
paja apolice amakhala ndimfuti,,or akanangoikapo katoni ya u-flesh tikanaziwa kt ikuimira uniform yapolice,,kkkkkk may his saul rest in peace
Hiiii koma zinazi tingoti mzimu wawo ukause mwatendere
Tawerengan bwno mkulu.
Maybe the problem is with ur 4n kkk sory 4 sayng dat.
Tawerengan bwno mkulu.
Maybe the problem is with ur 4n kkk sory 4 sayng dat.
Ataombedwa kapena ataombeledwa? Nanga siwaonesa mfuti. Chinyanja chakuvuta
kuombedwa(hit), kuomberedwa(shot) ! i rest my case.
Thanks sukulu simatha?
I think mfutiyo yangoikidwa mwatsoka…hahahahaha M24
mawu a ‘mfuti’ ali pati???? tell me paragraph & line!
Onani pa chithunzicho pali mfuti
So khuzing
aunt musandiseketse nanuso News 24 khuzing hahaha apa ndiye chimodzi modzi kuombedwa ndi kuombeledwa kwa News 24 hahaha
Koma Carol
hahahaha ndaseka
Ataomberedwa ndi mfuti tikuona mfuti apa
RIP Kma mfutiyo isowe…
mmmm zachison.
vuto la amalawife tilibe chisoni timayiwala kuti anthuwa ndi ofunikila kwawo ali ndi ana,mkazi,makolo apongozi any way RIP
Inenso nde mkudabwa mfutiyi ,achita kumuthila chipolopolo????
Ine ndikuona kut ayika mfut ngat chidziwitso kut wapolice sinanga amanyamula mfuti
Inenso wonder
Mmm so sad
inaima mobisala wa galimoto anaona mochedwa apa pali apolice
RIP
So sad
afela pa tchito yawo
RIP
nde Mfuti ikugwilizana bwanji