Soldiers in Blantyre have severely beaten a civilian whom they accused of pummeling one of the soldiers.
According to reports, the civilian who resides in Chilobwe beat up the military officer at a drinking joint on Saturday.
The disfigured soldier then went to Chichiri camp where he somehow convinced his fellow soldiers that beating the Chilobwe resident was a good idea.
Just as they would when going for battle, the military officers on Sunday boarded their dreaded Tata Truck and went looking for the soldier beater.
They found the person and took him to Chichiri camp where they heavily beat him.
When they decided that it was enough, the soldiers took the man to Chilobwe Police and told the cops that he was a suspect who was caught beating a soldier.
But the law enforcers refused to keep the civilian fearing that he may die at the police station.
As we published the story, the soldiers had taken the man to Limbe Police.
Gwirani ntchito yanu
Being a civilian siumunthu palimumafuna ma civilian ena amaganiza pamene enanu ndinu mbalame za anthu ndithu mungonena osaganiza mumafuna muzitilowa mchala ndipo ukulankhula zoduka mutuwe uleketu once kuzakupeza uzasimba zoona anthu tikuvutika ku dziko laweni kuno chifukwa chainu muzikanyanso mwana anthu osayamika inu muzatifuna chikazatuluka ballow ku malawi
Pita ku darfur kape soja wachani ungoba basi
Boko halam yaku Malawi yakwiya kikkkkkkkkkkkk
Aonetseni kuti ununso munali Ku xool zopusa zimene mwayambazo vuto nchani ngati achepa malipilo zisakhuze anthu odya mbewa ndima grasshopper galu MDF menyani njala osati anthu osadya
Kkkkkkkkkkk koma ndaseka amweneee!!!! Wina ati “Koma kuzolowela ma HAMALA ku mowa”
Kodi anakakhala kuti Munthu yemwe anamenya soldier yo wamenya m’bale wanu inu mukanatilanda?Inu mukunena ma soldier inu kodi anayamba a kumenyaniko musanawayambe? Sometimes wen u tlk muziganiza mwamva.lets respect dis pple they are doing a gud job.Ndipo ma Soldier osasiya kukhaulitsa onse opanda mwano ndi owononga mitengo. We love u vry much
Agalu osaka awa,,,,,mbalame za anthu,,,,
I will comment very soon,ndikubwera kaye
Ma soldier ambiri masachet heavy.
Zoopusa Basi ! Kod Tiziopa Gululo; Ngat Muli Madolo Bwanj Osatisakila Amene Akupha Azibale Athu Achi Albino, Ndye Mudzilimbana Mkumenya Anthu Mesa Munalumbila Kut Mudzidzatilondera Ndye Mwayamba Chani
OK,where is professionalism?
Bola Malawi Young Pioneers olo Malawi Youth League
Ngati kuli mbuzi za ma Soldier ndiye ku Malawi zimangolimbana mkumenya ma civilian
police & soldier r different so u deserve to differentiate
These Soldiers desire to be removed from their position. How can they take law in their own hands, no one is above the law .The very same citizen they are beating are the ones who pay tax for them to get paid.Being a soldier does not mean you are superior that anyone. They are damaging the name of the country and the reputation of other soldiers who are there to serve the nation.
Shame on them they must be prisoner at Maula prison and use their energy to do hard labour .
Ministry of justice should take charge of this, we cannot leave in fear of the people who are employed to protects us.
Achita bwino anyani ena mmanyoza asilikali…mukadangopheratu
Bombocrat soldier police in Malawi is dem weak character pon innocent civilians, SHAME!
Big up MDF!! Fanz yambili kumalawi kuno imakhala ndinthawi yambili yotokota mbwelera chufukwa chakusamenyedwa kkkkkkkkkkkkkk
Kkkkkk uphawi ndie wakula apa nanga soldger kumagona osadya malipilo kuchepa mapeto ake kumangomenya anthu
Amenyeni bac, kaya kushutanso mutha kutelo bac achita kukushoshani guyz!!
ow owww
ow owww
U Military ppl de problem u go around the city’s like u deployed mufwenge uheni
Ur busy camparing mdf with USA soldiers,dont u know that war is too expensive? You cant win it without enough resources. Our MDF is full of world class soldiers if u dont know. Our soldiers are the best in the world. But what matters is resources.. Don’t 4get that it is only fire that can stop fire
Asilikali akusowa ntchito nkwabwino tiwatumize komwe kuli nkhondo akakumane ndi anzawo
the problem of most of our soldiers they never been at war since they came from trainning! they are trying to show their powers on civilians? I thought soldiers and police are protecters to civilian citizens? zinatha kale zoti nsilikali mmodzi akapanga misbehave namenyedwa pamatchansi kuchilinde kamba komwa mowa wa eni, inu nkumakabwela ndi ma tata 47 odzadza nkumazalimbana ndimudzi onse?
Zitsilu izi amphawi kukhuta nyemba basi ndeu sathaso amadalira chigulu
Ife tikudziwa kuti ku America nkomwe kuli asilikali eni eni. Ku Malawi muli ndi ma jets angati? nanga Special forces, nanga battle ships? muli ndi ma satelite nanga nuclear weapons? munayamba mwamva kuti aku American abwera kuti mudzawaphunzitse kuchita detonate mabomba? Guns,bombs,tanks,vehicles,uniform made in USA, even support and command from azungu through UN. Mozambique kuchita detain boat, kuotcha ma truck a Malawi. TZ kuopseza pa Lake Malawi. Inu mukutibula ma civilians
Amaiwala kuti ndi alonda athu amenewa
Asilikali amalawi chidziwa iwo ndi kumenya anthu wamba osati kumenya nkhondo ata
Kma kumeneko
AMAYESA MPADA ETI KKKK@MAYO MAYO AKUSAVERATU KKKKK
Take it easy MDF
Good,,,,, awonetseni basi
Uhamala nkat
soldier akakhala savage akafika pamowa amafuna aliyense amudziwe koma aliponso ena ozindikila chikhalidwe akafika pamowa sungabziwe kuti ndi soldier,komanso omwe amatengana kukabwezela nzawo akamenyedwa kumowa amakhala opelewela m’maganizo.
Koma ndi nyatwa guys
some guyz u r talkng bulsht bt u hv no ldea wt u r talkng abtr
eyetu diso kwa diso inu c muziwa kuti soldiers amayenda ngati akakowa amathibula kumene
Asikali adziko lino kwambili chimene chimawavuta ndi umbuli, mutha kundikhulupilira amene geri yamukanika amathamangira ku usilikali, Munthu amene amumenyayo amamenyana ndi nzake ku mowa yemwe nzakeyo m’bale wake ndi msilikali, ndiye anakamema anzake nkuzamumenya kumutenga atasamba magazi, nkhani zoti nzakumowa, kodi anthu amene ali ndi abale awo ku usilikari wa aziputa dala anzawo pomadalira kuti ma TATA abwera? UMUNTHU ndiomwe ukusowa usilikari sichoopsyezera anthu ayi
if you don’t know you better shut your mouth mdf has the only nco academy in Africa and they are training Zambias on airborne why is it Malawians you don’t appreciate what your men in uniform are doing go to Congo you will see how good your army is those with everything they fail to fight
Mikango ndiye imeneyoyo team hard working ma civilian asamabweze moto kuwaonetsa basi
Thats why they recive 1500 rand salary
Tiasilikali tosadya’s bwino
Very weak army .when one is beaten by civilian. They run and call everyone with gun to revenge,if ur strong stand our own .
Soldiers are there to protect citizens not to marshal against them, I know also of some pple who stop at nothing to provoke the Army or police ,exercise caution, love peace.
eeeee mmmmm
Kkkk so funny , kaje timifuti take lol, sitophera nyama Ku game iti?
Zilipobe
Zamveka enanu ndi nsanje
Ine ndingot masodier panyapanu
sometimes I feel like loosing tym by commenting such army issues, coz I understand them that many of them behaving bad are not educated, and sangathenso kuwerenga commen yangayi
that’s really barbaric for our soldiers, I thought these soldiers are there for securing malawians, this is very uunfair
Tazilankhulani…tikuwerenga nawo…Onyoza tinyoxeni,Olangiza tilangizeni,Opeputsa tipeputseni,Onyadira tinyadireni…In da Army we believe in Discipline,Team work n ……………………………! Kma zikaonjexa nde iiiiih athemule munthu.Chala pansi,rolling,shower ndi zina zotero zidzamfikira…
Ndinkona mumamenyadi anthu chifukwa mwaiwalapo chimodzi. Yesu. Mmesa mumakafola pamnzere nkumapemphera inu. Ndiye mumapemphera zichani
Its a criminal case if he loses his life, you are trained on how to handle civilians who happens to breach the law without causing death and heavy injuries, you are part and parcel of law enforcement agencies such that you know many ways of correcting a civilian with such kind of behavior, unlike the way you have done. Learn to put a demarcation between personal issues and official or business issues that needs to call support from your fellow armed forces men.
KODI MA CIVILIAN NDI ASITIKILI MUJA AMAMENYANA PA CIVO MUJA MWATI ANAWINA NDI NDANI????? AMENE ANAWINAYO NDI AMENE AMATHA NKHONDO.
Veto mumaojeza zinazi mumaziyamba dala tizikuputhani kumene
Both Soldiers and Civilians are Powerless. GOD ndiye shasha, wamphavu. No man is an island. Kunali Gadaf, Shamola ndi wina wa ku Irran ali kuti lero? Tamazitamandileni ndi kupha makwacha kuti ife tisilire ndi kufunsa nzeru kuti nafe tiphenso makwacha osati zomenyana, zophana ayi. Mtendere ndi ofunika kuposa kusowesana mtendere
Sichifukwa China kumalawi kulibe nkhondo.Amaona ngati poyeserera nkhondo.Shame be on you soldiers. Leave us alone we r not of your size
Amalawi kkkkkkkkkkk ndiye akubwelanso2 lerolo mu Chilobwemo tione ngati muzizatulutsa mau.Mukazaziwa kuti Malawian Soldiers r th best soldiers world wide muzachileka ngati Tanzania inapeleka ulemu ask pipo frm DRC,RWANDA or Ivory coast osamashosha mavu 1day ma degree anuwo muzawasiya mnyumba nkumathawa chitalila zenizeni b serious popanga zinthu
maiko watchulawo anatchuka ndikugwirira a zimayi Google Malawi defence force in RWANDA uwone ngati pa bwere luso kapena uhule
Koma man ndinu osekesa….tafufuzani kachiwili
Kugwililako ndiye usilikaliwo mai ikazabadwa nkhondo pa Malawi pano inunso muzachidwa mosafuna mukukamba izi poti simunamve kuti GPMG ikalila zimatani mai keep on talking
@DAN kufufuzaso chani man
Km Ndie Mukunyoza Anthu Ofunikatu
@PENCIA sakuziwa mabulutuwa tht army ndi shop ya boma dzikoli likuyendetsedwa ndi dola zaku peace keep frm U.N koma poti umbuli ndi matenda thts why they can tok and shout.Ku Army xul ndiyachani popeza usilikali ndi Heart,blood and fitness inu muli ma pepala andi koma ndi ndege yomwe simunakwele koma a Malawi
Iweso Jonathan ndiwe omvetsa chisoni kkkkkkk kuzolowera kudya ndi kuvala zolandira basi mbuzi zachabe matama thooo amphawi mxiiiiiw
Iweso Jonathan ndiwe omvetsa chisoni kkkkkkk kuzolowera kudya ndi kuvala zolandira basi mbuzi zachabe matama thooo amphawi mxiiiiiw
Tapitaso Uko Nawe Mwana Wahule Undinyasa Jesca
Tapitaso Uko Nawe Mwana Wahule Undinyasa Jesca
Agalu ojiba pa thalaveni amangobwera ndi ya umodzi,,,,,bulangete lolandira,,, bed yolandira nsapato yolandira polish olandira,,,,kapu jagala yolandira nkumamulipiranso kma kulephera kugula zibag ziwiri mbalame za anthu,,,
Bst soldier kumenenya anthu wamba umbuli.
Ndiyawuza a silikali a renalmo mozambiq kut athane nanu 1 sordier amapha almost 3 full tatas nde akabwela tata nde kut ndi nonse samalani .
Guys munthuyo nde amuvulaza zachitika mu ghetto mwanthu #chilobwe sizinali boo
When a mosquito lands on ur testicles, thats when you know that violence is not the best way to end conflicts
Asilikali akumalawi tukuwadziwa ndi ankhanza kwa ma citizens…amadzinva u silikali hvy
..kulakwa kumeneku..tizkondana
There is book haramu in Nigeria why don’t they go there to stabilize the situation, lack of education, considering that most of these guys are Jc holders am not surprised
i never see hw stupid malawian soldiers are takamenyan tanzania ainso eish
anva ndipo mabwana awo amanva chicewachi.dzikuchikadi wina kuvala unifon ku ganyu yokakwenya ngongole.malamu mulibe ganyuyu koma nkhaza wina yose kuvalira kuchibuku.kodi mabwana anthu oterewa tinganenere kuti ? mbiri yanu isaore ndi mmodzi.
Un civilized army in short
Bullets 4-3 Moyale
Kikiki mpaka ambush kupangila afana oderera bwanji pitani ku tz eish koma
Panyapanu asilikali….mumalephera kutetezanyanja..kma kt pexela Ife anyani
Ooo Malawian sojaz they are fighting wrong battle.kungoti kumalawi kulibe nkhondo nde best option is to beat civilianz awh!!!!
masoja amamenya osawaputa dala guys !!!
Hw cn u compare Malawi Army n South African Army?? U dnt kno kut ku SA Army they hv all resources 4 their sojaz?? All sojaz r accomodeted within nyc barracks??? Well paid? Kwanu kuno ndinu amphawi u cnt manage welfair ya asilikali d@s y u see them in rents, dairly bzneses in local twnz u associate wit them in dairly lyf… Its true ku SA sungaone nsilikali wamba AND u fail 2 identify the reason basi nkumati kuno sitiona asilikali kkkk inu mutaniko uko?? Uchitsilu!!
God bless malawi
Malawian soldiers stop this barbaric actions on civilians some african countries needs your help fight against rebels there
So pathetic ntchito zoyamba schl ikavuta plz dont behave like cowards#usavage
Ngati kuli chitsiru cha usilikali mdiye ndi kumalawi,chimadziwa iwo ndikumenya anthu awo umene uli uchitsiru plus usaveji,
INSTEAD OF SEARCHING FOR THOSE ALBINO KILLERS YOU ARE BUSY SHOWING YOUR TALENTS ON A CIVILIAN ! ? SHAME ON YOU!
This is normal for these soldiers .. Yet there job is to protect civilians .. Too bad nothing is ever done to such people
Kkkkkk akati akulemba ma soja apa kumazaza ngat kuli mpila wa bullets ndi moyale koma apa kutukwana…. Mmati angomuyang’ana??? D@s soldiering usilikali ndi team wrk and nsilikali si John Rambo nsilikali sakhala modzi gyz…. Soka ilo mulungu ntchito yomwe akuidziwa ndi yausilikali basi olo analemba baibulo ndi asilikali kumwamba kulibe wapolice gyz kkkkk asilikali ndiodalisika mwamva inu kodi vacancy ya MDF ituluka liti tikalowe ife?? Lero pamalawi pano dhili ndiusilikali join army 2 kno the wrld kkkkk munthu nkumasilila kukhala kapokola zaka izi?? Kkkkkkk asilikali amatumikila team spirit u wl nva leav buddy behind in a battle field BRAVO MW SOLDIERS mumakwana……… And ur bzy talking abt TZ do u kno kut nkhondo pakati pa dziko lina ndi lina sichitika chisawawa mene mukuganizilamo?? And do u kno kut nkhondo amavutika ndima civilianz?? Tamaonelani zochitika kumaiko omwe kuli nkhondo and see kut amavutika ndindani?? U thnk asilikali amavutika nthawi yankhondo?? Kkkkkk innocent civilianz women n chldren r nw targets during war tym nt sojaz ena muganiza mwaumbuli apa
Asilikali awa, mmh osatinso asilikali koma astikali. Astikali awa akutengela nkhaza za Mutharika. Nkhaza sikumenya kokhatu
mukungotha ma Arvs basi ma complications akakuvutani kumenya munthu, asilikali thupi lyk toothpeak zopusa eti, jce or msce ndi kachaniso at this tym, eti leutenant, commander only at beating civilians and in most cases amakhalanso azimayi, rubbish, stop this shit immediately, ngati ndinu mashasha akanatiimitsa kutsekulira port mwachipongwe chomwe chija? koma inuuuuuuu musanilalatise mwava
Shaa angomuswa basi osamuonetsa buluzi wang’ala bwanji.
Ndigwirizane ndiamnzanga amene akunena za asilikari aku RSA,ndizoona kuno Ku SA siungaone asirikali a army chisawawa ayi,amakhara amwambo pamodzi ndi apolice,Zimene amapanga aMDF penapake ndiumbiri zimatha kuthandinzira anthu okhara mdzikomo osakhara ndimantha ndi Iwo,ntchito izingokhara kumenya anthu,kuwawopsyeza za ziii,mukaziona enanu mukadzapita Ku DRC,APA mumangodya ndarama zaboma popanda phindu,
oh noooo poor man is in hospital now beacuse of the bunch of the stupid soldiers, wishing him a quick recovery
Colinga Awawonere, Ufiti Bas Yesu Alibe.
That’s all they know
asilikali anji omenya ma civilian
Ma soilder sadziwa kuti pamenepa amaonetsa umbuli wawo onse,Cas munthu wam’bulayo ndi Mmodzi,Muoona ikubwera TaTa yokhoma bwino like akupita kunkhondo,Kuonetsera2 Mantha cas anthu odzaza TaTa kukamenya munthu Mmodzi ndekuti zimaonetsera2 kuti asilikali akumalawi ndi Panja peni peni,
Kkkkkk,koma ndye mungawanyoze a silikali argues,mmmmh,pot ndi pa social media’pa,kkkkkkkk,inutu simungayankhule manyi mukunenawa face to face with a soldier,dzabwereni ku monkey-bay mudzapeza a silikali a decent,openers,a magalimoto awo,otchena,koma ukawayamba!!!!,udzawaona ngatii savage’di,kkkkkkk,respect them please!!!!!
Punish them.
Fuck the Malawian soldiers
Ndizoonadi palakwika penapake koma tisachulutse kunyoza atsilikaliwa koma tingozuzulapo chabe mu njira ina pokumbukira kuti iwowanso ndi anthu omwe angathenso kulakwitsa m’machitidwe awo,kwa ine ndingoti “plz achitetezo lemekezani anthu amene mukuwateteza poonetsa chikondi pa iwo pokumbukira kuti inu mwatchedwa kuti atsilikali kamba ka iwo.”
Ndawona ndmaso angah zimene ku chirobwe
Malawi uchisi basi.
thats how foolish soldiers behaves
Asilikali ake ati taona asilikali ife pali chaninso apa taiputeni Tanzania ikupondeni muone.
Kkkkkkkkkkk its true guyz asilikali achiMalawi ndi achikape ngati ineyo kuno ku Durban sindinawone nsilikali olo wapolisi kupezeka kumowa ali mu unifolomu ndipo ndizosowa ukawona apolisi ali m’phabu ndite kuti akusa anthu amene aba penapake ndiponso polowapo amakhala atapemph a mwini bar
Bunji osangopita ku mwazambiki kukaphunzila nkhono . Kuzolowela kumangodya beef basi.
Shame on uuuu
ife tikukwera ma minibus ndi masoldier mmaikomu malo akatha kuimilira ife tili pa mpando osat ma soldier athuwa matama nthoo nngat anapanga ndi interview yomwe chonsecho anangowatenga ankolo awo
Lol ndalama zamisonkho yathu kusewela nazo kumeneko. Antcorruption ifufuze ndalama amaseweretsazo zachoka kuti?
come to S.A u can’t see solders everwhere like beggers they r well organised bt if u go to mw mmmm so shame drinking wine with sevilian while they r on duty.I hate them like my shit.kumangowaloza basi asamajaile
Don’t fight the people you are defending
Kodi inu asilikali musatisowese mtendere ayi dziko lino ndilathu tisakhale ngati ndife mafolena ayi komanso usilikali ndi uniform yako tsiku lina uzapezananaye zako nayo wotopa azakukwaphula uli muniform yakoyo
Adzaona polekera akadzayamba kunyera miyala ya telazo. Atakumana nazo.
Ukakhala kuti uli Ku Joni sungadziwe kuti ndikucheza nayeyu ndi msikali pokhapokha udzamuone ali mu uniform. Asikali kapena asilikali amayenera kukhala osunga mwambo osati omenya anthu omwe amayenera kuwateteza.
A galu amenewa kuda
Such a turd try me one day
Mahule awa lnu amangoziwa kunyenga basi
Nde kut anakunyengapo
Anakulizanayo utapolama eti.. Kkkkkk
Kambani nkhani yi modekha tonse Ndi a Malawi. Inde ndizowawa koma tiyeni tiphunzitsane kuti ndewu ilibe phindu
At a beer place anything goes. Asirikali pamenepa mwawonetsa nkhaza and abuse of powers vested in you
mmmm amalawi malo molimbana ndi njala mwayamba zina
Vuto sanamenyanepo taiyambeni Tz akukutheni
zovuta
….. The weakest army on earth want to be clever on armless poor civilians..! whaaat a shaaaaame……!
Mbuli zawathu izi ndipo amafuna kumapatsidwa ulemu ngat ntchito yawoyo analowera masters kkklkkkkkk zaumbuli bas ,, ngati muli madolo kaishoshe Tz tione
Mukaputa anthu kumowa kumadalila gulu agaluinu tikumana kumowa komweko
u need to respect us osadelala alaila inu
Kikikikikikiki,,,,,,,,,, ndili pano to read the comments,,, tiye nazoni zikukoma hevy,,,,,,,,,,,,,,,,
Bwanji azapange ka friendly ndi aku Zimbabwe ka ngodu
Akhuta nyemba amenewo asiyeni njala ikawa kwapulaso akadye anthu otani amenewo akamvula unifolomo ndimunthu wamba amafuna azisowetsa mtendele basi cholinga aziti ndi asilikali aliowadza khuni kumakampu.
Osaopa ndi dzina chabe loti ndi asilikali
But please if i come there I don’t want any accuse
Even GPS asilikari amakanika kuipanga follow…!
Map reading yake it imene munawerenga?..Zopusa basi, asiyeni Amalawi asakhale akapoli’mdziko lawo..
Ntchito kugulitsa zipolopolo kwa anthu akuba ndi Osaka ma Albino?
no mundo estamos sofrer por causa d esses gatunhos zimandi wawa hevy
Kkkkk kaya aisova
Asilikali aaaaaa wamba amakombola kumangotyapidwa
Mwawayamba dala tiyeni nazoni
Kkkkkkk a pmf bolatu amatetezako ko agaluwa angooletsa zida basis mantha!! Osapita kutanzanoyako bwanji kimenyela nkhundo nyanjayi chamba eti?
Asilikali wa akugwira ntchito ngati kuti akuchita kukakamizidwa!,mangawa omwe ali nawo kamba kochepa kwa malipiro akuthera kwa anthu maka akakhala kuti asiya kopanda ufa kunyumba akumalusa kwambiri,kodi bwanji osangosiya basayo ngati mukuona kuti sizikukuthandizani?Ftsek!!!!!!!!
Ulemu ukusowa asilikali athu we do not hear such stories in south africa but there are many soldiers
N ntchito ya asilikali ndikutiteteza ku mayiko ena osati zopusazo
Nthawi zambiri amakhalanso mabongwe ku baracks ko akatuluka amafuna kukhala ma shasha mbuzi zawanthu mmatukwanitsa ena osalakws
ngati muli asilikali enieni pitani ku Tanzania mukawaudze zanyanja akakutizimuleni muone
Maboys mwationjeza timaka mpaka mmakomo mwanu musamale. …. ngati amafuna jc ndiye ndikanatani ok…
Kkkk mpaka jc basi
Civilians kuphweketsa zinthu.. Akuchita bho usamayese!!
Ma ARV okha okha
A civilian is more dangerous than a soldier even a police man,,,when civilians come together they are not izy to deal with,we don’t need to face that experience in malawi plz our soldiers respect yourselves,,do u know what’s going on in USA,turkey and France all around the world,civilians when are tired of horriable behaviour becomes more dangerous than u our soldiers,,,
zoonadi mkulu matama amenewa kumachitira munthu opanda mfuti? ngati ndi ululu tomsefe tikumva ululu
Tikamapamantha Afana Oderera Sitima User Mfut Km Ma Brow Ndemukat Mfut Mukunena Mfut Yake It
kkkkk kukhala soldier sikumenya ukunama@paneciah
Zitsiru za asilikali kupamantha nde kuti chani,osakapamantha akazako akukudabula aja bwa,anthu akuba
man mwalemba zanzeru, uyu akuti amapamantha afana odelera mesa amadalira gulu” abwere kwaine yekha tiyesane man to man ndiphunzise Kung-ful
kkkk muzaziona
choka mlonda wachabechabe kaya uti ndiwe penaciah u do dat rubbish bcoz of ignorant. work hard so dat u teach yo children not to live savage life like that of urs.
amadalira gulu zitsilu zimenezi ife wina tinampamanth kwa bvumbwe.tamulandans nkazi
ndiye tizimenyana one kwa one, osadalira gulu
Ma Soldier samakhala gulu koma 1 family
gugz dnt play wth souljaz if u dnt hv anythng to do jst go ku toilet coz u cn be dead n mints
ma soja my foot mmangopagopamantha xoledzera inu
Loko Munganyoze Bwanj Km Ife Tikuvaya Chitsogolo Enanu Musamale Apa Ndukudziwan Kaya Mukupangira Kundidziwa Kumene Ine Osamandizolowera
Peneciah sogolo lake liti,we already resgmn
Come and beat me
Ndimenya Pat Mmene Mukuonekeramu Achitsiru Stupt
Tasilikali ta JCE ngati iwe #paneciah ndomwe mumazipopa kwambiri. Gulugufe iiwe et?
Sindikomenta ndikuopa kukhomedwa ulere
Nanga ntchito amalembedwa ndi J.C?
The most interesting thing with such issues ndi zoti u wont find a Cadet doing such uncivilized acts. i think mwina requirement inakhala Degree for one to be a soldier rhere would be descpline.
They are savages!!! Total savages!!! That is why you see them putting on a uniform even when they are on leave. Savages!!!!!!
Kodi tikamati dzikoli liri m’manja mwa agalu mukuona ngati a galu ake timanena ndani?
Kunali anthu a Xool achina Njoloma koma chifukwa cha nsanje munawapha…!
Tapitani Ku Mozambique mukalande area yathu yomwe ma Portuguese anatilanda thawi ya ma British.
Komaso talimbanani ndi mataifa kti tione kti ndinudi well trained!
amangoyenda ndi zima bag mtown ataikamo zovala za kunyumba kwawoo….Za ziiiiii total savagez…
Kkkkkkkk putting on uniform on leave,,,,u have made my day kkkkkkkk
Koma kuopa moza.
USELESS COWARDS….GRANT COWARDS…NOT SOLDIER
I don’t understand why some people clicking #like on story. Useless Soldiers
Lazy bones…!
Kodi imeneyiso ndi ntchito?.. Pajatu zikavuta aliyense amatha kukhala Soldier bola kumvetsa kti mfuti imatani…!
Musazuze a Malawi osalakwa pliz!
Ndiwe opusa khala chete
choka iwe mbuli za asilikali za jc chomenyela anthu ndi chan?
Iweyo Xool feez yako yalipiridwa ndi asilikari eti?
amatero kulimbana ndi anthu wamba ndikulanda makala komatu nyanja paja adatenga aTZ , ma truck amafuta ndi aja adatenthedwa ku MZQ pepani pepani
Phindu la malawi army sindinalionepo chibadwire changa,instead of protecting their country koma nkhanza zokhazokha,akapita ku DRC kophikira asilikali ammaiko ena zopusa basi.training ndi training koma kulanda makala dziko muli njala ili angoyang’ana bola asilikAli a zaka za mbuyomu achina,matewere,yohane ,chigawa amazuzula boma.
kumangowaloza basi stupid solders
mbuzi zawanthu zimenezi zimandibowa kwabasi.mbuli zolowera ntchito primary school leaving certificate. amazitenga ngati ndani kaya? ofunika ku kumana nawo mma Tarven mu kumangowapha agalu amenewa
Nde Yake Malamulo Ali Mmanja Mwathumu We Can Do Anything We Want Here In Malawi Mwachepa
usilikali amapitako ndi a JC nchifukwa saziwa cholinga cha usilikali
Akulephela ndikulemba english yabwino
usilikali sintchito yonjoyasa . anthu aliku usilikali mbuli za anthu. amazitenga ngati kuti ngophuzila chosecho ndi mbuli. ikakhala mduti njosavuta kugwira ena ndi zina chabe kuti usilikali koma angotolela zikwama.
Paneciah if l were u sindinakayakha check ur grammar
We don’t care about your so called grammar dat ix sojaling pace
Bola Mwamva Agaru Nomsenu, Mudzangoyerekeza Kushosha Mmodz Mwa Ife Mudzawone Kaya Ndikudzimva Kuphunzira, Komabe Muli Pans Mafana Muzipereka Ulemu Osamaphweketsa Ndipo Ine Sindinalowe Ntchitoi Chifukwa Ca Jc
Kmaso asamanyade, usilikali mkachaniso? Za umbuli baxi!
Hey u idiot stop talking shit. Usilikali sikuti ndiwe chitsulo. I have power than u. A real soldier has manners. its for lazy thinking pple. Ngongole mumahawkers pwa. What are u talkn. Akunyetsa ukatengera mawala.
Choka mphawi iwe kukhuta nyenba zofumbwa eti? ntchito kupempha galu chitsilu ine ndejha su gandimenye wamva???
kodi ku malawi kuliso asilikali
awaso inu
Mukuiputayi ndi #Civilianlifematters
A forest olanda makala
Zitsiru inu Tanzania ikukukanikani
Amumenya ulere!!!
Kodi mukudziwa zomwe ma citizens akuwapanga a silikali ku turkey…. zomango khalira kumva kuti wina wamenyedwa ndi a silikali ✋zitheretu zimenzo otherwise muzawuwona mkiyo wa umodzi wa anthu
Kodi bullets ndi moyale zinathabwanji
They are only good at beating civilians & threatening ppl at tarvens,its not their first time doing this unwanted behaviour,mxm go to Sudan mukatha nonse
Zitsiru zomalizira pa Malawi kumangolandila zaulele bas asaaah mphamvu salavulira pamunthu wamba ai.
asilikali ampira awa osati ankhondo mxiew!
Umafuna nkhondo Kape iwe Chonsecho umakhala ukuifuna ntchitoyi unya uwona!
iyi sintchito galu iwe
Kkkkkkkk komanso oyimba
Ndintchito iyi? alonda inu fokolo zanu
kumangolandira za ulere kkkk
Amangogula pant yekha….kkkkk
Kkkkkkkk
kkkkkk kudalira zaulere basi
bolaso ya kabaza
Pantso amalandira azilandira boxer amanamizila kuti pt
Kkkkkkkkk koma musandiseketse mwati ndi boxer yemwe amalandira??
Shame
WHAT A SHAME!!!!!!
LETS PRAY HARD THIS IS THE BIGGINING OF WORLD PROBLEMS