Bambo Kamlepo Kalua amene anamenyela ufulu wa zipani zambiri, ati asowa.
Bambo Kalua amene ndi Phungu mu dera la Kummawa mu boma la Rumphi ati sakudziwika kumene ali. Wanena izi ndi mwana wawo, Penjani.
Malingana ndi Penjani, amene amazitcha kuti Fredokiss pa nkhani zoyimba, Bambo ake asowa pa nthawi imene akufufuzidwa ndi a Polisi komanso bungwe la misonkho.
A Kalua akuganizilidwa kuti analowetsa galimoto mu dziko muno mozemba msonkho.
Koma anthu ena akuti boma la a Peter Mutharika likungofuna kuzunza a Kalua chifukwa akhala akulidzudzula mopanda mantha.
“Ife monga a ku banja zikutiopsa, Bambo wathu sachoka osalawila ngati umu zachitikilamu,” adatelo Penjani.
Iye anaonjezelapo kuti nthawi imene atate ake asowelayi ndi yopatsa nkhawa malinga ndi kuti anali akuthupsa boma.
Koma anthu ena aseka mwachikhakhali nkhani yoti a Kalua asowa.
“Walowa m’tchire ameneyo, paja anaopsezapo kutelo,” walemba mkulu wina pa Facebook.
Mmbuyomu a Kalua ankaopseza mtsogoleri wakale wa dziko lino, a Bakili Muluzi, kuti iwo azalowa m’tchire posakondwa ndi utsogoleri wa a Muluzi.
adzatipeza, chitedze chikadzawayabwa mtchiremo, adzabwerera kumudzi.
adzatipeza, chitedze chikadzawayabwa mtchiremo, adzabwerera kumudzi.
mumangova thengo eti nonse mukukamba zosagwira tima giys khondo siyamasewera mukakhuta nsima mumatakhula mwa uchisiru ndithu ndipo ngati amalephela kulipila sokho ndie ndalama ya zida akatenga kuti kkkkkkkk aaaaa mmmmmm amalawi kupusa tiyeni DRC, mozambic, naigeria,sudan, somalia. inu kuno ndie mulindikolowera inu osamangodya sima yanuo bwanji ndipo kamulep kamulepo basi uyo ali ku paliyamento mungonena za ziii
pitala nayeso asowe kuzunza mzika enidziko ndimagreencard anuwo kodi inu ndakumalawikuno? Zimatiwawa izi
Zayambika zikatelo
kamlepo ndiwabwino kusiyana ndi chaponda anaponda chimanga
Amangoti bweku bweku koma palibe chimene amapangaa tikufuna zinthu zowoneka ndimasooo.
Alowadi mntchire, ubwino wake anatsanzika ndiye no need to search for!…
KAMULEPO.TILIPO.MAKADETI.TITHANA.NAWO.M.C.P.BOMA.
No comment.
Palibe chomwe angachita ndi boma
Ngati kamlepo anamenyera ufulu wa zipani zambiri ku Malawi kuno,nde anthu ngati Chihana, Machipisa Munthali komanso ma Bishop a chi Katolika aja nde kut anamenyera chani mdziko muno nthawi imene ija ? Zonama pano ayi
It was simply a collective effort bro. If we have to single out only one person then it was Chihana who held his feet on the ground firmly than anyone else. Kamulepo was one of the most important and significant voices we often heard in those days. Don’t forget it wasn’t a physical fight so voices played a very important role
Fantastic, agree with you Esau voices yes played a major role in that time
Ayi sasowa amangomyata
Kodi amalawi mumakuziwa kumenyera ufulu kapena simuziwa?.mumusiye ife tikhala tikumudikilira kuti abwera ndichani m’tchire mwakemo.
ifwe shilefwaya fyaupuba awa akamulepo ali kuchitekete umo mu malawi wesu so imwe mulelanda landa va upuba basop tulemona
ndi miracle money imeneyo
Wamkulu samasowa
What is if it’s true was indeed invading the tax?
Kufuna kuioisa mbili ya DPP zofoila izi
Zonama izi zongofuna kuipisilia mbili izi
akunya ameneo kodimunthu ukapitakuchimbunzi sokawapezakomunthu kupita kumtchile ndikulakwa akunya akaseta abwelako GUYZ
Akamulepo amalankhula chilungamo , osati mbuzi inu.kodi mukufuna tizikhala ngati tili mu 1 party system?
A kamlepo adamenyera ufulu. Ndi chifukwa chani mukuwazunza ? A dpp mwafika pochititsa manyazi.
Ndie?
akamlepo akumwa MIDIRO alitchilekwan zabozabac abwelako
Osangoti likulakwa ai fuso mkumati magalimotowo aka mlepowo adalipira kape ai? Tisanadzudzule boma nanga lamulo ndi akamlepo wamkulu ndani?
Tax free as an MP, all documents available
dats depromatic… even if he can go to india he cn do what ever he wonts, worlds political rule dat was issued in 1859
Koma tisapenze tafa ndiye kuti iwe nala ulipamabvuto ngati njoka palibe chimene walakwa ndiue ukusowensa anthinmunjira imen e ikufuna
Ine lero ndamuona ku boarder ya muloza akudutsa msewu wachidule opita ku moshko chamma 5 pm
Ayende bwino,,,,atipeza
Kkkkkkkk zina ukamva
If he’s going to bush …..don’t wory he will come back …after finish what he want to do .there…….
Ndizosatheka, Asatinamize
DPP too much kupha uyo akwirira munapha Chasowa inu Mafunye
Ndizosatheka, Asatinamize
Ndizosatheka, Asatinamize
Amene Amupezeyo Ndimupatsa Ciona Maso
Ameneuja angangone kutchile wabisala kulodge
Hahahaha
I have no comment, Nonsence, Za Chaponda zili bwa?
TIMUSUNGA NDIGOGO WATHU UYU BWANJI SAKUZUZA ANABA NDALAMA ZATHU?
Wasokonekela munthu wamkulu ayende bwino
Çhwee mwana chweeee! Mumva naye ñtedza ameneyii
mmmmm
mkululuyu wachita misala anasuta heavy
Kusowa a Kamlepo akulukulu aja aaa mukunama alipo paja kuli ndege zausiku avaya kuholiday koma ngati alowa tchire adziwe kuti zingawatsatire ndi tchetche.
Kkkk sangasowe frxiday muzamuthaima ku parliament uyu
wangena mnthengo…
Akufuna kumupha ngat chasowa etii,1 day they will answer for what they r doing to Malawians these guys ,they think we r fools
kamlepo watopa ndichilungamo tiona kuti ife titani popeza tatani kale nkhondo kuti buuuuu!!!!””” ine kumva kukoma mwina tingamapasane ulemu ziko lopanda osutsa boma limakhala lopanda sogolo basi kaluwa yiyambe mwina angaziwe kuti siwe munthu okuseweretsa
Malawi iiii basi busy kumasowesa muthu kufuna kulemera kapena akukuziwani zifukwa.nkhondo mukuiyamba ana anjoka inu
Iwe penjani bambo ako pamene amachoka anamvala chiyani tifunefune mokuthandinza iwe Amai ndi banja Lao ndipo apolosi apite kunyumba akufunse sannayambane ndi akazi ao
Mkulu ameneyu simasewera, kafunseni a CONGRESS.
Panthawi yosowayo anavala zovala zotani?
Kkkkk
Careless and childish journalism
Bola akalowa mutchiremo pobwera abweremo ndi gwape
Mtchilemo bola abweleseko nyama mapoto tatsuka kale
ALIPO WANGOBITSALA HIYA
mwacoka pa maizegate nkufka pa persongate? ABAKHA
Munthu mumampatsa matama zedi.
Mmmmmm mukamva phooooo!!!!!!! Phooooo!!!!! Phooooo!!!!!kamlepo wafika akudzatenga galimoto yake …..muluzapo Zambiri apa bolani mukanangosiya
LUCIAs banda is next one KKKKKK politics Malawi
Apatu sananene kut waphedwa akut wasowa ndye mmalo mot muzimufunafuna komwe wa lowera mukungotayapo nthawi apa panja ankanenatu kut adzalowa mutchire tengani agalu mukamusake ku tchireko
Kkkkkkk ndakomoka
Bolanso manganya acting amayidziwa osati kamlepo
Kamlepo Kalua who some misguided individuals reported as missing in an attempt to gain public sympathy, following the raid that MRA had on his house and the summon which he got from Police Headquarters is indeed hidding from his wife for reasons better not to himself, and enjoying sex at one of his girl friends in Guliver,Area 49 in Lilongwe. [ 116 more words ]
http://malawiindependentblog.com/2017/05/03/kamlepo-kalua-not-in-hiddingmissingenjoying-sex-at-side-chicks-house-in-area-49
Olo atamwalira angadandaule Ndani mtumbukayi otha ntchito
Ronaldo scores hattrick in the semi-final against atletico while messi watching it on tv.. Just give the ballon d’or already to him
Go to hell with ur tonaldo, u don’t know soccer,
That’s what we Malawi, sugar K1200/kg ngati akuchoka Ku Japan, Kamleponso ndi uyo wasowayo eeeeee kaya!
Walowa ntchile akusaka bewa
Akusaka a bwampini muchile nkhuli yampweteka
Rumors are carried by Haters,spread by Fools accepted by Idiots
Wina akodzedwa ndithu
Njira ndi zambiri zomwe anthu amamenyera ufulu mu Dziko,komabe kulankhula kokha pa channel Africa kunabweretsa change ku Malawi,nthawi ija akadadziwa ndani za ulamuliro wa nkhanza ku Malawi kuno,kapena kulankhula osanyongedwa.
Man Osanamapo Apa, Anali Matha, Kumenyela Ufula Samenyela Kwaeni, Zaboza Man
Iwe wamantha ndani? Chinekee ndiye siamabwera nziko muno, Iweyo unali uli ku mudzi kweni kweni
Inu #Apeter, Galu Akamakuwa Atapindila Ntchila Dziwa Kt Ndi Wamatha Gat #kamlepo, Kukuwa Kwaeni, Wekha Ukut, C Africa Nanga Ndi C Mw
Misoya Atleast he played a role unlike these mafias. .remember media has power more than u can imagine.so kamlepo played his part
Kamlepo anayesesa kwambiri dat tym or kungolakhura pa media kunasitha zinthu kuno. Remember ana amutharikawa anathawiratu
Ndizomwe dpp imafuna zimenezo kumva kuti wina akuvutika Iwo kumtima kuti mbeee!!!! koma ndikuuzeni amene mumaitenga miyoyo yanzanu yosewelesa kuti tsiku lina muzaona polekela komanso chomwe mungadziwe ndichakuti ngati kuli munthu mmodzi amene anamenyera ufulu wa Dziko lino nde Mmodzi mwaiwo ndi Kamlepo kaluwayo Abakha enenu mudakali kumbuyo kwa Amai anu. nde tsiku lina zizakutembenukilani muzaona ngati tsoka
Dont Judge A Book By Hz Cover!!
Lmfaoo RIP English @ #Gracee_Mwalee . “Hz Cover?”. Next time better use this one the Standard one ” Do not underestimate the power of simplicity”. your synonym phrase is older than you, and was expired. Or kanjani Admin?
But at least you have understand what she meant by her sentence & keep it up not down #Gracee
Yes dont talk too much or put to conclunsion that he is dead but wait and see what outcome. Dont judge bcos u have no clear information about that. I agree with gracee mwalee. And dont laugh gramma bcos u are not whiteman u can also made mistake
Yes dont talk too much or put to conclunsion that he is dead but wait and see what outcome. Dont judge bcos u have no clear information about that. I agree with gracee mwalee. And dont laugh gramma bcos u are not whiteman u can also made mistake
BIG MAN WITH BIG BRAINS < THIS MAN REALY LOVES MALAWI
Malawi say something true,”Kamlepo anamenyela ufulu wake uti?.
Ufulu wa democracy kamlepo wamenya nawo pa wailes ya chanel africa,mwina ulimwana nthawi yimeneyo….
yah i cn agree with #joe. dis guy he z one of our heroooox thou its often dat most government do persecute him durin ther arena…
Kkkkk osamasewera ndi boma baba.
Koma M’Malawi muno nthawi zina zake sitidzathamangako…
kulupha zeje kulionera patali akukachalila 2019 kkkķk
kulupha zeje kulionera patali akukachalila 2019 kkkķk
Musiyeni alowe m’tchilemo akakomana ndi ankhandwe akalumidwa aonaso
Ndi munthu wamkulu ameneyi,akudziwa chomwe akuchita.
Tikupepesa kubanja la osowa.
ndinakumana nao pamene ndimalisha ngombe dzana akufula uchi!!!
Umaganiza ngat Nkhwali yeni yeni
asabwerenso or aferekonko
Akapezeka tivela kwa inu ine pheeeee zosandikhuza
CORRECTION :Kamlepo sanamenyere ufulu wa zipani zambiri. Amangolongolola pa Channel Africa. The Catholic bishops, Chihana, Bakili, and the majority of Malawians were here feeling the real heat NOT Kamlepo.
ndie kt nthawi imeneo iwro kulibe.waonesa kt sukuziwa kanthu.
anali ali ku sudan
A kati kumenyera ufulu ndie kumeneko kaya,,,kapena amalongolola zakunyumba kwakwe?
1994 Kamlepo adaima nawo pachisankho cha president. Kampeni yake amapangira pa Channel Africa?
Vuto lothawa xul ndilimenero bro.Kodi akadakhala kuti sadamenyere nawo ufulu akadakhala ndichipani?Ukalowenso mclass ukamve kuti atsogoleri alipowa ndi ati adamenyela ufulu wazipani.
Ngat siukuziwa kanthu it’s better to keep quite
Umafuna atenge zibonga NDE uziti anamenyera nawo ?? Inu mwabadwa my ulamuliro was Joyce banda NDE mukuwawata chan APA! Ukat amangolongolora ukutanthauza kut amayankhula zosamveka?kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk achina petala anuwa koma anathawira Ku america
kamlep wamenyera ufulu kuyambila chipani chimodzi pakana pano! alipo akubwela cheese! mwana chweeee!
Nthawi imeneyo timkati Tchweee Mwana tchweee. Peter Muthalika atathawa tisakuchiziwa
Kamlepo potiyimïlira panapita pãno amatipolamira#wakulu wathuwathu
Kusazisata nanu. Ukati amangolongola meaning what or amalongolora zakwawo??
Thank u for collection, I dont see any difference between him and steve liwewe banda, the only difference is that steve is one of long serving football commentor while him is a long serving political commentator, both commenting off the field. You cant say steve is a footballer pioneer.
amat musamathawe xul,,,si izi lero??
Atumbuka kuyesesa kubakila zot zosabakilika, chsanzo nd icho mwauzidwacho, sports pundit sikut iyeyo nd osewera ay, osewera mpira nd wina pundit nd winanso. Kamlepo was at that time a political pundit and offered nothing than that, coward ngat ameney akakhale omenyera ufulu? Mwna ufulu wa atumbuka okha kapena?
Chihana ndi amene anamenyera ufulu pamodzi ndi catholic bishops ndife a malawi eni ake. Ngakhale pamene timachita campaign ya referundum chitsiru chanucho kunalibe. Tinavutika tokha iye anabwera after referundum. Ngati simukudziwa lero mudziwe osamangonyoza ena ngati inuyo mukudziwa kanthu. Mmaso mwanu mwakudamo
Zsru zmenez zkumaztenga ngat iwo ndan kaya?
Amene mukut kamlepo anamenyera ufulunu mulbe ubongo olo pang’ono
A Madalitso Mpindamalata, inu ndiye mwayala mfundo!
Nkhani ili pano siyasukulu kapena age, kwa amene mukuti munapita kusukulunu. Nkhani ndiyoti Kalua sanamenyere ufulu wa multiparty. Ndibwerezenso, I repeat, two times, twice, for the second time, AMANGOLONGOLOLA!!! Komanso pano sitimadziwana amwene nchifukwa chake mumangonena kuti ndiana, othawa sukulu. Koma omwe mumawanena chonchowo mukuwadziwa kuti ndindani, amakhala kuti, and amatani for a living, munayamba mwawaonapo.
Grey Mpithi…. ayi ndithu!!!! kkkkkkkkkkkkk.. wati chani?
paja nonse alomwe nd ma cadets,,,nchito yopanda qualification
Peter kodi uli ndi nzaka zingati? ukuoneka ngati mwana.Akati kumenyera ufulu samatanthauza kumenya ndi makofi.
Footballer pioneer yemweyo
Ngati Kamlepo sanamenyere ufulu wa dziko lino ndiyekuti nayeso mbusa John Chilembwe sanamenyere ufulu wa Malawi!
Iwe nd bakha bwanj, kamlepo ukafanize nd chilembwe
Nkhani ili pano siyamitundu kapena misinkhu koma mfundo mu debate basi. Kutero mukupereka mfundo ngati mtundu wa kwa Kaluwa kapena m’Malawi? Sindimapereka mfundo ngati mlomwe kapena wachipani ayi koma ngati m’Malawi molingana ndimomwe nkhaniyo ilili. Pomwe inu mwachita kuonekeratu kuti mumatsatira “wakwathu syndrome” or zikhale zabodza.
Sitingafanizire Chilembwe ndi Kaluwa, KUTALITALI, inunso mukudziwa mukufunsa dala. Kambani mfundo ina, iyi tachotsa.
The difference between Kamlepo and Chilembwe is that Kamlepo played a vital role in fighting for the National Freedom while Rev.Chilembwe was fighting for freedom of his church congregation and pple around Chiladzuro district.
Akulu, this is what I call deliberate distortion of facts. Was Chinyama from Chiradzulo? Choona chenicheni mukuchidziwa kuti Chilembwe fought for the freedom of Malawi then Nyasaland. Go to the national archives and read. Koma Kaluwa sanamenyere ufulu wa democracy, period. But If you just want to glorify your lie, go ahead. Koma kwa ine and many well meaning Malawians respect the Catholic bishops, Chihana, and few others not this coward! Komanso you are totally off track. The issue here is kumenyera ufulu wa zipani zambiri not kumenyera ufulu from the colonialists.
Mwaiwala kulongololako ndie kumenyako chifukwa ena amamva
Chikulu mwavomereza kuti amangolola.
Amangolongolola.
Ndi wamkulu akudziwa chomwe akuchita.
Alipo ameneo amfuse kamudzu…
Kodi muzapuma liti zandale bwana ?
Tikumva kwa inu zoti asowa a dpp akuziwa komwe ali
musamusowetsetu munthuyu!!
Pitani ku kupolice ndiye mutiuza ife ndiye titani anzanu wachibale akasowa amapita ku police. komanso fufuzani kwa achibale anu ku Tanzania kwawo
Olo atapanda kupezeka palibe akusamala
paja kno mkumalawi chlichonse ndi ndale.tiyeni tizngoyang’ana mmene zithere.
Palibe wa ndale amene adamenyera ulamuliro wa zipani zambiri koposa kungolowererapo pa ntchito yolemetsa imene ma Bishopu a Katolika akugwira polimbana ndi Dr Banda.
Zalowa ndale za Dpp izi
Akukapanga training pochoka uko samala naye
Team #fredokis……..sangasowe ndpo munene bwno bwno zopusa et
Kamlepo ndi munthu woti anachita za inteligence ndipo akudziwa kut the moment azatengedwe kukagona ku police-he is gone!! Mark my words
Thank you prophet Mboro, I won’t buy your prophecy
Mmmmmm ndimunthu wankulutu ameneyo aziwa zimene achita muziwe kuti pochoka mtchilemo ndi nkhondo basi.
Ali ndikhobili loyambisila nkhondo
Wapita Kochekera visamba uyu kkkkk
Akadatiuza tikadalowa nawo mtchiremo kaya. M’dziko muno ma cadet akutumbwa maningi
Kkkkkkkkkkk akatulukira akudzalanda boma walowa mtchire akukathamangathamanga
Alipo ndpo ali bwino bwino
Amenewo nd wakulu akamabwela kumeneko nd mbola.
kkkk walowa mtchire? ndie kuti akatulukila mu nseu,mwamupinga too much!!
Kkkkkkk kunyasaland koma guyz
Mwina wamusowesa ndi mkulu wachimanga uja
Team Fredokiss….. kamlepo sangasowe
Kupha Kamlepo ndikuziputila nkhondo cz w won’t rest instead will bring unrest situation mudzikomo…………..AGALATIYA OTCHONA KU USA UFULU UJA MWATILANDANSO???????
galatiya ameneyu wandikwana ine
Kkkkkk asavumbuluke tikumana komweko
Kkkkkkk
Boma laji ili chuma chikuakanika bas kugolimbana ndi anthu
Mufunilanji munthu wamoyo pakati pa anthu akufa kkkkkkk
akukatenga zida mumva manyi adpp
ok
Mwayamba kulimbana ndi anthu chitukuko cha kukanikani kkkkkkkkkkkk
Mutchire muja ?mwamuziwa kaletu tangomubwezani basi!
akapha gwapeyo andigaileko kamlepo ndithu. nanga mchire walowa yekha opanda amzake kodi ikavumbuluka nyama agwira yekha
Anaopsyezako boma my nthawi ya ulamuliro wa a Bakili!
Nanga ino ndi nthawi ya Bakili ??
Xitikudabwa Ku kusautsidwa kwa a Kamlepo ,
Ndizomwe a DPP amaziwika nazo kuzunza aliyese wowapatsa befu.
Wapita kokhadzikhapila Ku Mozambique Kaye kkk
akanakhala ndi zida ndikanawasata koma mmalo mwake or sapato sanavale azangobaidwako ndi minga
Asowe tiribe nazo nthito zimenezo.
malawi 24….is a dpp machinery….you have sold your trust to the dogs……
Ali ku camp ameneyo ndekut wayambitsa gulu la zigawenga kut alande boma…a Peter amukakata nde mmmm achitepo kathu wina ataya mwazi akangotulukira..kkk
Kungofuna kutchuka basi,aMalawi akhalire zimenezi
wamkulu amasowa?
HEEE HEEE HEEE…akukasaka mbewa
Kkkkkkkkkk amusake
nanzi imamuzula heavy ask a Chair admin
Akamabwera uko mayiiineeee nkhondo amawoooo, DPP samala
Peter amangidwe wapengetsa mwana mpaka kucholela den mkumulanda njale aaaaa mwalakwa!!!!
A Kamlepo kukhala ngati alowa m’tchire muja: sakudziwika komwe ali ayi mukuziwapo kamthu mwaziwabwanji kuti alowa mchile malawi 24 mukamba momvekatu inu
Mutchiremo apita kokatchera mbalame??!
abwelekotu ngati asabwele Dpp isova
Kape iwe
Ukuona ngati kuti afe ameneyo dziko lingakodwe? Uzilankhula bwino mbuzi iwe
Kodi Obook , ndiwe m’Malawi dzinaro sizikugwilizana ndikukhala mmalawi
zosakhala bwino kweni kweni
Atipeza
kkkkk koma a news inuyo kkkk mandiseketsa zedi.
Mtchire muja ? As if mumadziwa kale kuti adzalowamo ? Mmmm
mmesa yekha ankanena kodi? mwaiwala tym yomweyi kodi kapena kunalibeko?
Kkkkk mwina tinali tili ana enafe amwene
kkkkk mdala ndiwa drama uyu
Kkkkkkk mtchire muja???????ayayaya ndaseka ndithu
Kkkkkk koma admn uyu
DPP samalan alikokasaka zda
Zosakhala bwino