Phungu wa nyumba ya malamulo wa dera la pakati mu boma la Mwanza, a Davis Katsonga, aletsedwa kupita ku nyumba ya malamulo kamba kovala ka chisoti ka chikhalidwe chawo.
A Katsonga amene ndi Phungu wa chipani cholamula cha Democratic Progressive (DPP) apitikitsidwa mu nyumba ya malamulo lachitatu ati kamba anaika nthini kumutu.
Wachiwiri kwa sipikala wa nyumba ya malamulo, a Clement Chiwaya anathamangitsa Bambo Katsonga ati chifukwa momwe anavalila sizogwilizana ndi ndondomeko ya nyumba ya malamulo.
“Dzulo tinakuletsani kuvala chonchi, lero mwabwelezanso. Nyamukani muzipita,” anatelo a Chiwaya.
Iwo alamula a Katsonga kuti asaoneke mu nyumba ya malamulo kwa masiku asanu ndi awiri kamba koti anavala ka chisoti kachingoni.
Dziko lilironse limadziwika ndi MAVALIDWE/MAYANKHULIDWE/CHIKHALIDWE chawoooooo
Ndichifukwa chake timalankhulanso ENGLISH kunyumba yamalamulo m’malo molankhula CHICHEWA chathu akuti kufuna kusangalatsa AZUNGU.Pa MOZAMBIQUE pompa amakambirana MUCHIPWITIKIZI chawo kuti aliyense ADZIMVAAA.Popanga CAMPAIGN mumatilankhula CHICHEWA koma mukapita kumeneko kumakambirana mu ENGLISH.2019 mukamadzapanganso CAMPAIGN muzapangenso mu ENGLISH muwone ngati MUNGADZAVOTELEDWENSOOOOOOOOOOOOOOOOO
Zachimalawi nde ziti kodi
Kupusa kumangodalira western things
That’s stupidity they were supposed to be in Gale!!!
Zachimalawi ai eti??
Siwonse Wochita bwino amene ali ozindikira even ife anthu wamba timangovala zithu zina Ku malo osayenera , koma ngati tsiku limenero mumakambira za cultural there is no any problem
WHICH IS WHICH?WE ARE TIRED OF WESTERN STLES OF DRESSING.
WHICH IS WHICH?WE ARE TIRED OF WESTERN STLES OF DRESSING.
Walakwa odevie koma mpaka suspension ulakwa sanabwere bwamuswe mnyumba yachifumu
Zinthuzina zimafunika dongosolo sizongodzuka basi lero ndivala pant yekha ku paliament ayi……..pamafunika kugwirizana kuti guyz mawa tikavale mapant okha ……
Simfulu ndekuti ku dziko la kwawo komwe?
Ndiye kuti aziloleza ku vala zachikhalidwe ndiye a chewa nawo avale zawozija za gule, olo sipika wanuyo angakhalemo mmmmm kaya
kkkkkkkkkk
You must try to have laptops . most of mps they don’t know to work with laptops
You must try to have laptops. Most mps they dont know even
Retrogressive! They need a learning visit to Nigerian Federal Assembly, be proud of ur culture. The best would have been to allocate days for cultural dressing
Umbuzi ndye vuto lathu A MALAWI vuto ndichani muthu kuvala zachikhalibwe chake ndye unduna wazachekhalidwe chathuwo ulibe phindutu nonsense fooling MALAWIANS
Nanga alomwe zpewa zaa ang’az zja zngakabebetu
Osamavala zachimalawi?
Ndiye azivala zakuti?
Hahaha enanunso tavalani zakwanu tiwone bravo Hon.Katsonga
Thats sound stupid, colonised
Kkkkkkkkk ask Julius malema
Koma Malawi Iiii
EFF salola zimenezo mpaka amavara ma ovolosi
Nonses azikzmbirana za development osati zachivalidwe just imagine is there any effect towards devlpmnt or akungofuna azingokangana ndizopanda pake mumalo molimbana ndi corruption ndi kutukula dziko
Mmmmmm
Wasowa zokamba,,, waiwala chisoti chake..
Kkkkkkk mumuletsa bwanji poti iyeyo ndI mmalawi? Samutsani parliament to America tizikavala zakumeneko
Mumafuna Azivala za ku saud Arabia?
Nanga kut aliyese adzvala cachikhalidwe cake zkakhala bwno alingalileni achewa kungakakhale zotani
kkkkkkkk achewa anvaresozawo
Nyau
Iwe dzmikannjotu mwna ena mwaganiza znaso mumetapo cabe
Man U was 6th last year (2016)
Man U are 6th this year (2017)
Man U were 6th 3 months ago
Man U were 6th 2 months ago
Man U were 6th 1 month ago
Man U are still 6th this month
Man U are still 6th this week
Man U are still 6th yesterday
Man U are still 6th today
Man U are still 6th right now
hahaha YNWA
Mwasowa Chochita Kunyumba Yamalamuoko
White man rule
Amapanga zomwe angathe ndey ndimocrass
Nde democrance ilikuti munavomela nokha azivala!!
M’kutheka n M’nsilam
Uchisilu kwa kumalawi mukatero mwapeze nkhani for sake
Kodi Ku Nyumba YaMalamulo Ayamba Kulankhula Chichewa! Ndamvera Malawi24
Malawi 24 stupit kagulu akakalindi dziazitolankhani dzitsilu Zokhazokha nkhani yakatsonga siilichonchi sananekuti osavala zachimalawi bt malamulo akuletsa phungu wachimna kuvala chinthu mmutu y mmafuna mzizondotsa anthu nditinkhani tanu taumve,,
Munthu wavala buluku la mzungu, jekete la mzungu, thayo ya mzungu, nsapato ya mzungu, lamba wa mzungu, mphete ya mzungu, mandala a mzungu, panti wa mzungu, kumayankhula chinenero cha mzungu, koma kungovala ka mthini kosonyeza chikhalidwe chake likhale tchimo?
kkkkkk frying pan yemweyo kkkkkk
Kkkkk koma guyz
Parliament salola kuvala chisoti kupatula Speaker yekha amavala chinthu ku mutu lamulo akulidziwa amapangila dala
Kkkkkkkkk koma ine nde mutu ukundipwetekatu kamba kofuna kulitanthauzila dzina lanulo abwana
Hamba = yenda
Yedwa= yekha
nquma
.decide, determined (among other meanings)
nqumayo
he that is determined/ has decided
Therefore, Hambayedwa Nqumayo in this context should mean he who has decided to walk alone.
that’s a ngoni name
man inuo ndi doro flying pan yomweo kkkkkkkk
m’m
owo auzeni kuti ifenso takana za kunja makamaka za amuna kapena akazi okhaokha kukwatirana…mmalo mokambirana chothetsa/kuchepetsa uphawi komanso mavuto amene akulepheretsa chitukulo osati chifukwa cha mavalidwe. sipresident anati buy malawian…. umbuli otheratu umeneu iyaaaa
A
Ine phwete lokhalokha, koma amangwetu kanundu eti
owo auzeni kuti ifenso takana za kunja makamaka za amuna kapena akazi okhaokha kukwatirana..
Kodi aphunguso amakagula kuti kanundu wamkulu kkkkkkk
cheap post.. its like household joke..
aah
hahaha kma aphungu aku Malawi… mmalo momakambirana za nzeru kumeneko you are busy nd zinthu za zii…
Kkkkkk
Kkkkk sozeeeee
We need to re-visit the ideas of one of the greatest and best African President , the Upright Man ” Thomas Sankara”. He believed in African way not Western way. Its higher time we start believing in our own culture including African dressing code in order to promote our own culture thereby uplifting our economy.
Bwana Katsonga mutisokonezela zinthu kumalawi kuno.Nankha Chakwela naye akazalowa mnyumbayo atabvala makanja wake ndiye kuti akulakwa ?
Malawi kuli mbunzi zokhazokha basi walakwa munthu kuvala mwachikhalidwe cha kwawo shame!