A 16 year-old boy was on Wednesday found hanging from a mango tree in Thyolo district.
The boy has been identified as Chitani Mtambalika.
Police said the teenager’s mother left him in their house with his two young brothers on Tuesday and went to a nearby church.
But when the woman came back from the church service she only found the two young brothers in the house.
Chitani did not come back home that day and on Wednesday the woman began looking for her son.
“He was found dead while hanging in a nearby mango tree,” Police said.
Meanwhile investigations are underway to establish what happened to the boy.
The deceased hailed from Chafa village, Traditional Authority Changata village in Thyolo district.
63 thoughts on “Teenager found hanging from tree”
Comments are closed.





TAnfuseni Kuti Pano Aliku?Sakuothela Moto Galu Ameney?
mmmm koma a Malawi24 dzoona umeneu ndi mutengo wa mango zedi
Muku nyanyila inu anthu olela ana kuzuza mwana wang’ono ngati ameneyu nkumamuti ungokwatila mmmmmmm Shem kummana chakudya kunthamangisa chifukwa siwanu ongolela kumpasa zintchito zoti sizasayezi take aaaaaaaa ayi ndingoti Rip
16 yrs
koma ine sindikuonapo munthu apo ngati muli serious nchifukwa chan mukupanga edit a photo??? maliro mpana edit,,,,RIP
Very sad
Sad
Chisankho chake potinso anabwera yekha ku dziko kuno.
RIP
Malawi imeneyo dziko lamavuto kma eeee tikutha zoona
koma ngati ndimuthu wachita zimenezi ameneyo kumoto bas ngati anamulakwila mwanayo bola anakangomulipitsa mlandu umatha ukukamba osata kupha ngat mwachitilamu uku mkulakwa ndati ngati ndimuthu wachita zimenezi ukapsa ndi mano omwe
Kape….
Ndizomvesa chisoni kwambiri
Zomvetsa chison
RIP TIKAMUPEZA KONKO KWATHU SIPAZIKO
ndikumva chisoni ndimwanayu ndim’bale dzina lake ndi Titani Matambalika Ochokera Mmudzi Wa Chafa T/a Changata Thyolo Moto Pano Ndalandila Uthenga Guys Ndikuona Ngati Kutulo Zoti Mwanayu Watisiya Pazifukwa Zanzii Ndipo Ndakhulupira Ndi Amalawi24wa Ndimawona Ngati Bodza
Komano Berna ukafufuza utiuzeko kut chapangitsa kut mwana wang’ono ngat ameneyu kut azimangilire nchani…utiuzeko pliz…