A 16 year-old boy was on Wednesday found hanging from a mango tree in Thyolo district.
The boy has been identified as Chitani Mtambalika.
Police said the teenager’s mother left him in their house with his two young brothers on Tuesday and went to a nearby church.
But when the woman came back from the church service she only found the two young brothers in the house.
Chitani did not come back home that day and on Wednesday the woman began looking for her son.
“He was found dead while hanging in a nearby mango tree,” Police said.
Meanwhile investigations are underway to establish what happened to the boy.
The deceased hailed from Chafa village, Traditional Authority Changata village in Thyolo district.
TAnfuseni Kuti Pano Aliku?Sakuothela Moto Galu Ameney?
mmmm koma a Malawi24 dzoona umeneu ndi mutengo wa mango zedi
Muku nyanyila inu anthu olela ana kuzuza mwana wang’ono ngati ameneyu nkumamuti ungokwatila mmmmmmm Shem kummana chakudya kunthamangisa chifukwa siwanu ongolela kumpasa zintchito zoti sizasayezi take aaaaaaaa ayi ndingoti Rip
16 yrs
koma ine sindikuonapo munthu apo ngati muli serious nchifukwa chan mukupanga edit a photo??? maliro mpana edit,,,,RIP
Very sad
Sad
Chisankho chake potinso anabwera yekha ku dziko kuno.
RIP
Malawi imeneyo dziko lamavuto kma eeee tikutha zoona
koma ngati ndimuthu wachita zimenezi ameneyo kumoto bas ngati anamulakwila mwanayo bola anakangomulipitsa mlandu umatha ukukamba osata kupha ngat mwachitilamu uku mkulakwa ndati ngati ndimuthu wachita zimenezi ukapsa ndi mano omwe
Kape….
Ndizomvesa chisoni kwambiri
Zomvetsa chison
RIP TIKAMUPEZA KONKO KWATHU SIPAZIKO
ndikumva chisoni ndimwanayu ndim’bale dzina lake ndi Titani Matambalika Ochokera Mmudzi Wa Chafa T/a Changata Thyolo Moto Pano Ndalandila Uthenga Guys Ndikuona Ngati Kutulo Zoti Mwanayu Watisiya Pazifukwa Zanzii Ndipo Ndakhulupira Ndi Amalawi24wa Ndimawona Ngati Bodza
Komano Berna ukafufuza utiuzeko kut chapangitsa kut mwana wang’ono ngat ameneyu kut azimangilire nchani…utiuzeko pliz…
Ndie nkhondo yakumalawi imeneyo sitidzaona nkhondo ya mfuti koma kudzimangirira, ufiti, kudulana ziwalo ndi zina zotero.
DPP siikuziwapo kanthu pa imfa imeneyi?? Pajatu chilichonse mukumangoti DPP.
Nyapala wachabechabe iwe !!!
Mkandawire, do u knw the meaning of the term ‘nyapala’??? I have million plus reasons to overstand and forgive you. Zikomo
Mmmmmm
Utakhala ndi mafuso pankhawa komaso chisoni chomwe chakugwela mum’tima kt sudapeze yankho loyenelera zotsatira zake zimakhala zimenezi
Mmmmm nzobwitsa idzi kudzimangilira sichinthu chapafupi
My name is Musonda Kaluwe and this a testimony of how i became HIV NEGATIVE, i have been suffering from HIV for the past six years, i have spend a lot of money finding cure for HIV/AIDS until i found this true man who cured me completely with his powerful herbal medicine, i have tried different means to get this virus out of my body, all the possible ways i tried did not work out for me, i came across doctor olumo through some amazing testimonies concerning how Dr Olumo has cured different people from various kind of sickness like HERPES,HIV/AIDS, CANCER, with the help of his powerful Herbal Medicine, so i was encourage and i contacted Dr Olumo i told him about my Sickness, He told me not to worry that he was going to prepare some Herbal Medicine for me, after some time in communication with Dr Olumo he finally prepared for me the herbal medicine which he sent to me through courier service and he also gave me prescriptions on how to use it, after taking the Herbal medicine for some days, i went for test to confirm and the result was totally negative ,i went for test again in a different hospital still the same negative , Today i am fit and healthy to live life again, I am so happy for the good work of Dr Olumo in my life, if you are having a simillar problem kindly email HIM on { [email protected]} OR CONTACT HIM WITH HIS NUMBER OR CHAT WITH HIM ON (WHATSAPP) (+2348138956767) together we can live an HIV free life.
Why only Nigerians cure HIV/AIDS? mmmmm there’s something behind this!
Hahahahaha who knows
wachita bwino kulithawa boma la Dpp lophanali, RIP.
koma abale
May De Soul R.I.P Indeed.
sataniki pamalawi ali pa no 1.
Good day good people of malawi: Please, if you are a native siswati speaker and able to do translation job, that is, English to siswati…..Then contact me….The job pays very well…..Send me a private message here or simply add me as a friend, then I will contact you. If you are on skype, then mine is sonnyhoney1
Anatupidwa mbewa ndi ziwala ameneyo
Maludzi anapanga nawo ubale kwa nthawi yayitali nde adangoganiza zowatha che maludziwo
Kutelokotu wapha munthu ameneyo akayankha mlandu wakupha
zamukonda zitete!
Mavuto ake ati mpaka kamwana ngati kameneka kumazinyonga.xieew.RIP Anyway…
Vuto ana aku Malawi amafuna kulemera asanakule
Mwanayu waganiza bwno, amalakalaka ife yake itafanana ndi yudas scarliot ndi zachtika. pita bwno ukapume ngakhale wathawa kulima. ukhaula kumwambaso masku ano akumalima.
Kikikikkk
Alomwe kupusa…..
Dzikol lalowa zwanda, chfkwa macku ano khan ngat iz zukuchulukir
Maybe he saw something maybe its a setup a boy on that age can not commit suicide wat do u think guys ?
wina akuthatha Ku Qeeiz uko!!!! kufuna moyo wina ndkumatere?????……………RIP
RIP
Ati Adapeleka Mimba, Ndiye Amaopa Makolo Ake
Pita bwino mwana wakwathu ukapume watopa ndi ziko lapansi.
Eeeeeeeee koma inu ufiti ulipodi mwana mpaka kukazimangirira.Ayi kalipo kalipo zachisoni ndithu
kudzipha siyankho
Mavuto awa mpaka ana hanging zoona kukhalad m'malawi nkulimba mtima
Ohooo!! pepa
Bad_news.com
Mwina akuganiza ngat azabadwanso m’moyo uno!
Kukhuta ndi Life .
Mlekeni akuona ngat ndikomwe kuli mtendere!
Adzayankha Mlandu!
Sorry
hmmmm! zinthu zafikapenapache kumalawi, ndi ana omwe kuzipha okha,, Asaaa!! tsogolani tikaonana kuchiweluzo.
Mavuto mwana kutopa nawo uku nanga atani cimwinaso adalibe makolo ameneyu
Mwina anatopa ndikumva nkhani za cashgate
Koma anthu aku seweletsa moyo bwanji
Very sad indeed why so early so young? MHSRIP.